ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Today is my birthday no one like my comment 🥹
Happy birthday to you
Happy birthday to you 🎉
Happy birthday Dear
Tsopano a Nepman nsapato yabwanji imeneyi😂😂😂😂😂
Koma mayi shokoshoko akamamwetulira ndiye akumasangalatsa bwanji 😂
I love Mai shokoshoko she is beautiful
Beautiful indeed
Nice one
Wina akuti first to watch 45 mins ago... winanso first to comment 48mins ago😂😂😂
Ine ndikule inu muchepe
Ya ndimadikilila ine saname mimandimvetsa kukuma 😂😂 e mumandichotsa nkhawa
Kkkkk kd Mr Nepaman mwavalawo malipha maphazim kkkkkkk",Ngat wavala chang'az
Kkkkkkkk....mkazi shokoshoko ndi one 😂😂😂 pachoka zako pali malo
Francoh wayamba kumuvetsa kuwawa Nepman, kkkkkkkkkk
Mwana wamkango my favourite 🔥🔥🥰
Amene tabwereza pa nyimbo ya Nepman yo let's gather here..😅😅
Naye ching'axy angooneka ngat antchona😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 shokoshoko ndi half Man
watching from cape town mwana wapa zomba songani man joe tailor nep man umakwana
No one is talking about the nepman shoe😂😂😂😂😂
My daughter did ndipo waseka heavy 😂😂😂
Kaya ikupezeka nyanja iti
Nde mwati anyamata amapedzeka munkhalango akufuna atakatile makuwo🤣🤣🤣
Am first to watch 🎉
Kamwanako ndie kakutakatira makuwo ###koma chiphwanya kkk
Live from south Africa cape town
Kadwafu kkk welcome back mr chokochoko
Nep man mwaluzatu apa kkk
Ana amudyangu ose afoira kwa zikazi kkkkk following from south Africa Midrand side
Kkkkkkkkkkk km Mayi shokoshoko halla😂😂😂😂😂
Kkkkkk akuti adapita Ku Halftime shoko shoko wazibwana ngenge Ngati imeneyo ungayipitile Ku change zoona
Kkkk ashoshoko akuti za size ukuziziwa ndiwe😂😂😂
Half Muthu kkkk 😂
Kkkkk inu mukule ine ndichepe yemweyo
Apa bolano yayamba kuveka
Nsapato ya Nep man kkkkkkk
Mwati akusintha chani chikombole kkkkk koma guys za size mukudziwa ndinu
Kkkkk koma mwana wa mkango aaaa wabwera kuzakhaladi sungamuthandize chiphwanya moveka bho
Mlelemba last scene wapha hvy kkkkkk
Mulelemba wati bwanji 😂😂😂😂 APA iliboh heavy nepman Mpakana kukana nsima at nkhawa kkkk
Kkk Nepman mwati kufumsila kumakuvutani mkazi walora kare uyo
Koma mlelemba 😂😂😂😂 umandiwaza
Km nyumba imenei ikalipirudwa let kkkkk yamalata,yosawotcha kkkkkk abale ziliko
Koma ili bwino apa ndikuwobela Ine kuno ikumveka
Junior atakatile makuo bas 😂😂😂😂
Quuen love you ndwe wabho I hope tizakumana zakuone
Ambuye ndiwabwinooo koma amulelemba
Junior akufanana ndi mwana wa mdyangu wa mkadzi uja
I'm watching from blantyre ndirande ❤
Kkkk Nepman my guy kuuma kwabwanj uku 🤣 komanso silipasiyo nde eee 😂 mai shokoshoko mmandiwaza hvy 😂 Junior Mdyangu kupasidwa ndalama mkuzatulukanso nd nsima yomwe 🤣🤣🤣
❤❤❤❤ first to comment
Kom nsapatoyo kkkkk😂😂😂😂
Upulofeti wako wabozawo kkkkk
Km nepman ndimavuto nsaname mpakana canavas wa fish ai zikomo😂😅😊
Mai shokoshoko can smile 😂😂😂 beautiful smile always
Chipwanya maboza Kaya 4n ndyawodi❤😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 Akazi koma akazi Ashokoshoko momwe muvutira muja koma njara ija anakonza
Ati nzanune ndathodwa..koma chiphwanya ..zankazizo😂
eshi weavzone wa chambo cha fresh😊😅😅
😂😂😂😂 koma amulelemba, mayi chokochoko ati nda ex anga😂😂😂
a Junior mwalilowa banja koma shokoshoko akupeze😂😂😂😂
Watching from Westville DBN❤
From Mozambique watching the program
❤❤staff ikokedwe🎉
Mule ufuna umpake peanut mmanja mwa Mai Shokoshoko😂😂😂
Yaaa yayamba sopano ❤️❤️
Kulibe mpira opanda change😅
Kauzeni ankolo akufunsililreni mnakazi oyimbainu hillbrow jouburg
Inu mukure ine nichepe😂😂😂
Agwidwà kuno mayi shokoshoko 😂😂
Kkkkkk koma sapato ya nepman makina😂
Koma prisca madress omwe umavala😂😂
Chiphwanya ubashala wakukwana bwelako kkkkkk😅
i like it
Zikukhara bwanji volume
Nepman mutu sukugwira😂😂😂
😂😂😂Achphwacha mwana wa mzako half man
Mai shokoshoko mumativesa kukoma ❤❤❤
Koma sapato ya nepman kkkk fish shoe 😂😂😂😂
Mayi shokoshoko ndi amunawo😂😂😂
Mwana watakatira makuwo kunooo🤣🤣🤣🤣
Mawu sakuvekatu koma bwanji
Kkkkkk koma banja la adyangu silizatheka
😂😂😂kom mulelemba ubusa muwusiye mwava
Mayi stive from mayi shokoshoko aaaa mwina tizolowerabe 🤣🤣🤣🤣
Kkkkk kumadwafu😅😅😅
Nanu mayi shokoshoko mpakana shoti ❤❤❤❤❤ kkkkkk
Nep man game wailuza kkkkk
Kudontha mafilu defiya
Mai shokoshoko kusinthasintha chikombole😂😂😂😂
Bwanji osangomenya ameneyo a shokoshoko kkkkk
Mabodza chiphwanya😂😂😂
Kkkkkkk mayi shokoshoko ATI x wanga 🤣🤣🤣🤣🤣
Tafika💃💃💃💃🔥🔥🔥🔥
Amene tinatumizapo transport let's gather😢😢😢😢
Kma chiphwanya aaaaaa😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤
Koma nsapato ya Nepman 😅
Komatu nepman slippers lmeneyo😂😂
Kom Abusa mwata sah watan ???
Mulelemba koma 😂😂😂😂😂😂
More fire mabomba
😂😂😂😂 anapita ku half time a choko,choko koma guys ndaseka kkkk
nice
Kodi Sindi ( Mai mulemba) mubereka lit?,😂😂😂😤
Shokoshoko anali ku half time 😂😂😂😂
Koma chiphwanya ndidolo😅
Mumaitha guys

Koma ili bwino apa ndikuwobela
Ine kuno ikumveka