Fr, Elizeo Nthalika:::wa mpingo wakatolika akupitiliza kung'alula MCP_ _Ana okula ntima

แชร์
ฝัง

ความคิดเห็น • 41

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 4 วันที่ผ่านมา

    I love this message!

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 4 หลายเดือนก่อน +2

    Katolika imadana ndi anthu oputsa Chakwera udziwanso, APM my vote ❤❤❤❤❤❤

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili1362 5 วันที่ผ่านมา +1

    Mawu omveka bwino kwambiri 🙏

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 4 หลายเดือนก่อน +2

    Akuluakulu agreed with him,i traveled different places especially in the villages kumene olemera zangatsafike moyo wake onse,athudi akuvutika kuti mukawone madzi omwe akumwa apa chitsime guys you wont believe it,i agreed with u too.ine Wales munundo,from ndauza village,TA Changata.God bless you guys keep on.

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon วันที่ผ่านมา

    INUYO MA BISHOP MUKUTIIMIRIRA OSATI AZIBUSA ENAWA ADYERA KUIWALA ZA CHIMENE MULUNGU ANAWATUMA , KEEP IT UP,

  • @annembepula
    @annembepula 7 วันที่ผ่านมา

    Musanyoze atumiki Amulungu anati musakhudze odzodzedwa ake akunena zowona iyi ndi imodzi mwa ntchito akuyenela kugwila padziko Ambuye akudalitseni ma Bishop

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 7 วันที่ผ่านมา

    MAY GOD BLESS PAX ROMANA IN MALAWI

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 5 วันที่ผ่านมา

    Power to that 🙏

  • @user-vu9rt8gj3o
    @user-vu9rt8gj3o 4 หลายเดือนก่อน +1

    Apm my vote

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 4 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera anawaputa akatolika ndipo akhaula zedi❤❤❤❤❤😂😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 4 หลายเดือนก่อน +1

    Amen

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 4 หลายเดือนก่อน +1

    Salute

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 9 วันที่ผ่านมา

    Tell them man of God

  • @jonathanmalanda7742
    @jonathanmalanda7742 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu akulankhuleni mwapadera mutha kukhala amodzi mwaathu osokeretsa anthu

  • @annembepula
    @annembepula 7 วันที่ผ่านมา

    Zamphavu mmatiyimilila ma Bishop

  • @user-hl3vl9nt1b
    @user-hl3vl9nt1b 4 หลายเดือนก่อน +1

    Awuzeni father sakuziwa anyapipewo

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 4 หลายเดือนก่อน +1

    🔥🔥🔥

  • @JanaMussa
    @JanaMussa 2 วันที่ผ่านมา

    Zona malume mutalika

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 6 วันที่ผ่านมา

    Kunena mosanyengerera zofooka za awa zapambana eg kugwa kwa kwacha kusowa kwa cha kudya kukwera kwa zinthu ndi usogoleri otembereredwa

  • @PetersonBizwack
    @PetersonBizwack 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbambande kulamkhula mogwira mtima pitilizani

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 8 วันที่ผ่านมา

    Ndiye muwaziwa alonwewo pano kuti ndinjuchi komaso olo nchewa oganiza fetereza mene wadulilamu chilichonse chakwera pano nkumavutikaso ndinthu kuvotera mcp guys olo muja asanaonjezere mavutowa pano ndiye nyanyi akanamgomusiya chilima akapikisane paground koma amamuopa koma mulungu apanga njila

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 5 วันที่ผ่านมา

    Pakufunika changu kuchitapo kanthu tisanathe a Malawi

  • @gracemnenula2518
    @gracemnenula2518 7 วันที่ผ่านมา

    Mawu mawu achilungamo awa

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 6 วันที่ผ่านมา

    Mpakana amipingo kuku ndaura chakwera uribe peace bas

  • @MemoryKamanga-pu1tj
    @MemoryKamanga-pu1tj 4 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi bwanji sipakukambidwa zoti tisanavote tiwunikeso malamuro a kayendetsedwe ka dziko la Malawi?Chifukwa kunena zoona a Malawi tikupwetekedwa ndi malamuro adziko lathu lomwe,tili mu democracy koma malamuro ndi omwe aja a chitsamunda ndi Kamuzu Kodi pamenepo ziku balancer?

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 6 วันที่ผ่านมา

    Koma zoti anapochera tuma envelope ndi zoona kapena ayi

  • @user-vq1qf2hn4y
    @user-vq1qf2hn4y 4 หลายเดือนก่อน +1

    Aaaaa malo moti azikakwatirana amuna or akaz okhaokha😂😂😂😂

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 2 วันที่ผ่านมา

    MCP dzitsiru dza anthu ndithu inu kupha Chilima munthu oti anakuthandiza kuti mulowe m boma

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka 3 หลายเดือนก่อน +1

    Akatolika samapanga za mpingo koma ndale ndi usatanic basi.anthu ama thanyula awa opembedza mafano,ena oyika mkhosi ena mkachisi.
    Ine ndi mkatolika koma my vote is for Chakwera basi

    • @EmmanuelGasiten-fo5dr
      @EmmanuelGasiten-fo5dr 9 วันที่ผ่านมา

      Iwe ndiwanyau, osati mkatolika

    • @AliceYankhoKakusa
      @AliceYankhoKakusa 5 วันที่ผ่านมา

      ​@@EmmanuelGasiten-fo5dryes uyuyu simkatolika

    • @james-zd2nz
      @james-zd2nz 5 วันที่ผ่านมา

      galu wachabechabe nkhope ngati yovala

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka 3 หลายเดือนก่อน +1

    Vuto ambiriwa ndi alomwe omwe mkale lose sanavoteleko MCP ndipo sitisowa vote yawo

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 6 วันที่ผ่านมา

    Iyi ndi nthawi yothana nawe wa satanic tikufuna chilima wathu😢😢

  • @OssmanAbubaker-st7pu
    @OssmanAbubaker-st7pu 7 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi tilidi kubagamoyo tinalakwitsa poasakha boma la MCP boma lopandamzeru

  • @isaaczuze
    @isaaczuze หลายเดือนก่อน

    Chisilu china chake chikuti akatolika za ndale ndipo amapanga mathanyula ......iwe ndiwe munthu wopusa kwambili ....mmene chawera mmene waonongela zikoli ungamalembe zopusa zakozo .....iweyo ndi mbuzi kaya ukudya nawo ndalama zokubazi tazingodyani muzaona polekela ....galu iwe

    • @ChimmsRichardOrden
      @ChimmsRichardOrden 8 วันที่ผ่านมา

      Koma akunkuyu nkhaniyi Adaimva?akuyenera kuwauza a bwana awo kuti mwina asinthe

    • @AliceYankhoKakusa
      @AliceYankhoKakusa 5 วันที่ผ่านมา

      ​@@ChimmsRichardOrdenyou mean he doesn't know what is on ground? He knows

  • @isaaczuze
    @isaaczuze หลายเดือนก่อน

    Ndipo wa satanic ndi iweyo ukudya ndalama zokuba zachakwera ndipo chakwera ndiye wa satanic weniweni galu iwe