Boma La Chakwera Ili Ndilakuba - Abdul

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 3 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 12

  • @eliasMwamba-q5f
    @eliasMwamba-q5f 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mwalankhula bho man Koma enafe ndi a DPP☑️

  • @lyiemax
    @lyiemax 3 หลายเดือนก่อน

    Powerful!!!! UDF ibweleredi m'boma

  • @jamiajafali6619
    @jamiajafali6619 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu akudaliseni Abdulu

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 หลายเดือนก่อน

    Koma Chakwera ndi boma lake la MCP akuti boma likuyenda bwino kwambiri , ndipo akuti lipilila mpaka 2030 😂😂😂😂😂😂

  • @kennedychinguwo1640
    @kennedychinguwo1640 2 หลายเดือนก่อน

    Mr Abdul,don't tell us to vote for Atupele chifukwa ndi wa ntundu wanu ayi,ndale zovotela munthu chifukwa ndi wakwathu ndi zomwe zikutibwezera m'mbuyo ife a Malawi.Tizivotela munthu mosayang'anila dela lomwe akuchokela koma yemwe ali ndi mtima ofuna kusintha zinthu mokomera dziko lonse osati mtundu umodzi kapena kwao kokha ayi
    Therefore,Mr Abdul,do not bring divide and rule,with your tribalistic sentiments

  • @sheila5812
    @sheila5812 3 หลายเดือนก่อน

    Bomali aziyendetsa Asilikali basi ,zovoter zo ayi.

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 หลายเดือนก่อน

    Achakwera Maine agaluwa akuba kwambili

  • @desirebeseni6695
    @desirebeseni6695 3 หลายเดือนก่อน

    Atupele muluzi ndiye ayi mwanama man😂

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 3 หลายเดือนก่อน

    Komaso u d f singawine atupere nayeso azaononga osati masewera

  • @MecyMalothi
    @MecyMalothi 2 หลายเดือนก่อน

    Nkhani ya mayi Mia

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga 3 หลายเดือนก่อน

    Dziko lonse lapansi likudziwa za katangale

  • @Jasonnyatwa
    @Jasonnyatwa 2 หลายเดือนก่อน

    UDF ndi DPP Bola UDF atupele sanga fanane ndienawa