Love this show because it's a reminder of how ridiculous malawian men are. Albert has a whole child and another woman but truly thinks he is the greatest victim in this position, and his friend won't even call him out on his nonsense.
Phunziro lalikulu likuchokela Malo awiri, 1) ukakhala osungidwa umavela chilichonse , usayende nd uyu umasiyà kutero. 2) nkhan za banja kukambilana mwakambirana like real issue ndazikonda zmenez. Note: aunt ake a berita amayankhulitsa kwambiri ngat kut anali nd chmwemwe chot ndkukaoneka pa air nde ndyipatse, pamenepo snayende bwno ngakhare sizinaonekere! Big up fanz yonse
Koma guys this episode is the best and kumene tikupitaku ai ndithu zabwino zokha zokha .koma pempho langa mubweretseni pakati please chonde..amabhebhetsatu..
Ganizani is a rare breed of actor. tisamudelere amatha.🔥🔥
Ndpo kwabasi
Love this show because it's a reminder of how ridiculous malawian men are. Albert has a whole child and another woman but truly thinks he is the greatest victim in this position, and his friend won't even call him out on his nonsense.
😐Breath
@@mfumuhyphen 😭😭😭chabwino tipuma komano Albert akundikwiitsa ngati Ganizani ndi money ya plot.
Also, great work! Love the show.
@@mfumuhyphen😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Oooh koma zikubebera Berita azinyengesa kwa Mtebede?
@@jameskuse7767 like husband like wife.
Iiih kma berita
Mesa unachoka utapanikizika nacho Chikondi 😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 iiih ine koma Ntebe amandiwaza nsaname😂😂
Albert umatha 😅😅😅
Kanyimbo kali kumapetokonso nde kat kabhebha chochoko
Kkkkkkk belita belita uhux ndi bodza lomwe
Nzosiyana kunama muli awiri ndikunama muli ndi ine
Belita wazunzikatu kkkkk 😂 😂
Ka m'busa akaso inu eeeh🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Undikhululukire ndisiya kupemphererana ndi invigilator kkkkkkk belita woyeeee
😂😂😂😂😂😂 auntie mumenyeni chi mbamacho changu changu 😂😂😂😅😅😅
Muli bho ma guy.... pangani za ka sound track kali ku mapetoko
Km Belita mpaka kutembenuza nkhani 😂😂😂 kuyembekezera kuti zimukomera😂
😂😂😂😂😂 it's khala pa camouflage for me
Belita she is a very good actress
It's Hyphen's iiih for me 😂😂
Ife tufuna kanyimbo kali kumapetoko 🤭
You guys mukubwela bhoo. One day I will visit you
Kkkk kma Jede suzatheka 😂😂😂😂😂 omwe azakukhalirani pakhomo ana sakumwanirayi? Albert osasintha maganizo bweresani wamwanayo basi enawo akachedze kaye kwa aunt awowo kaye. Ma3ru ma3ru #teamusauver
tigaileni nyimboyo abale aaah mwatani kodi
Aunt phuma poyankhula
Phunziro lalikulu likuchokela Malo awiri, 1) ukakhala osungidwa umavela chilichonse , usayende nd uyu umasiyà kutero.
2) nkhan za banja kukambilana mwakambirana like real issue ndazikonda zmenez.
Note: aunt ake a berita amayankhulitsa kwambiri ngat kut anali nd chmwemwe chot ndkukaoneka pa air nde ndyipatse, pamenepo snayende bwno ngakhare sizinaonekere!
Big up fanz yonse
Aunt a Belita amachitadi kuonesera kuti achita kuloweza zoyenera kuchita, azidekhako pang'ono. Komabe tiyamikire zilibwino 🔥🔥
@@atusayemwafulirwa3715 ndkupezamo phunziro lalikulu mu sewero la usauver
Akuti "khala pa camouflage po"... Mtebe atumikire mlongo kaye!
Yamba kuyenda mwachangu,,,, fast fast ku get
Aunt awa ndi fire🤣😂😂
Belita akunama cfukwa e😂😂🙌
Berita Bodza😂😂😂😂
Abale Gani mutu ng'aning'ani ngati ndasi
Aunt mpatseni chimbama beritayo
Koma guys this episode is the best and kumene tikupitaku ai ndithu zabwino zokha zokha .koma pempho langa mubweretseni pakati please chonde..amabhebhetsatu..
Pakati aliku ndendetu😆😆
Amutulitse sizoona..😅😅
Life imprisonment pakati2😂
@@franciscoduartie5762 ai ine nde sindilola...🤣🤣🤣...life imprisonment kuti walakwa chani pakati?😭😭😭 @piksy tiyankheni ife..
