Taonani izi ku MCP. Okha Okha amafuna kuphana.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 104

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +3

    Inu a UTM❤❤❤, DPP💙💙💙, Aford💙💙💙, ndi UDF💛💛💛, mumvetsere bwino audioyi mpaka kumapeto. Osatukwana msanga. Mwana otayikayu walapa.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +4

    MCP ndi ufiti weniweni inu mumasapoteranji MCP.

  • @PeterJames-i8y
    @PeterJames-i8y หลายเดือนก่อน

    Amenewo ndiye ochewa a mcp mungawachitire chabwino chotani amabweza chipongwe

  • @smikemw7
    @smikemw7 หลายเดือนก่อน +2

    wausilu uyu akha manyi kkkkkkkkk appreciate 🙏 ndazikonda

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 หลายเดือนก่อน

    AKULU NDAKUVERANI CHISONI KWAMBILI MWAPULUMUKA KOMA MUSAYEREKEZE KUKUPUSITSANI KUTI WINA AKUYITANENISO AI MUTHERA KU MCP MWAVA SAMALANI MOYO ATALA NKHANI MUSAMANYENGEDWE NDI NDALAMAZI MOYO NFIWABWINO

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga หลายเดือนก่อน +1

    Akanachipambadza😂😂😂Mesa yekha amati amawadziwa nde amakataniko😅😅😅😅

  • @IanAllstal
    @IanAllstal หลายเดือนก่อน +2

    Timukhululupire Amenei ? Amatelo akafuna kukupanga zinthu.Nanga mwadya zingati

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 หลายเดือนก่อน +1

    😢😂😢😂😢😂😢 Akulu mwalira ngati Mkazi wosiyidwa Chibwezi mpaka wuwuwuwuwuwu 😂😂😂😂😂😂 Pamenepa Phanzi mthaandize thawani sipokhala.

  • @alexanderlinzi2532
    @alexanderlinzi2532 หลายเดือนก่อน

    PAJA UNANYOZA ASILAMU KUTI UTHETSA CHISILAMU MDZIKO MUNO. NDIYE LERO UKUTI BWANJI?

  • @AbrahamTembo-z5k
    @AbrahamTembo-z5k หลายเดือนก่อน

    TULUKANI BRO, MWINA NDI MWAYI WANU. AWOWO SAFUNA CHILUNGAMO. Munthu kuyankhula chilungamo walakwitsa? Vuto la ndale za chi Malawi ndilomweli. ZIPANI ZONSE MUNO ZIMATERO NDITHU, KAYA ZINAKHALA BWANJI?

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba หลายเดือนก่อน

    Iweo ndi kape alipo anatenga Colgate kumasuka nkamwa mwa mkango akutizimule kumene athu mukuzuzisa ziko lino ndinu tikutibulaso tokha akakusiya azakowo

  • @YusufAjiruh-c5q
    @YusufAjiruh-c5q หลายเดือนก่อน +2

    Kd inu simukaziwa kuti mcp ndi manyi zedi muziona😅😅😅

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga หลายเดือนก่อน

    sasamba lwe usatiuze nyasi ukufuna umve chani kwa malawi

  • @trickermussa472
    @trickermussa472 หลายเดือนก่อน

    Musatinyase phanani komko zanu izo

  • @user-fd7fg1bx4y
    @user-fd7fg1bx4y หลายเดือนก่อน

    ndimaona ngati ndiwe dolo koma aaaaaaah za ziiiiiii

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o หลายเดือนก่อน

    Takulandiran sunganimoyo,, masewera ndi mcp kkkkkkk

  • @MphatsoPemba
    @MphatsoPemba หลายเดือนก่อน

    Akuchitani bwino kuti muziwe fisi saweta.

