ALEXIOUS KAMANGILA LIVE TODAY - WAJAMA YA UTM, SKC, THOM MPINGANJIRA, NORMAN CHISALE AND MORE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 93

  • @tiongegondwe7219
    @tiongegondwe7219 6 วันที่ผ่านมา +7

    I agree with you, I have been a victim of corrupt lawyers, they take your money and run away without helping, the so called senior councils

  • @EzekielWakudyanaye
    @EzekielWakudyanaye วันที่ผ่านมา +1

    You are doing amazing work.
    Justice delayed is justice denied!
    Keep the fire burning!

  • @ethelmkonkha6921
    @ethelmkonkha6921 6 วันที่ผ่านมา +2

    I like that qoute" Good people need to meet and discuss" because Evil people also meet to discuss their evil plans. Oh God bless our land of Malawi keep it a land of peace.

  • @LufeyoMlumbe
    @LufeyoMlumbe 6 วันที่ผ่านมา +1

    That's our men,can't wait to see you bcomin our chief of justice to take out this nyakanyaka in dis country, we salute you sir

  • @SolomonMumba-i5n
    @SolomonMumba-i5n 5 วันที่ผ่านมา

    I like your views coz you put them as they are. Big up grootman

  • @joabamathosi9356
    @joabamathosi9356 6 วันที่ผ่านมา +1

    Well done kamangira, you are an honest and brave man to lecture every one of us

  • @RheggieIssah
    @RheggieIssah 2 วันที่ผ่านมา

    Am proud of you. Keep it up.

  • @gracem-y8p
    @gracem-y8p 5 วันที่ผ่านมา +1

    Been watching this for the longest. Based on lived experiences, and when you hear this you wonder whats left of the country. It looks like there is competition to be the most corrupt and this goes all the way to ground level. Private individuals, all the way to the village, are now culturally corrupt. The question is, with this level of thiefocracy, who will turn things around?

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s 6 วันที่ผ่านมา +4

    Channel iyi ili bho❤❤

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev 6 วันที่ผ่านมา +1

    Iwe ndi munthu wankulu simply you are the best ❤❤❤

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 วันที่ผ่านมา +1

    One thing, Kamangira you should do is to choose a language. To present your this program.
    Zomayankhula chizungu ndi chichewa pena sizikumakhala bwino.

  • @nelsonarthurphiri9901
    @nelsonarthurphiri9901 วันที่ผ่านมา +1

    Wachamba iwe . U r more of Chikangawaism guard

  • @AlickMDayi
    @AlickMDayi 6 วันที่ผ่านมา +1

    We are be hide you brother AK keep up good work💪🏼💪🏼❤️

  • @geofrybanda4601
    @geofrybanda4601 6 วันที่ผ่านมา +1

    May God Almighty bless you, protect you and give you energy

  • @moffatbanda-p3z
    @moffatbanda-p3z 3 วันที่ผ่านมา

    Osapanga zachipani ai Imani mbali yanu ija ya judge corruption not kumati ine ndiwa mcp ai

  • @ENOKMAKONDI
    @ENOKMAKONDI 3 วันที่ผ่านมา

    Akulu palibe Angel padziko lapansi mukatelo muzinyenga nokha ndipo mwainu mulibe chilungamo izi ungoziziwa...

  • @UnjiunjiGeneral
    @UnjiunjiGeneral 6 วันที่ผ่านมา +1

    Mudzina la tate. La mwana ndi mzimu oyera. Amen

  • @mondivamaloya1683
    @mondivamaloya1683 2 วันที่ผ่านมา

    koma Malawi ngotembereredwa

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 วันที่ผ่านมา +1

    Government of the people for the thieves by the thieves😂😂❤❤ng'alula don't keep one in the under pit.. aliyese must be checked

  • @kondwanienock
    @kondwanienock 6 วันที่ผ่านมา

    True fighter osat ojiya,,kutchaya mbali zonse sizandale koma chilungamo basi

  • @Saeed-r3z
    @Saeed-r3z 6 วันที่ผ่านมา +1

    I igree with him coz chilima anali ndi katangale yooopya angakhale akanakhala Ali moyo sakanakalandira ulemu nziko muno LA malawi

