Mulipo mwakwera ndege ya boma. Bwanji amanama kuti zathu. Chakwera atule udindo

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 4 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 37

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 3 หลายเดือนก่อน +2

    Osatopa, osaopa osafooka tiyeni guys tiyimwe ngati anthu aku Kenya,Viva SKC Viva

  • @Masturdthepoet
    @Masturdthepoet 3 หลายเดือนก่อน +3

    More than 💯 agree iweyo walowa mmaganizo mwanga ndikuonjezanso... Thank you very much. I love it ❤️❤️❤️❤️❤️ TIYENI TIKAPANGE ZOMWEZO BASI

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 3 หลายเดือนก่อน +5

    Iwe ndiye wanena zoonadi what we waiting for, Chakwera mtiti yokupha uchoke pita udzikaba chopekeka ku church

  • @MercyKatongo-p9b
    @MercyKatongo-p9b 3 หลายเดือนก่อน

    Guys let's go let's go am coming from Zambia chakwela out

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 3 หลายเดือนก่อน +1

    Its Chakwela Ndi Cibwenzi cake cimakhala monyasa cisilu cija for me

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 3 หลายเดือนก่อน

    A Malawi Ukani ku Umbuli and fight for a good Cause..Chilima was Malawi's only Hope 😭😭😭...Jac up go and protest..Wise Words Sir..Go People Go We behind you

  • @dinganinedsontchongwe610
    @dinganinedsontchongwe610 3 หลายเดือนก่อน +4

    100 percent correct lets go out guys

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 หลายเดือนก่อน +1

    Acorrin Zambia ndalama zathu angogula mipango yadzaza ma suitcase koma mene a alibe ndalama kaya amai amene wa amaoneka ngati mwamuna tu ndi zikhale ng'oma amaoneka kaya ngati chani

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 3 หลายเดือนก่อน +1

    Zoona zake,

  • @Masturdthepoet
    @Masturdthepoet 3 หลายเดือนก่อน +2

    Usazafe aise wandisengura kwambiriiii 👍👍👍

  • @HaliJana
    @HaliJana 3 หลายเดือนก่อน +2

    MUMUUZE CHAKWERA PANYO PAMAKE SITIMUFUNASO KU MALAWI KUNO MIKE UYU TIMUSOWESE KENAKO ZIKHALI MKAKA KABINETI YOSE KUIPONDESA KASIPA MOZI MOZI CHAKWERA WAKUFAYU UYU CHAKA CHINO MZIMU WA CHILIMA UMUGWILA PAKHOSI, CHAKWERA PA MTUMBUPAKO KOMWE ULIKO WAVA

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 3 หลายเดือนก่อน +2

    Pepani president ameneyi ndi wa MCP...enafe tilibe

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 3 หลายเดือนก่อน +2

    ❤❤ zowona tituluka

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 หลายเดือนก่อน +1

    Angakadye ku Parliament anthu akamapanga ma demo ndiye iwowo amaotcha katundu wa Malawi azawo osawotcha katundu wa boma ndi ma nyumba aminisry

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri 3 หลายเดือนก่อน +2

    Zoonadi Brother inuyo ndizoona ndithudi

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo mene aphwera ngati galu saulosi chilima

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 3 หลายเดือนก่อน +3

    But what is it that you have done apart from talking come we do together

  • @SostenKalumo
    @SostenKalumo 3 หลายเดือนก่อน +2

    Anthu muli ndimatha hvy ndiye kut abro wa sadalankhure zanzeru?

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 3 หลายเดือนก่อน +2

    Amalawi ndi amatha koopya,kaya kofunika titenge, anyamata ndi asikana aku Kenya kaya,kunena,zoona andale,anatitola,mumalawi muno.munthu,akusainila kuti zikwele muziko amalawi tinangoti chete.ku Kenya uko,kungolankhula asanamalidze,anatuluka, anthu.lero,akumufuna,achoke.

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds 2 หลายเดือนก่อน

    Nthawi imeneyo mudali kuti boss kuti mutisogolere ziwawazo

  • @RitaDickson-ls7ol
    @RitaDickson-ls7ol 3 หลายเดือนก่อน +1

    Also you you are Malawian so you can start demostration 8:05 8:05

  • @omegasheibamussa3900
    @omegasheibamussa3900 3 หลายเดือนก่อน +2

    Vuto ndi ku Malawi kuno ifeyo ndihogona Kwambili

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 3 หลายเดือนก่อน

    Akulu akulu bomali likutipweteka misokho phwi phwi. Wina nkumati zandale sizindikhuza . Akuluakulu andale atigulisa ku Azungu Kodi ndalama yathu yatha mphamvu bwanji . Asamunda akadatilamulira

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa3 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mautu awa

  • @BlessingsChitekwe-k5z
    @BlessingsChitekwe-k5z 3 หลายเดือนก่อน +2

    Zooonadi mau mphamvu kwambiri

  • @DavieKanthiti
    @DavieKanthiti 3 หลายเดือนก่อน +3

    Not Ali kutali aye inuyo tengane uthengawo wosati muone munthu kt akulankhulila kt chilungamo ndichimenecho kuotcha zosezo sanganene kt taononga katundu wathu mayazi

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc 3 หลายเดือนก่อน

      ​@@MartinKapanga-q6mimeneyo ndiye yofunika basi tidzaomba manja,mpaka liti.

  • @Floranyimbiri
    @Floranyimbiri 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ulemu timapeleka kwa bambo kalindo enanu mukungokuwila kutali uko and ife titaphedwa kuno inuyo or mwana wanga simungamgulile ndi boxer yemweyi. Bwelani tidzayendele limodzi osati zongolubwa muli kunjako ayi

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc 3 หลายเดือนก่อน +1

      Inu,for example,ku south Africa uko,ana asukulu ndi omwe anasitha ziko lija.ku, Kenya uko kusitha, chifukwa,cha, anyamata ndi asikana.inuyo,mukaope kufa,iyaaa ndichifukwa mukulamulidwa ndima America,ndi ma rwanda.ma,china awa angoba, gold ndi diamond kumapita,nazo kwao.chifukwa,cha anthu ngati inu.demo sikuyenda,ngati mukupita,ku ukwati, imeneyo ndi demo?iyaaa.tikhala, nawo pa demo ikubwelayo mudzaone.

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 3 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwela ndi fiti

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 3 หลายเดือนก่อน +1

    Tiyeni tikaotche konko

  • @Floranyimbiri
    @Floranyimbiri 3 หลายเดือนก่อน +1

    Amwene ndukhulupilila kuti muli kutali nde zisiyeni zidachitika basi palibenso angabwenzeletse miyoyo ya azibale aja. Inu mudalikuti?

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 3 หลายเดือนก่อน +1

    Manyi akenso hule ameneyo

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 3 หลายเดือนก่อน +2

    Zowona zake zimenezo anthu aku Malawi tikugona kwambiri osadzuka pa ifa ya vice president eeeeeeeeesh analoza ife anakwanisa eeeeee mabvuto tili nawo osayamba

  • @Floranyimbiri
    @Floranyimbiri 3 หลายเดือนก่อน +1

    Amwene ndukhulupilila kuti muli kutali nde zisiyeni zidachitika basi palibenso angabwenzeletse miyoyo ya azibale aja. Inu mudalikuti?

    • @uzaleuzale8603
      @uzaleuzale8603 3 หลายเดือนก่อน

      Tiye uko iwe nthaw zonse umakhara kumbuyo kwa mcp osaganizila zowawa zomwe zikuchitika mdiko muno