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน

    Musamuvere chisoni mkuluyu amayerekedwa kumayakhula motumbwakuopsedza azipani dzina kuti asacite mademo kulilongwe akanakutibula kukupweteka zikanatisangalatsa chisiru iwe eti manyiiiii ako

  • @SinyoroMoyo
    @SinyoroMoyo หลายเดือนก่อน

    Ayitu ife yayi takukana khala komko

  • @JonathanMatiki
    @JonathanMatiki หลายเดือนก่อน

    Basi sungani moyo wanu malume kkkkk

  • @HaroonMaundala-lg5lg
    @HaroonMaundala-lg5lg หลายเดือนก่อน

    Pamtumbo pako. Osamangopita kunyumba kwako bwanji? Panyo pako

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 หลายเดือนก่อน

    Amen asungani

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo หลายเดือนก่อน +1

    Tulukani ma young generation ku MCP mutherako 😢

  • @FrancisJumbe-zj4ue
    @FrancisJumbe-zj4ue หลายเดือนก่อน +2

    Muphana agalu Inu kkkkkkkkk panyero pano

  • @FelixChipoya
    @FelixChipoya หลายเดือนก่อน +1

    Akufuna ndalama awa tangowapani1mta athese mavuto. Kulira mkkkkkkkk sono akazi anu nkumati akaona nkumati adadi akulira

  • @MaryJefry
    @MaryJefry หลายเดือนก่อน

    Muthanako choncho 😂😂 chipani chokupha

  • @AishaChipande
    @AishaChipande หลายเดือนก่อน

    Achimwene gwilani ntchito politics I'd zikhale chinthu chomslixila pa moyo wabwino

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 หลายเดือนก่อน +1

    MCP ndikachani kut uzilira galu iwe😊😊😊😊

  • @CharlesKanyumba
    @CharlesKanyumba หลายเดือนก่อน

    Iwe umayesa ndi chipani chabwino

  • @SueWahna
    @SueWahna หลายเดือนก่อน

    Walira mokweza mwana mamuna pofikizana size iyiyi mtimad wang'ambika azipan zina khululukan ndithu wasweka mtima munthuyi wavomereza kulakwa kwake😊

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 หลายเดือนก่อน +1

    Payanani uko..Ndinu Akupha Agalu Inu...How is what you are saying helping Malawi mxaa

  • @user-fy5lw8vk9k
    @user-fy5lw8vk9k หลายเดือนก่อน

    Tchimo limabala ifa...Lapani Achimwene Kondani Mulungu osati chipani..Cjisomo chakugwerani..

  • @DisireDokotala
    @DisireDokotala หลายเดือนก่อน

    Mudya ndithu

  • @gabrielinjesi4460
    @gabrielinjesi4460 หลายเดือนก่อน

    U know each other

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 หลายเดือนก่อน +1

    Mukapanga masewela mumalizana mcp ndi chipan chakupha simukumva

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน +1

    Osamubvela ameneyi ndi odwala,iye amafunako chiyani akumatukwana ku ma Media?anganamupha kumene.angofuna, kuchuka,maso anthu ali pa utm UDF afford and dpp.matama,akuluwa ndi amatama, ndalama zache ziti,wachamba ameneyo.

  • @ruzuwanmoyenda23
    @ruzuwanmoyenda23 หลายเดือนก่อน +1

    Nde uzimukumba?😊

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o หลายเดือนก่อน

    Sunganimoyo kkkk kkk uli booo

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂 ndinokhanokha kuthanakuthana basi iiiiii

  • @chachaamoah3592
    @chachaamoah3592 หลายเดือนก่อน

    Mwayamba kumenyanatu nokha nokha simunati. Khalani konko kwa bambo wanu ng'ona yodya anthuyo chakwera.