  • @ErnestGwelema
    @ErnestGwelema 5 วันที่ผ่านมา

    What a genius lawyer 😅😅

  • @JoyceShaibb
    @JoyceShaibb 5 วันที่ผ่านมา

    God protect you ❤❤

  • @hi-profileltd
    @hi-profileltd 5 วันที่ผ่านมา

    poweful spealing bro

  • @AndrewKadammanja
    @AndrewKadammanja 6 วันที่ผ่านมา

    Ofcourse, kaya ukunena zoona za SKC, kmno szngatithandze chfukwa wakufa saimbidwa mulandu, and udalikut pot Chilima adali mu court? Munthu akapezeka olakwa pa milandu yakatangale chilango chake ndkuphedwa? Ndchfukwa chan munasankha kumupha? Mot onse akutibelawa tikuenera kudzawapha? Uyankhe zimenez Kamangila please 🙏

  • @JailosMwanza-c4j
    @JailosMwanza-c4j 6 วันที่ผ่านมา +5

    Aaaamuthuyi ndiwotaya mutu bas

  • @StevenMasiku-xe4zx
    @StevenMasiku-xe4zx 5 วันที่ผ่านมา +1

    You need to be sober so that you understand this man, otherwise uzingotukwana

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 6 วันที่ผ่านมา

    My brother please try to use chichewa when you are sharpening the eyes of vulnerable malawians chizungu munthu amene sanaphunzire ndibwino azimva nawo cos ndiamene amafinyidwa kwambiri if you use English ndi anthu ochepa kwambiri omwe angamakumvese komanso angamakutsate ndiochepa

  • @hi-profileltd
    @hi-profileltd 5 วันที่ผ่านมา

    big up boss

  • @macleanldzimkambani7773
    @macleanldzimkambani7773 5 วันที่ผ่านมา

    Rest in peace MSB sudzabweleraso😪😪😪

  • @funghiemw
    @funghiemw 5 วันที่ผ่านมา

    As evil people meet and discuss ways of doing evil to particular people or society, indeed good people should also meet, strategizing on how to do good. The world remains in trouble today, not because of the people who are actively committed to do evil, but rather because of the people who are tolerating evil.

  • @BenardChilemba-k8w
    @BenardChilemba-k8w 6 วันที่ผ่านมา +1

    Kuyakhula kopanda mantha ndikukondera uku....mbali zonse zikumanyika....anthu dola zawo zikumawateteza...osaopa

  • @MagieJames
    @MagieJames 6 วันที่ผ่านมา +2

    Iweyo ndwe wamisala kwambili wapatsidwa ndlama kukamba za munthu omwalira ndewe mbuli bwanji kusukulu nd kusukulu kunena zoti munthu sangakuyanohe osakamba zomwe akucita katangale mpakana kugulisa nyanja nd mapiri masaya otupawo ngt walumidwa nd mamvu ngalu iwe mbuzi anthu asiya kukukonda wasowa zokamba nyani jama ina tikondabe kabambeyo ngakhale uzinyera mabozawo

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 6 วันที่ผ่านมา

      Inu ndinu mbuli kwambiri ku school simunapite eti

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 5 วันที่ผ่านมา

      Mwanyozatu popeza akamba za chipani chanu 😂😂😂😂😂

  • @AWARIBLACK
    @AWARIBLACK 6 วันที่ผ่านมา +3

    Akamangila ziwani kuti athu omwe achuluka kusukuru sanapite ndye ziyesesan kuti athu akumuzi omwe akumakusatilan azivanawo chifukwa mukusatidwa ndiathu ambili

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 วันที่ผ่านมา

    Even amene anafa ul😂ula, asazitenge ngati Iwo anali ayera mutima mbavwa ndi mbavwa If chilima was sizina nitole yankhula, ngati Chakwera ndi mbava yankhula Yaya bingo , Peter Joyce Banda ndi muluzi wonse aponye poyera tiziwe chowonadi... chilima usamuwope Poti dzina lake ndi Champaign wa UTM... Ulula chilichonse

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 6 วันที่ผ่านมา +2

    Ukajama yimeneyi anthuwa Ali moyo

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 6 วันที่ผ่านมา

    We are suffering because of rich people
    Tiyeni tapase mphuma amkulu amkulu

  • @StevenMasiku-xe4zx
    @StevenMasiku-xe4zx 5 วันที่ผ่านมา

    Muuzeni azikhala consistent polankhula osati kuiyamba iyi kuphatikiza zina

  • @chawanangwamkandawire5850
    @chawanangwamkandawire5850 6 วันที่ผ่านมา

    Za ndale zili ngati za chipembezo, gulu iliyonse imakondwa kukamba zolakwika za ma gulu ena osati zawo.

