I just like the way adult women are waking up today. What they have missed in there youth age they can achieve it even in time where they are no longer hot. The voice of abit Nanjere is nice. Just improve on both audio and video production. 60 out of 100
I thought it's only JETU is the only one keeping the fire burning in MW kansi there is another one Malawians you doing in different style we have not yet experienced elder artists in Zambia otherwise great work keep the 🔥🔥🔥🔥🔥
Jetu came with force.... And is loved by all. Its not hate but there was supposed to be a different style, different directing not copying jetu, otherwise ITS A NO FROM ME. ONLY THAT UKAONA NZAKO AKIGULITSA TOMATO UMAYAMBA NAWO KUMAYESA MWAYI WANZAKO NDI WAKO
Nice one macten keep it up may God bless your music
Good start keep it up Abiti Naje
Pang'ono ndi pang'ono tsokonobwe anatha mtunda ndikundupha ❤️
Pali zambiri zofunika kukoza
Komabe the song is nice
The best part of you is, the ability to start. Keep it up one day u will sing with munthu wamkulu kwambiri jetu😂😂😂
Wow keep fire burning
Keep it up, one step at a time. You will rich there
Sinapyeeee kweni kweni komabe popeza amati ladies first
Keep pushing jetu naye anayamba mkunyozedwa ,, AMalawi amatero osafooka ai
Ndipo zoona 🤣
Kkkk najere uli boh keep the fire burning
All the best Abiti. Atleast you took a chance.👏🏻❤️🌹👆God give you what your heart desires.❤️👏🏻🤗😘
I just like the way adult women are waking up today. What they have missed in there youth age they can achieve it even in time where they are no longer hot. The voice of abit Nanjere is nice. Just improve on both audio and video production. 60 out of 100
I just like the variety in music industry
Jetu fans let's gather here and tisake hahaha 🤣🤣🤣
Yes kkkkkk
❤❤
Aaaha
Hahaha
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
💥💥💥💥💥atsikana wo nde akudukat
😂😂😂😂😂😂ndaseka mokuwa
Komatu .....mhuuu ndye mwat message yanji 😅😅😅🤣🤣
Ndayikonda good start mami osavela za athu ndwe dolo olo jetu athu akamunena chocho❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
I thought it's only JETU is the only one keeping the fire burning in MW kansi there is another one Malawians you doing in different style we have not yet experienced elder artists in Zambia otherwise great work keep the 🔥🔥🔥🔥🔥
ABITI NAJERE nyimbo mayasi apatseni malo azikapanga ma zewero ndi achina jokes 🙏🙏🙏🙏🙏🇲🇼
Exactly
exactly
This is crazy azimayi akuluakulu , satana akulamulila
mwaza mwa upcoming mwina muyesenso
Keep up the good work 💕💕💕
Mmmmmmm mwatithela mbando eeasshe!!!!! 😢😮
Nyimbo ndiyabwino because mayiyu wayamba kumene
Just because wina akupanga ndekuti winanso sangapange iyayi. Aliyense azipanga zofunza zake, ine I'm here to support women! Tiye nayo Naje
Me too am supporting anaje
Problem is abela Jetu the music production
Kumalawi nkonkoma😂😂🎉🎉🎉
Never Give up, my wanga one day u gonna be like ajutu
Style like Jetu aaaaah fotseki we love Jetu ife❤ 4:55 4:58
The acting is super.😅🤗👏🏻Lets go Abiti.🤗👏🏻🤗👏🏻
I love the way dancers are collaborating but voice need thoroughly training
Kuonera kokha ndi support yomwe.basi tiyeni nazo mwabwera basi. All the best anajere
production yi ndi mbola koma concept ndiyaboo eee tiona zinthu 😄😄😄😄😄
Keep it up najere amalawi tiyeni tidzisapotana eeeeee
keep it up abit najere,Malawi is changing by bringing such people in music industry
All in all am still in love with JETUU❤❤❤
Start your style. Not copying
Beautiful
Better than nyimbo zonse za Jay Jay cee
Keep it up!!!
Kambisalilano wen weni tim jetu😂😂😂😂 akalemba walemba mulungu 😊
Limbikilani Mayi zitheka
Much love from here♥️
Okay chabwino
What is the title of the movie pls and which country is this?