  • @user-mq2or1lz8h
    @user-mq2or1lz8h หลายเดือนก่อน

    I hope uchila pompano 😂😂😂😂😂

  • @user-dy5bj9ck5e
    @user-dy5bj9ck5e หลายเดือนก่อน +1

    Zikanakhala bwino ndiwe wamanyi kwabasi pamtumbo pako mesa ndiwe dolo

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 หลายเดือนก่อน

    Samalani man MCP ikupwetekani komanso mukapanga masewera akuphani

  • @HarveynsonthiNsonthi-u4n
    @HarveynsonthiNsonthi-u4n หลายเดือนก่อน

    Ukanati udzilire wekha ubale wake ndi mulungu ndiotani osati zomwe wachita apazi wandinyansa iwe galu kobasi

  • @GilbertKuchipinda
    @GilbertKuchipinda หลายเดือนก่อน

    Ukufuna kum'bela ndani?

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 หลายเดือนก่อน

    Propaganda yachabe iyi guyz, usatitenge a opposition ife ngati opusa wamvaa, akutumawo awuponda phwanga, DPP, UDF, UTM, AFFORD musamulore uyu please, wachita kutumidwa, muziwina malilidwe akewo ochita kulira ngati kamwana ka imbwa 🐕🐕 kaa

    • @FelixKachera-je4yk
      @FelixKachera-je4yk หลายเดือนก่อน

      akuluwa ndi propaganda akunenai aaaa nde akuti samadziwa zimene amapanga?🤔🤔 okay any way paja ndeu yaeni savulira jeket

  • @AndrewMagombo
    @AndrewMagombo หลายเดือนก่อน

    Akt nthima wake Wang,Ambika

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 หลายเดือนก่อน

    Mwaona akulu bola isakhale ndale

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e หลายเดือนก่อน

    Mudyana

  • @WonderfulOdala
    @WonderfulOdala หลายเดือนก่อน

    Wanyatu anakakuponda umandinyasa

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s หลายเดือนก่อน

    Uyu ndiofoila wamisala uyu

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu หลายเดือนก่อน

    Zochitsilu zopusa ndiye ife chikutkhudza ndichani? Dziphanani ife tili pamalilo a chilima

  • @YusufAjiruh-c5q
    @YusufAjiruh-c5q หลายเดือนก่อน +1

    Ndiy inu maganizo anu ali pati?😅😅

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di หลายเดือนก่อน

    A dpp audf autm a afford musamalenaye ameneyo musatengeke mutola njaoka andale ndinu an' dede

  • @user-rd8vw1pc4b
    @user-rd8vw1pc4b หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo siunati

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x หลายเดือนก่อน

    Kkkk km kumeneko

  • @VioletMovella
    @VioletMovella หลายเดือนก่อน

    Awawa nde atiphadi😢

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 หลายเดือนก่อน

    Ukunama ayise , kumene ukulowelera ine ndikuziwapo . Khalani ndi MCP yakoyo

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa หลายเดือนก่อน +1

    Mcp ndi mbava Komatsu kupha anthu

  • @AfricanKingdom-uv1qb
    @AfricanKingdom-uv1qb หลายเดือนก่อน

    😂😂😂 mulungu àmba kukukathani

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 หลายเดือนก่อน

    What goes up comes down, you were arrogant telling Malawians not to protest in LILONGWE and you thought that the whole world owes you a living, remember you reap as you sow. You are harv what you planted.

  • @RonaldodalitigerSpencerDaliRic
    @RonaldodalitigerSpencerDaliRic หลายเดือนก่อน

    Nkhosa yosochera yapezeka,,,ndee funso langa ndilakut muli kmwekobe ...?

  • @user-ul5hh3cz8z
    @user-ul5hh3cz8z หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk woyikonda anayithawa .koma chachikhulu wamudziwa pano.

