You're all good actors Good Camera nice acting continue Piksay we know that you're the Head of these movies We trust in u if u stop acting then others again they will stop please continue A ngozo From ZAMBIA
Very nice kwa Malawi mutapitilidza kutele ndikuganiza kt Usova azaika pa top Malawi tsiku Lina nonsenu ndi ma actor abwino musamaziyanganile pansi kms ndipempe kumapanga mwachangu zinthuzi timaona kuchedwa thank you all.
Let's gather right here for Ganizani 😂😂😂 thus dude always make my day whenever new episode comes out 😅😅
Dolo😂
Big Up Man Gani,
Uyuyu ndi dolo ,kwatswiri ,katakwe, namatetule 😂😂
He has talent
Amangoyankhula mtima uli ziiiiii
Let's gather here for Ganizani 😂😂😂😂 ati nduyenera ndipeze mkaziyo kkkkkk
Koma ganiyu gayezi😭🤣....can't take this man serious In real life olo atandilozeza mfuti🤣🤣🤣🤣🤣
Such a well-written and well-acted drama. Loving it, truly.
omwe we are here for Emmie let's gather here 🎉
Muli chikoka😂
Amene sanaitsate past seasons zomwe akunena sing'anga zawapeta apapa 😂😂😂😂😂
Shado woyeeeeee🎉
Ine ndayitulukila kkkk that's why watsata nkodzo wa A shado kkk
You're all good actors Good Camera nice acting continue Piksay we know that you're the Head of these movies We trust in u if u stop acting then others again they will stop please continue A ngozo From ZAMBIA
Can you explain very well.
meaning you did not understand what I said
Very nice kwa Malawi mutapitilidza kutele ndikuganiza kt Usova azaika pa top Malawi tsiku Lina nonsenu ndi ma actor abwino musamaziyanganile pansi kms ndipempe kumapanga mwachangu zinthuzi timaona kuchedwa thank you all.
Koma amanthu mfundo ngati Rasta ..... Fuso ndiloti udziopa
Where can I get that sound track?.. it's a masterpiece
Like my comment ❤
for what
f u
Mwna zizimba😅😅@@levisonmwale5443
Sing'anga uja watithera nthawi asazabwerenso aaah
😂😂😂😂
Aaaaaah mwauze asing'anga anuwo sakubebesa akungobhowesa iyah
Komatu Gan ndinkhan zina. Sizothandiza mwana wako ulele😂😂😂😂😂
Ganizani is always the best actor
Naye Sing'anga wapanga trace mkodzo uja 😂
Wa Shadow
Kodi whats the credits song???? Is it Sangie ft Piksy? I cant find it
agani ndi mulamu wawoyi mmmmmm ayi kkkkk keep it up guys mumakwana ndithu mumafasa osati zaphokoso ayi
Kod what's the title of the soundtrack yakumapetoyi?😢
I want that song imaveka ikatha comedy yo. Title please
You deserve to have usauver channel to a certain tv station guys you have got Skill and talent achina ganizan big up broh.......
Ganizani 😂😂😂😂 Ngozo flu yo bwanji ...nsinganga uzipesa eh eh eh 😂😂😂😂😂😂
Angogwila mfanayo nkono.avekele misala chani kapena akundifuna😂😂 eish chemwali awa hiyaa😂
Chemwaliwaa phokosoo kwabasii 😂😂
Gani aise❤❤ iwe ndi vibe ya bho,,umatha aise
Kmatu sinathe bhoo 😂😂😂 next episode chonde fast fast izayambire pompo😂😂
Much love team yonse imu mulibe mbola
Naye sing'anga
Bar man kudzakhala ngt wayamba kugwelamo mwa amathu, kenako alamu ake a Gani nkudzangofika😂😂😂 love u gusy
The ending , now that's what we call a cliffhanger! Apapa mwatipatsa njala ya next episode
Kkkk man gan tsopano😂
Like my comment 🙏
I love that you've made the episodes longer. Sharp!
Hahahahha Gan aaah iwe ukufunaso uziswa mtedzaaa day yothandizaaa please 🥺🥺🥺
Am craving for the next episode abeg ooh
😀😊☺ashado ongoyenda ndinjala
Anawo ndizingowathandiza ulere😂😂😂😂😂Koma ganizani ndi dolo kkkk angozo simungazimvetse, msamangothandiza ulere
Kodi moni waa mtundu wanji umenewooo asing'anga (dotolo) 😹😹😹😹😹
Ati pepani eti ineyo nkoyamba kukhala pafupi chonchi ndi sing'anga🤣🤣😂😂🙌
😅😂😂😂😂😂😂😂oky I have alot of comments.... buh first... Ngozo ndi Patricia... it's time we see a Juniour 😂😂😂😂😂
Amathu hitting on Edo so hard😅😅😅😅😅😅
Namulondola akusatira ngini zomwe shadow anasiya pacorner yampanda wangozo😂😂😂
This guy Ganizani ndi chi vibe😂😂😂
Sitikuthandiza ulere😂😂😂
Ati namulondola wa mu handbag🎉🎉❤
This series is dope. Just needs subtitles
The song kumapetoku ❤❤
Link bwa?
