Great work guys, I am following from Zimbabwe. Can you add English subtitles so that those who doesn't understand Chichewa can enjoy as well. Keep up the good work.
koma Chemandota ndi Morgen mukanakhala mapasa ine nkanasiya kubereka, kkkkkkkk. Kankhani, plz keep it up you have a God given gift umaoneka serious, kkkkkkkkkkk. langizo langa kwa Chemandota ndi Morgen 'Kankhaniyu akutoperani!' Warm love guys.
Big bro inu mumatha ndipo But please man may you remix your episodes in one disc kut anthu athe kumawonera pa nkhomo mma weekend mu Zitha kukhalat zinthu zokongola kuwonera pa banja izi!! May Allah bless you brother
Big up to u Chemandota Umatimvetsa kukoma mulungu azikudqlitsan bro masophenyan anu azakwanilitsidw...... aaa aa aa afanesa ndinuo kkkkkk umakwana ailafusi yu
Great work guys, I am following from Zimbabwe. Can you add English subtitles so that those who doesn't understand Chichewa can enjoy as well. Keep up the good work.
Click where there is cc it will show
The cc function only applies if the language in the video is English
True dat
This is true they need to consider about this
Ma comedy ophuzitsa
Mwejo wakulungwa mandota mangamba geto kale
Akuluakulu apa ndiye actor wafa😅
Nice video 😘Che Mandota mwabela olakwika,timakunyadiran mupitilize kutisangalatsa
Mupaka opelekela kulibe
Ati ndililawe Kaye 😂😂😂😂😂😂 inuo ndi one
Mumakwana. Kma maili Ali bwanj
Never give up
Inu ndi madolo keep the fire burning 🔥🔥🔥🔥
Mmmmm che mandota u have why sapport
Atii kunjoya ndimahule zakumwa zake Yes🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkk
right lens ndiimene imalemba mogwirizana ndi mandotayo?
Imajambulq
@@CHEMANDOTACOMEDY oky Bossaro, ndiwe genius.
Ine ndiri gulu longony'odza pang'onolo 🤣🤣 Mumakwana inuyo🔥🔥
😂😂😂aaaah nde tidzikankha muli nkatimo ? 🙌
Ayi guys mumaitha kwabasi mmmm!!! Keep it up guys
Thank you 🙌
koma Chemandota ndi Morgen mukanakhala mapasa ine nkanasiya kubereka, kkkkkkkk. Kankhani, plz keep it up you have a God given gift umaoneka serious, kkkkkkkkkkk. langizo langa kwa Chemandota ndi Morgen 'Kankhaniyu akutoperani!' Warm love guys.
Ayi simunatchene Bola mkanjo oyamba uja kkkkk Mervis I love to watch you guys
Kkkkkk all the best guys inuyo mumatha oh akut Ife sitimachita kukozekera zonena kuzimva udolo kumeneko KKK🤣🤣🤣🤣 much love you all
Koma kankhani amakuzunzani brother 😂😂😂😂big up keep on entertaining us we lavuziyu tumachi👍👍ALLAH bless you
you are the best comedian
😂😂😂😂😂
Kkkkkk majeketi amenewa umakiniki wake uti
Tiva zokuthaitha km atakubela kkkkkk😅😅
Kuwononga zinthu zabwinobwino zija🤣🤣🤣🤣🤣akanangofunsa ndalama ina yake poti vuto silidali lalikulu koma poti Chemandota ndi anzeru zawo tiye nazoni
Beautiful one........great comedy
Mwati akufuna kulawa🙈🙈🙈
Wow nice one guys
🤣🤣🤣Kom kakhan ndi big mn che mandota Naye ndikukanika kuthawa 🙌🙌🔥🔥
Kuganiza za nsima kundende 😂🤣🤣🤣🤣🤣
Jamiel, you are blessed my brother... May Allah continue to guide you 🙏
Next
Che mandota udabwera kudzakhala iweyo🔥🔥🔥
Detective inspector Kankhani, inuyo mumabebetsa. Che mandota fans lafusi yu tu mach❤️❤️
Timaziwa ife kuti che mandota apusa ndithu, but nice one guys
Big bro inu mumatha ndipo
But please man may you remix your episodes in one disc kut anthu athe kumawonera pa nkhomo mma weekend mu
Zitha kukhalat zinthu zokongola kuwonera pa banja izi!!
