Limpopo watulukilaso Ntanyiwa kudzathila nchenga mu mpunga wa boma kuwavetsa kuwawa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 1 ก.ค. 2024

ความคิดเห็น • 29

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa 12 วันที่ผ่านมา +5

    Alemba mmadzi amenewo olo akamapereka R2000 ifekuno ku Johannesburg sitingachite za kanunduzo. Azibale athu kumalawiko akuvutika kaamba ka boma lonunkha mcp

    • @user-re7fo3be2z
      @user-re7fo3be2z 12 วันที่ผ่านมา

      Ndipo tikumva pain heavy

  • @SymonYohane-i5q
    @SymonYohane-i5q 12 วันที่ผ่านมา +2

    ❤🎉 mbambande iweyo umakwana ntanyiwa keep it up

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 8 วันที่ผ่านมา

    Tell them Comrade

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 12 วันที่ผ่านมา +1

    Tipha kuno 💪💪💪

  • @HafsaAbwanali
    @HafsaAbwanali 12 วันที่ผ่านมา +2

    Uthengau upite kwa brother nthanyiwa auze boma la ku South Africa ko kuti dziko lawomo mwalowa zifwamba zochokera Ku malawi zabwera ndiupandu. Nde muziwauza madera. Omwe Ali azifwambawo apolice awangire akaponye chakulinderako azikalima masamba tizigula mashop mu asazatulukenso chifukwa akutengela phamvu kumanja powaona kupusa eni dziko nde anthanyiwa musankhale nchisoni ndi crocodile pple agwidwe basi komweko uthengau ugwirisireni ntchito kuti akamangidwa ena atengereppo phunziro

    • @user-re7fo3be2z
      @user-re7fo3be2z 12 วันที่ผ่านมา

      Ndipo azikalimadi masamba kunoko asabwele

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 11 วันที่ผ่านมา

    🤔big up big♥️💪💪💪💪✊✊✊✊✊✊🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z 12 วันที่ผ่านมา

    Tanguwawombela komweko afele komweko akuwononga ndalama za amalawi

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y 12 วันที่ผ่านมา +1

    Anthu awa asatidanitse amphawi ife ndi dziko la south Africa mu south Africa ndikumene tikupezelako thandizo lathu tikumakwanisa kusamalila makolo ndi ana kumamiziku ndiye inu aboma chepesani za chibwanazo muzipanga ku mudzi Koko kuno ayi tikupondani tikakuziwa tikufinyani ndithu akunkuyu samalani chifukwa mwatulusa maso ndi chipani chanu mutha kufa ngati nkhandwe wokuba nkhuku musamale koma

  • @LouisChipanda-ux9dz
    @LouisChipanda-ux9dz 11 วันที่ผ่านมา

    Akunama amenewo tikangowadziwa akumana ndi ma tsotsi kunoku

  • @user-ml8lk9dr7t
    @user-ml8lk9dr7t 12 วันที่ผ่านมา

    Zilipo njira zina zamwamuna zooneka zoongoka koma tsiliziro ake ndi imfa anzathu tsogolo palibe munthu ukamafa umayamba kugontha mkutu ndizo zikuchitikazi

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 12 วันที่ผ่านมา

    Shaaaaa km ndaramadi iripaminga et

  • @henrynsiku2108
    @henrynsiku2108 12 วันที่ผ่านมา +2

    Tiwagwira kuno ayerekeze kuyambiya kuno Pretoria comrade #MCP must gooooo!!!!!!!

  • @DysonNakhaphe-bo4dl
    @DysonNakhaphe-bo4dl 11 วันที่ผ่านมา

    Man mukutiyimilila and tikudziwa zambili kuzela mwa inu pitilizani

  • @ThompsonMakwakwa
    @ThompsonMakwakwa 10 วันที่ผ่านมา

    Awomberedwako chabe kuno!! Asamaletu other wise apita opanda moyo!!

  • @KennethKilembe-ex5ro
    @KennethKilembe-ex5ro 12 วันที่ผ่านมา

    Great ntanyiwa

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x 12 วันที่ผ่านมา

    Ayitu Mr Ntanyiwa inuyo simugwidwa mulungu sakulola anyapapi amenewa kut akwanilitse zofuna zawo nthawi yawo yoyaluka yakwana mudzingowayang'ana

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa 12 วันที่ผ่านมา +3

    Mr Ntanyiwa mmatiimirira monga ife amalawi omwe tiri panchombo penipeni pa Johannesburg tikukupemphanikuti tazizutseni zipani zosutsa kuti zizipanga zochirimika pa ground kuti boma lokuphali lichoke

  • @thondoyaenterprise3795
    @thondoyaenterprise3795 9 วันที่ผ่านมา

    Mkhuku imeneyi mukiyifuna ?
    Ndikuyidziwa pamene imakhala.
    Ndikakuwonetani pamene imakhala

  • @vincentbarnes5872
    @vincentbarnes5872 12 วันที่ผ่านมา +1

    DPP sikuti inalinso ya bwino mulakwisa kwabasi. Utsogoleri wa DPP kapena MCP sitikuufuna ata pang’ono koma utsogoleri wa masomphenya a Dr Saulos Klaus Chilima

    • @AbrahamTembo-z5k
      @AbrahamTembo-z5k 12 วันที่ผ่านมา

      You are one of the wise, just & intelligent people.

  • @user-dh1oi8mb4v
    @user-dh1oi8mb4v 12 วันที่ผ่านมา

    Ndipo sitikwanitsa achepaaa

  • @LindaMakalani
    @LindaMakalani 12 วันที่ผ่านมา

    Palibe chochitika mulungu ali nanu cholinga

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 12 วันที่ผ่านมา

    AWAWA GUYS AKANGOFIKA MU JONZ MUNO AKAMABWERERA ABWERERE ATASINZINA , ASABWERERE AMOYO IFE TAGWIRIZANA NDI MA ETA TIKANGOWAPEZA TIKUWAVEKA MA TAYALA NKUOTCHA TIKANENA KU POLICE KUTI NDI ZIGAWENGA ZACHOKA KU MALAWI KUFUNA KUDZASOKONEZA DZIKO LINO, ASIYENI A BWERE TIKUMANA KONKUNO

  • @user-jb5hr4rz2s
    @user-jb5hr4rz2s 12 วันที่ผ่านมา

    Timakondwera nanu a bwana

  • @elizasingano
    @elizasingano 12 วันที่ผ่านมา

    Kod anthu akunyamuka ku malawiwo ayenda pa bas ? Ngat ili bus tiziwisen kut ndi bus yanji

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 12 วันที่ผ่านมา

    Mr Ntanyiwa Kodi ifeso timaika ma comment zikhale ng'oma atigwilaso😢😢😢