  • @laurentbutao4084
    @laurentbutao4084 6 วันที่ผ่านมา

    Umazaona ngati wabereka mwana,osadziwa wabereka chinthochi.

  • @markanthony5402
    @markanthony5402 6 วันที่ผ่านมา

    Its true kuti chilima naye anali wakuba ndipo ine i said kuti chilima sadakakhala president wabwino ayi komabe a MCP anamupha zomvetsa chisoni

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 5 วันที่ผ่านมา

    Ndimankonda uyu koma zonena munthu oti anamwalira ayi apa pokha akulakwa munthu wakufa sakamba nkhani tiyeni tizinena amene ali moyo kuti ngati kuli kukhamba nkhani tikambe ndi amenewo or kayima pa khothi zitheka koma munthu wakufammmmmm kulakwan

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 5 วันที่ผ่านมา

    Zuto ndikochokera kwawo adamphunzitsa kutukwana ndiye kudya kwawo ,ana asatana kwaiwo chanzeru ndikutukwana basi agaru

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 6 วันที่ผ่านมา

    Ndizowona zoti chilima adali wakuba koma sada mcp sida ka mumpa ayiiii

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 5 วันที่ผ่านมา

    Mbuli kwawo mkutukwana ndi mabodza basi

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 6 วันที่ผ่านมา +1

    Dzikamba za anthu omwe Ali moyo coz izo or mutero munthuyo anamwalira

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 6 วันที่ผ่านมา

    I like this guy

  • @ethelmkonkha6921
    @ethelmkonkha6921 6 วันที่ผ่านมา

    God bless Malawi

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 6 วันที่ผ่านมา +1

    ZOONADI UFULU WA ANTHU OKUBA THE PRESIDENCY AND THE CABINET MINISYERS AND MT THÒMPINGANJIRA ETC..MAKING MALAWI NATION AN ABOMINATIÒN BEFORE GOD

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 6 วันที่ผ่านมา

    Ndilibe nazo ntchito kuti Chilima kaya muti anali wakatangale, koma munthu uja potential ya utsogoleri adali nayo and zolankhulazotu singandibwenze mmbuyoooooo
    Ine vote for DK basi

  • @WilliamBanda-rw7yw
    @WilliamBanda-rw7yw 6 วันที่ผ่านมา

    Akamangira ndimakonda kukuvetserani please ngati muli ndizithu n ndiwumboni wake please just take them kumabwaro amirandu tikuphuzira zambiri from u tikufuna tive kuti ena mulinawo kumabwaro amilandi bcz kuchokera tsiku munayamba khanizi no one was arrested or anachotsedwa ganyu wake

  • @Hdsagdf-t1n
    @Hdsagdf-t1n 6 วันที่ผ่านมา +2

    Kung,alulesotu chipani cha makolo akocho akutuma et ukatelo wadya chi bamsi utm suithetsatu wachepa iweyo

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 6 วันที่ผ่านมา

    Nick chakwera zoonadi afufuzidwe

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 6 วันที่ผ่านมา

    Let's work together brother

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 วันที่ผ่านมา

    Tili pambuyo payiwe❤ kamangila, we need new Malawi

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 6 วันที่ผ่านมา

    Where is Ralph Kasambala, Chilima, how corrupt or clever you can be, there is always your end and leave everything behind, shame!

  • @rosechapita3434
    @rosechapita3434 5 วันที่ผ่านมา

    Bwanji sunabwere anthuwa ali moyo umaopa chani. Udwalatu ndi dzindevu zako

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 วันที่ผ่านมา

    Mbava ndi mbava even they died must be talked.. chilima kamuzu and Bingo please tiwuze kodi anali woyera or mbava?
    Chilima was thief but his courageous was brilliant...koma very thief that's why he was close to thief lawyer kasambala

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 5 วันที่ผ่านมา

    Akamangira tithandizeni pankhani ikumvekai yanyajai zoti talandidwa ena akuti lagulisidwa komanso phiri sindikudxiwa kuti ndphiri lakeliti popeza ndimphekesera chabe ngati zitati ndizoonadi tingatani kuti zinthuzi zibwezedwe manja mwa amalawi ngati dziko tingaziyendese bwanji?Popeza kulingati kagulu ka anthu ochepa abera dziko imene ndilaanthu ambiri chonde tabwerani ndinkhaniyi mutiunikire

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 6 วันที่ผ่านมา

    Mpamtumbo Pako ndithu kare loseri umatan kuyakhula yachilima pano anapita uziti chani panyero pa omwe anakuberekawo