May Allah bless you brother
Kkkkkk kmma iwe ndipatali 😂😂😂😂😂
Wauuu festa tsopano até embreagem de frozey komatu inu ndi mbambande 😂😂😂 koma nde kuziyambakuziyamba
Ndipo akita wafelatu😂🙌
Mandota mandota ineyo koma ndilibe mau big up bro
I like your video here in Pretoria East
Munthuyi ee! anakoza ma ulemu respect🤔🤔🤔
Kkkkkkk koma mandota umathatu ndi nzakoyo
Makaniki🤣🤣🤣mwachena ukanjowo
Nice one
iyi ili boo heavy please we need part 2
Mandota uja musazamu phwekese guys ndi shasha😂😂😂😂
Very nice guys
Big up to u Chemandota Umatimvetsa kukoma mulungu azikudqlitsan bro masophenyan anu azakwanilitsidw...... aaa aa aa afanesa ndinuo kkkkkk umakwana ailafusi yu
Mumakwana brother always watching from Michigan wachiyawo wangalusa
Ndikaledzera ndimaiwala mavuto 🤣🤣🤣🤣🤣🤣👍
Nice bro...akuti kulibe ondibweretsera nsima😂
Mmatiimirira keep it up chemandota
Kankhani ati uzadyera nsima pa waya🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
I proud you Mandota
kkkkkkk pali che mandota ndi mologeni ayi zikomo nde che kankhani eeee amatokhala serious kwabasi kupha actor
Nice one mandota
Keep up guys mumativetsa kukoma, che mandota squad moto kuti buuuuuu
Marcus watching from Durban keep it up,oktukwa awo amakhala Kuti uthenga wabaya kkkkkk love you all
Mumakwana chemandota 😃😃
The great work guys
Chobizi lol outfit ya nyowaniyi ili bho heavy!
That's more fun chemandota keep it up white❤😢😮😅😊🎉
Che mandota galimoto ija inatheka akanangobwera mkuigwilagwira bas
Umakwana mandota nice video my brother
Mudapeza munthu omubera munthu wake si kankhani tu🤣🤣🤣🤣
Great job guys
Hahahaha tsiku lina mudzayankha naxo murder mutatipha ndi opwete guys😂😂😂😂😂😂😂
Umakwana kuphunzitsa chikhalidwe keep it up 👆
Mologeni Kankhani ndi Chemandota ayi zikomo anyamata mukubwera bwino kkkkk
Yokha yi nde unakwanuratu
Aaaaa mechanical wanji opanda ma tools🤣🤣🤣
Kom mumatha ndisaname iweyo iii ayao
Iweyo 😜 ndi one
Dr mwamponda so akakhani 💥💥💥
Iyiyi nde ndi MORE ✍️✍️✍️✍️✍️✍️😝😝😝
Mulanje + mtaja = ufiti okha okha😅😅😅
Ziribbwino hvy Mr mandota moooooo fare
Great work guys I love it
Apa ndiye wafadi Mandota
Kod che mandota frosy amaseraso?😂😂😂
First to comment... inenso ndikufunikira award yanga
Timakunyadiran brother keep up the good work
Mumakwanila inuyo mumativetsa kukoma
Kangani umakhala seriousl asee
I can't stop laughing. You guys are too much hahaha
Zinaumangoona waziyambadi chemandota kuchenjeresa iwe aaaaakkkkkkkk😜😜
Umakwana umandivesa kukoma
You make us happy
Eee sindu sake Kkkkk iweyo adakoza
Ulemu wanu che mandota. Mumatha
video ya pamwamba nice one
What a pleasure 🥰 mandota ulemu wanu
you guyz you are talented.keep it up
Allah apitilize kumuzunga ndi moyo ishaallah umakwana
Excellent 👌👌👌 #Mandota
Actor we yeah😄😄😄 keep it up
Che mandota inu,ndinu katundu omanga ndi mawayana.kkkk
Big up guys mukugwila ntchito pitilizani kutisangalasa
Naweni brother wangu chemandota
Chemandota nd crew yawo 😂😂, mulibho anyamata, keep up bros
Km umakwana aise che Mandota
Mandota wapangatu upongwe sanoyo
nice bosses mmakwana
Nice one Malawian moveng
Chemandota mumakwana mumatiyimilira
umakwana mesa mandota is madala or fact mologeni
Nice job guys❤ love 😅😅😂😂😂😂
Cool