Konzani ka chakudya mukamuone uko pakati kkk
The show is good so is the song at the end🔥🔥🔥🔥
Ase iyiyi tikambilanabe. Piksy amatha guys
Sangie u looking good 🔥 belita koma nde kunamatu uli serious🤣🤣 love it
👏🏾👏🏾👏🏾 great episode!!! Keep them coming from Florida pa boma
Belita ndi chani koma😊😂😂
Kkkk koma belita eti ndikhululukire
Ndangoonera 2mins Koma eeeeeeehe 🙌🙌 Berita waiponyera kwakuya😂😂😂😂
😂😂😂😂 koma guys women can lie eee🙌🙌🙌
Kkķk Mulungu ali pamavuto😂😂😂😂 Neba woyeeee
Belita bodza eshi malawians the danger of one sided of hearing story
Komqtu Belita Belita
Waondadi berita😂😂
ndikumenya chimbamatu😂😂😂😂
Mtebe akut mwadula madzi
Berita is olwes calm..koma apa wanama
Belita tchulani choti akukhululukilenicho......hahaha ati waonda iiiih
Kma belita😂😂😂😂
Mumatha inuyo guys 😂😂😂 Albert khululuka ndibwelele pa khomo😂😂😂
Mbusa uyu ndi power 😂😂😂😂😂
Chi neba cha Ntebe zopusa sichipanga nawo😂
Belita belita belita
Usauver inabwera kuzachotsa ma stress, nkuzatiphuzitsa komwe....
Koma iyiyi ndi fire
It's khala pa camouflage for me 😂😂😂🙌
Mtebe👐👐
Moti waonda belita 😂😂😂
😂😂Belita watheratu akuti
Wasala mafupa okha okha akut😂😂
Eeh komaaa😂😂
Chipongwe kwa ife ma small meat😀
Ndipo tazimvera chison 😂😂 Mwina ali ndimafula akulu chabe 😆😂
Neba usatuluke, akupemphelereni nonse kkkkk
Koma sanjie😂😂😂😂😂 I love your voice enway
Moto kuti buuuu🔥🔥🔥
Big up guys 🔥🔥 neba wakanikitsa aneba kudya 😂😂😂
😊😊😊 timakunyadilani gyz Koma relo nde yachedwa ,,,, paka timafuna tikulowereni inbox hahaha
Munabwera ngt coming 🔥🔥🔥
Dazi la ganizani nde likuwala ngati alipaka komba
Albert nyumba yake samakhoma
Inetu kudabwa 😅
Kkkkkk ndadabwaso
Belita belita
The song for me 😊😊😊❤
❤
🤣🤣🤣 week iliyonse ikumabwera ndi hot kkkk
Belita iiiiiiiiiiiih 😂😂😂😂
Koma sangie akut ukafotokoze wekha ku police zomwe ukuchita😂
Usauver ndzaidandaula ikazatha 🔥
😂😂😂😂😂 pemphelo lakanika Neba
😂😂😂😂😂😂ati waondaatu
Kma berita mabodza😂😂😂
Abusa akumwa gin 😂😂😂😂 Neba naye kukakamila mapemphero
Mwadula madzi neba tifa ndi ludzu
Mmenyeni chimbama ameneyo ndipo osamukhululukira😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 Belita
ati ine ndikhale oyipa nde bwenz ana abwino akumabwera
Iyiyi mwasinjanso ma guy, Jededaya Mtebede bwanji nanga chimaso masochi!!! Kkkkk neba kuzadula madzi pamene paja komanso ka mtsikanaka si kamene akathamangitsa mayi Ngozo kaja aka? a.k.a nzake wa Ganizane sing'anga wa dazi
😅😂😂ati basi bawo mwawina
Kwachema munthu wa Mulungu, Tituluke Jede ampempherere mwana kkkkkkk
eti uzandipemphelerabe🤣🤣
Angonyamuka osatseka nyumba
Belita mabodza 🤣🤣🤣🤣
Mwadula madzi😂😂
Hyphen is the best 😂😂
Eee zoona eee mwadula madzi hahahahaha 😂😂😂😂
Km nyimboyo🔥🔥🔥
Kkkkkk neba kukakamila eshiiii. AzmAi Bodza kkkkkkkkk ai nd2
It's the dressing ya piksy for me
For me too😃😃
Neighbor Ali pano akufuna mapemphelo 😂😂😂😂😂😂😂 kkkkkkkkkk
I can see improvement,,now cz every part of the sorry is about ngozo family and hyphen ,tizionako za local apa
Beli unathawa wekha love yodxadxa usanamepo
Koma Mtebe amwene aah😂😂😂
Best actors
Am a Belita u r looking good
koma Belita can lie for the whole continent...ayayay
😂😂😂
😂😂😂😂 😊
Buluku la a Ngauxo🔥
Belita😂😂😂😂😂😂
Mtebee ñdi more