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 6 วันที่ผ่านมา +1

    M'malo moti uzikamba zaanthu amene akupanga katangale pakali pano your too busy kukamba zoipa zamunthu amene kunja kuno kulibe, sangayankhe kalikonse kaizi, sadzaonwkanso kunja kuno, misonzi ikanali mmaso ku family yake, tatha miyezi ingati chimwalilireni iyeyo? Khalani ndi umunthu man, kulankhula zaChilima oti kulibeko, apapa mwandinyasaaaa man

    • @brightben3984
      @brightben3984 4 วันที่ผ่านมา

      Justice ilibe chisoni... Justice simafa chifukwa wopanga injustice wafa aiii... His wrong doings are going to answer for him cuz his wrong doings are still alive.. Justice should save us

  • @gomezthera535
    @gomezthera535 6 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤

  • @DavidMalewa
    @DavidMalewa 6 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅 mng'aluli tiye nawo andale akutitora

  • @EmmanuelSikwese
    @EmmanuelSikwese 5 วันที่ผ่านมา

    Kodi inu izi mukubweretsa lero izi nthawi yoseyi unali kutiko? Before the death of late SKC?? Mupindula nazo chani lero?? Mufuna kuchuka kapena??

    • @brightben3984
      @brightben3984 5 วันที่ผ่านมา

      Hahaha 🤣😂 before Chilima escape from Justice he was already accused of the same cases ndee osadabwa ayii all these were already there... Phindu la zonsezi is about Justice... Munthu wamzeru amadziwa kut chilungamo sichimafa even munthu olakwira chilungamo yo atafa... Thank you very much

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 5 วันที่ผ่านมา

    ❤😂😂

  • @KelvinPhiri-z9d
    @KelvinPhiri-z9d 6 วันที่ผ่านมา

    Musamayakhule zamunthu omwalira chifukwa sangayakhe olomutapita kukhot sazayankha

  • @ManzyNgoleka
    @ManzyNgoleka 5 วันที่ผ่านมา

    Inu mumatikankhulira nkhani zolimbisa ntima km nkhani iyiyi olo saulosiyo atakhara kuti ankapanga zonse mukunenazi km sikupanga sense clz munthuyu adafa kale kale,mukutiuza kuti mutha kumutengeraso kukhothi?,, munthawi ino aaaa nkulu ndizoona kuti sugwedezeka ndizokamba zaanthu km kukamba zamunthu okufa zitha kupeleka chithunzi thunzi choti mmutumo penapake sizikuyenda

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 6 วันที่ผ่านมา

    Iweyo nchimachine

  • @Ayanali-cr4vy
    @Ayanali-cr4vy 6 วันที่ผ่านมา

    Chilima sanali wabwino olo pang'ono
    Kumbukirani wamzeru osati wandale

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 6 วันที่ผ่านมา

    eeeeeee uyuyu apweteka gulu!!!! kodi mpakaso ankafuna kuphedwa!!!! eeee koma ziliko

  • @FaithGondwemaomba-bz6nt
    @FaithGondwemaomba-bz6nt 6 วันที่ผ่านมา +1

    But the lips and sound mmmmm

    • @amtvmw
      @amtvmw  6 วันที่ผ่านมา +1

      Might be technical error we noted that too in the middle of the video.

  • @StarfordKAMOTO
    @StarfordKAMOTO 6 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk.
    Akulu inu aaazowonadi

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 6 วันที่ผ่านมา

    MALAWI NATION TO SHUT UP AFTER THE BRIBERY FROM.

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 6 วันที่ผ่านมา +1

    Amey🙏🙏

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 6 วันที่ผ่านมา

    Hiiii galu ndalama hiku baya kape

  • @MfuneExwalu
    @MfuneExwalu 6 วันที่ผ่านมา

    Useless,,man ndikakutenga ngati was zeru koma out box enieni , unali kuti thawi yomwe anali wamoyo ,amayendela kukhoti uko more than some days , mpaka kufika komupha ,, siguli lake ndinu , choncho muziti zikoli litukuka ,kifuna kunchuka chani, mvuto tili nalo mumalawi muno aliyetse akufuna aoneke ngati akudziziwa zithu ,eeee

  • @BashilNikisoni
    @BashilNikisoni วันที่ผ่านมา

    Bobut

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 6 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 5 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 4 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤

  • @GroupFortyfour
    @GroupFortyfour 4 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