Inetu ndikudabwa ma prophet akungokamba za ndale basi asiya ntchito yamulungu akufuna zosangalatsa anthu, ndi kuntchuka basi samalani pogwira ntchito yamulungu.
Atsatu ndawi yophembela mulibe basi one day pa week ndaleso pomwepo kwanamisa anthu kuti mumalangulana ndimulungu koma kwiyo wamulungu ndimoto wosata samalani
Every prophecy imakhala ndi direction yake.. once you miss the direction, forget about the manifestation... It is not duty to say who is right or wrong , false or true But , God is God. He hear our prayers so let us pray for our nation
Inetu ndikudabwa ma prophet akungokamba za ndale basi asiya ntchito yamulungu akufuna zosangalatsa anthu, ndi kuntchuka basi samalani pogwira ntchito yamulungu.
Ngat alindizelu zanji , pamene inu mukulosela
Mlhomwe uyu akubakila ambuyache profeti profeti za zi
Zambiri simukumalizisa ziuleni tiziweletu
Ambuye akuchitireni chifundo pakuti simukudziwa chomwe mukuchita
Tiuzeniko a prophet anapha Mcdolnard Masambuka ndi ndani.. please
Mulungu amukhululukire m'busayu
Kampeni ya DPP eti
Moto khosa mkumat tili nda abusa mm km yah
Satana walowa ku ma prof
Mukukamba zandale bwanji tapempelelani Malawi khozi zimene zikuchitika kuno
We don't believe in prothet we believe in heaven God shame on u
Atsatu ndawi yophembela mulibe basi one day pa week ndaleso pomwepo kwanamisa anthu kuti mumalangulana ndimulungu koma kwiyo wamulungu ndimoto wosata samalani
Kkkkkkk aprofit
Mulungu yekha ndamene akudziwa zonse
One prophesied that chilima will govern the country km anatisya.... Abodza awa
Every prophecy imakhala ndi direction yake.. once you miss the direction, forget about the manifestation...
It is not duty to say who is right or wrong , false or true
But , God is God. He hear our prayers so let us pray for our nation
Za ufumu wa kumwamba zilipo apa?
Koma ine kumalawi omwe anatembelera dziko lakumalawi iiiii aneneri
Aprophet akuona dpp ikupita kumasankho Opanda tsogoreri
Abusa mavesi ngsti atha yambani ndale mulungu wathu alibe chisokonezo
It's your job to pray for them
What is your job?
Kodi zimenezo ndi za Mulungu kapena zamutu
Ndapangani za mulungu Nanu bwanji pomwe mwakhala basi za chipani kungofuna ndalama mzina la mulungu kkkkk
Iweyo ndi mbusadi koma kapena wachita kutumidwa