Sing'anga kupanga trace mkodzo wa Last year eish
Namulondola wake ndiwaukali
Mpaka kununkhizaso kamwana ka ashado 🤣🤣🤣🤣🙌🇲🇼🔥
🤣🤣
People who don’t watch this series are missing out😂
Amathu, edo yo ngouma, tabwerani kwa ine timvane
Big up man ngonzooo the way you act so impressive mix Emm all good guys salute 🫡
Flirting yamasteniwo top notch 👍🤣....
But guys gani amatha am telling you😅😅😅 I like this guy indeed
Watch from capetown, ndazikonda!!! Ngozo sakonda zausing'anga
Amathu ndi ngozo zakumana!! Nxt!!!
Iyiyi nde yatha isanayambe and big up to Gani😹😹🔥
A Edo NDE muli kuziwa poyankha amantha !
Gan km nd actor mbambande💥💥💥💥💥
Heavy
Uyuyu ndikatswiri
Mr gan what do u mean Kuthandz ulere
Eeeh koma Emmie 🔥😂🙌
I need the song ya kumapetoyo, i like it.. anybody who know the title
Kom.kasewelo akaka ine ndizalowe nawo ndithu. I feel so good. Kamandichotsa tima stress 😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
Eshiii yathera poyipa bwanji...timafuna tiwone amathu kut atana ndi angozo ku bar
Gani😅😅😅😅ATI chilichose chaukwati chatheka kale watsala ndinkazi opanga naye ukwatiyo😂😂😂😂
Sing'anga uja asazabweleso angozo
Ganiii and amathuu inuyo ndi more 🔥🔥🔥🔥
Gani and Amathu! True artists!
Ngonzo ukuoneka ukuononga zithutu iwe kkkk all the time u go kwa Edo umakumana ndi mathu km manthutu akuti sakuziwa nde usamale mayakhulidwe 😂😂😂😂😂
Achina Gani ndi makolo,akatakwe
Next pliz ,,,,,, Tione kut Anguozo ndi amathu zitha bwanji kutengela kut apezana 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Amathu frits hard,,,komanso Ganie ati nzingowathandiza ulele 😂😂
I've been sulked into the series badly ❤❤❤
Palimbe kungothandiza ulele ayi koma make akhale mugalaundi😂😂😂😂😅
She nkope 😂😂😂🙌🙌🙌
Where can i get that song ya sangie yo or title yake ndi chani?
Mkodzo wakalekale wa shadow anakodza kuseri kwa mpandaaa
Akaxi alutsat kungowapatsa Mon basiti umva "bwanji zondifuna" 😂😂
Amavutika kukhala osayankhula... alindikavuto kameneko
Gan 😂 eeeh it's a actor 🔥 kma EDO timisechee timamuyanja😂
Isamathere pamenepo...where is the full video lol😅
Ganizani 😂😂😂
Kumuyang'anatu dotolo🤣🤣🤣
Edo anabwera kudzakhala,,, ma guys mumatha eeeeeee ❤❤❤
Ati nanga ndizingothandiza ulere😂😂😂😂
Gani akufuna azipakula😂😂😂
😂😂😂😅
Gani akuti Namulondola wa mu Handbag wafoila.......
Big up man gani
Ndiwe dolo kwambili 😅
Chi gani ndkatundu yabhoo
Komaso iyi muli ma scene onse abhoo🔥
And I like the song
Kkkkkkk anzawooooooooo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Edo amalemedwa Ndi nkhani zoonaa😂😂😂
Komaso asing'anga sanalakwise tu, paja Ashado ankanama kuti kwa Ngozo ndi kwawo 😂 and asing'anga akutsatila nkodzo🤣, Ashado ziwavutatu apa
Gan sakufuna.kupeeleka money ulele at tizikumana
Kod Ganizani kupanga madongosolo a ukwati ndikupeza mkazi amayambila chani???
Gani amandisangalasa
He is natural
Nde man Gani mwati ndakazi anu munanyerana??🎉
Tamuuze abweretse chakumwacho 😂😂😂😂😂 Che Mkope tsopano
Koma Gani amandiwaza eeeeish my favourite 🔥🔥😂
Nyimbo kumapeto title ndichani?
Live from South Africa cape town
Ati anawo nde nzathandiza ulere😢😢😢??kuganiza mobwerera m'mbuyo.
Right zakumanizanano 😂😂😂 Kodi ngozo athawidwanso can't wait
Hahahaha koma Gani ndaseka kufuna kususa kenako uthandize
😂😂😂😂 Emmie iwe nd zina zina asee😂😂
eeer kma gani 😂😂ati zonse zaukwati zatheka kwatsala kupeza mkaz ndi dollar 😂😂
Gani ndiosokoneza straight kkkk ati azimupwalanso nkaz wakale kut Airtel money ivaye kkk
Ah koma Gani amwene aaaah program ya banja yatheka kwatsala nkupeza nkazi