  • @FilbertKomba-fi2nl
    @FilbertKomba-fi2nl หลายเดือนก่อน +1

    Za kubanja kwanu ife zisatikuze amwene musaipitse mbili ya mcp

  • @TisunganeNkhoma
    @TisunganeNkhoma หลายเดือนก่อน

    Lchenjela

  • @user-pe2tu1ip3v
    @user-pe2tu1ip3v หลายเดือนก่อน

    Yeah wuli be tchito mapwala amako iweyo ngakhale akanakuthimitsa

  • @JamesKhengemussa-t1d
    @JamesKhengemussa-t1d หลายเดือนก่อน

    Kuli kanthu this is mcp brother

  • @JosterNgalawa
    @JosterNgalawa หลายเดือนก่อน

    Iwe pita komweko ku MCP ko akutuma, tikuziwa kale, ma pran ako sagwila

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 หลายเดือนก่อน +1

    Isandithere data langa nkhani yakoyi pankholo pako

  • @LiamTennessee
    @LiamTennessee หลายเดือนก่อน

    No you love Evil thats period

  • @JoshBranquinho
    @JoshBranquinho หลายเดือนก่อน

    Zaziiii akuthibule wazindikila mochedwa

  • @FainessMwanza
    @FainessMwanza หลายเดือนก่อน

    Moti m paka pano simuziwabe kuti mcp ndiyapha

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of หลายเดือนก่อน

    Iweyo kalowe Ku utm Ku MCP sitifuna anthu azibwanatu ai ndi we chisilu

  • @jameskimu3961
    @jameskimu3961 หลายเดือนก่อน +1

    Wamisala iwe

  • @LiamTennessee
    @LiamTennessee หลายเดือนก่อน

    Now that God has rescued you mkamwa mwa Ng'ona think twice

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 หลายเดือนก่อน

    Achitsilu inu Bola akanakuphani tikanasangalala a Thailand kuwili inu

  • @LongiMtimabii
    @LongiMtimabii หลายเดือนก่อน

    Galu iwe

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di หลายเดือนก่อน

    Ukufuna ulowe kuchipano china iwe akutuma kuti udzawonongeko

  • @alexanderlinzi2532
    @alexanderlinzi2532 หลายเดือนก่อน

    UPEPESENSO ASILAMU

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm หลายเดือนก่อน

    Muyamike akusiya amoyo akolo

  • @user-qs2tx7wt6g
    @user-qs2tx7wt6g หลายเดือนก่อน

    Bodza iliiii

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo หลายเดือนก่อน

    Siyani ndale

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di หลายเดือนก่อน

    Chipaniicho ndichokupha iwenso uli mugululo zakoizo

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm หลายเดือนก่อน

    A brother ndi achisilu

  • @jameskimu3961
    @jameskimu3961 หลายเดือนก่อน +1

    Nde titani

  • @KumbukaniKafatia-cd2hq
    @KumbukaniKafatia-cd2hq หลายเดือนก่อน +1

    Judas!

  • @user-pn7cj9hb3t
    @user-pn7cj9hb3t หลายเดือนก่อน

    Simudapambane zisankho ayi

  • @elbeys783
    @elbeys783 หลายเดือนก่อน

    uli ndi thawi dala iwe

  • @YughozMaonga-ft2ny
    @YughozMaonga-ft2ny หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @AndrewMagombo
    @AndrewMagombo หลายเดือนก่อน

    Mphanani Ng,Ona zonkha zonkho

  • @user-bb5iy7ry5h
    @user-bb5iy7ry5h หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AishaChipande
    @AishaChipande หลายเดือนก่อน

    Shem sorry brother

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkk zaugaki

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef หลายเดือนก่อน

    V😂😂

  • @GenitojosebingalaJosebingala
    @GenitojosebingalaJosebingala หลายเดือนก่อน

    😂

  • @CharlesFalakeza
    @CharlesFalakeza หลายเดือนก่อน

    Eya amakupha ndinzako kumene Chilima anamulakwila chani Chakwera zabwino zonse anamuchitila zija mphoto yokampatsa ikhala imfa

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera หลายเดือนก่อน

    You have been castigating people who were talking about MCP.

  • @malawililongwe
    @malawililongwe หลายเดือนก่อน +1

    Uwu ndi mchenga mu mpunga