Nyimbo ilibwino konzani mavinidwe poti abiti satha kuvina mukanapewa kuchulukitsa kuvinitsa iwowo komaso pezani achinyamata oziwa kuvina amapiano mma school.
Keep it up abiti najere🔥🔥🔥
Wayiponda najele
Izi ndiye ayi yambani zina mayi
Kee up the good work
Bwanji mukuimba bit ya ajetu mwatan nanu osapanga zanu bwanji
Zoimba zake zimenez aaaaaa kmso mimba za masese angt zimenez akutan nazo ayamb kuvay gym chimimbacho chiphwe
Akhwaka pitilizani wezwez koma audio ndiyofunika kukonza. Kumaimvera mwachidwi before shooting a video
Voice yabwino km yofunika youth kwaya
Nyimboyi inakankhala yachipani bwez itakoma kwambili
Good voice than jetu
Sewelo kodi?? Anyway nice
Mwayamba bwinotu mpaka kumuposa Q mishu 😅
Mimbayo bwanj mwna akudwala
Ineso ndadabwa nawo a najere chimimbacho eti
😂😂😂
Mwayamba bwino
Ali ndi mawu abwino
Love this 😂
Muli Nd tc😮hito 2:39
Kut mufike pa 😮jetu 2:56
Km munakapeza style yanu osati ya jetu
anthu ake sali serious they are shy and akukhalangati akufuna kuseka eti
Osanama Guys Kunena Moopa mulungu
nyimboyi nde yonyasa kwambiri
ilibe tsogolo 🙌🏾
Jetu came with force.... And is loved by all. Its not hate but there was supposed to be a different style, different directing not copying jetu, otherwise ITS A NO FROM ME.
ONLY THAT UKAONA NZAKO AKIGULITSA TOMATO UMAYAMBA NAWO KUMAYESA MWAYI WANZAKO NDI WAKO
Love the beat
Inspired by Jetu go our mamas
I am just vibing to the mimba dance 😉😉
Ndpo😂😂
Nice ❤
Wokamenya ndewu amavala magalasi😂😂😂😂
Upcoming uja ndi uyu jetu sanafkire pamenepo ayi try again 😂😂😂😂😂
Wabwera munthawi yachabe
Jetu ndi jetu
100k afika
Zoona
Ngati ili mimba yamwana mukanachila kaye mai kenaka kumapitiliza bwino fukwa ndiye ummmmm
Komas producer wake uti abatulutsa nyimbo imeney. Khulupilil nd supporter wa MAN U ameney
Chakwaza ija simasewela
Iwe najere upange style yako🙆...zobelena nd jetu waife ayi😅😅😅
Iweo uziyimba trap or Hip Hop 😂😂
Fire Nanjere 🔥🔥🔥🔥🔥 don't give up
Fire ting 🔥🤞😂
More dire babe we are with you
Wabela jetuuuuuuu😂😂😂😂😂😂😂
Zilibwino limbikiran anaje
kumalawi mwasowa zochita yet kkkkkkkkkkkkkkk
Very good zatheka❤
Bola mwatchuka enafe tithela pompa
Zaziii
Ayi,no comment poti ma comment anthu mwaponya kale
Zilibwino Abiti Nagele our women are empowered
Congrats 👏, ad time goes on there will be an improvement, kmn scene yoyambilirayo, kms mau amene akuyankhayo akanawapanga zna nd zna kmn zosangalatsa
mupeze zina zochita pepani chimbali yanu . zamkutu
Employ another alternative koma za music muchedwa nazo mama
Mwati Amayi Awa Satamba 😳🥲🙂💀💀💀😂
Mene mumamunyoza JETU uja mumafuna izi? JETU uja ndi Boma palokha
Komabe wezwezi mawa zizatheka
Mukukakamìza zinthu. Musawapepelese akuluakulu wa
Eeeh chikuvinikatu ndazikonda ....work on it koma zayambabe bwino
kkkkkk indeed
Mwalandilidwa abiti najere tiyeni tipushe basi nthawi zonse chiyambi mchovuta mwamenya sound yabho osafooka ayi
Kom uyu ayi alibe fundo. Dolo ndi jetu 😂😂😂😂
Kkkkk koma kuchuka kuvutatu apa zida ndi mau zikupita kosiyana