Wawa kwathu ku ndirande woooooow my beloved brother may the lord almighty continue protecting you wherever you go in Jesus name Amen brother ntanyiwa mumatiimirila brother 🙏
Ineso ndilikuno ku south africa mbali ambiri tikoza kukuwuzani wina wake mzimba amanyamula karundu kenako kukasolo katundu wama customer or mate bwanji iyeyo mamasula
Auzeni ndithu onse amene akukusakani kuti akupheni Inu Mr Comrade Ntanyiwa ,BMTv ndi Bone Kalindo ,kuti sakuthani chifukwa Mulungu Ali mbali yanu ❤❤❤❤❤❤
Wawa kwathu ku ndirande woooooow my beloved brother may the lord almighty continue protecting you wherever you go in Jesus name Amen brother ntanyiwa mumatiimirila brother 🙏
Mtanyiwa unali kt ndawi yonse BP inankwella posankuwonani👊👊👊🔥🔥
Bp inakwelat musamasowe choncho mr Ntanyiwa mumatiyimilira inuyo Allah azikutetezan mthawi zonse hearing you from Zambia
Weldone Brother NTANYIWA
Keep moving forward and keep updating fellow Malawians.
Ku MCP Kulichiwanda choyipa mchifukwa chake zochita zawo zambwerera bas Zilope zikuperewera , MCP kadyeni Zilope uko zokhazo tikudziwa mumatchipisa😂😂😂😂😂
Well come back Mr Comrade ntanyiwa
Koma chakwera iweyo thawi yako akuziwa ndi mulungu
Ndipo tinakusowanidi Mr Comrade Ntanyiwa🎉🎉
No ntanyiwa ,no bon kalindo ,no bakili muluzi tv Malawi is nothing ❤
Respect big mmakwana,pilizani kutidziwitsa zambili
Wawa comrade well came back.
Kuwaona akupha anzaoo nkhopezo mmmmmmm God have mercy on us
Mr Mtanyiwa please musamasowe,anthu akumaona ngati mwagwidwa
❤🎉 we love you comred
Mr Comrade ntanyiwa Allah alipo azikutetezani thawi zonse
Maganga was a master minder that's why anatuluka kunja during the mission and he can win the case
Mr mtanyiwa tinakusowani ife stres inayambatu timakukondani braz. Mumuuzeso kamajeketi machine ake apite akaphe kaye abambo ake chakwela anthu akusaukitsa dziko lanthu anthu oyipa mulungu azakulangani
Ineso ndilikuno ku south africa mbali ambiri tikoza kukuwuzani wina wake mzimba amanyamula karundu kenako kukasolo katundu wama customer or mate bwanji iyeyo mamasula
😂😂😂😂 e km anthu satheka akupanga zithu eeee
Mr Comrade
Ndipo Mulungu amene amatiteteza ku zooneka ndi maso komanso zosaoneka apitilize kukutezerani azibale athu🧎🧎🧎
Kunkuyu is a madder , he must be Arrested for real, Thanks to Mr Mtanyiwa and Limpopo FM
Akangomupha bon kalindo adziwe kt tisanaike kalindo iye adzakhala atachoka pa mpando
Kma kukuyu unakaxiwa iwe muwauze kt zimene anapanga ku Lilongwe zija ifes ngati ana okwiya Blantyre takwiya nazo kukuyu MCP ichoke
after 2 days❤❤
COMRADE NTANTIWA sakani number ya munduyo mutiwuse ndi kanyamura ameneyo tipaseni marowo
1st comment
Kunkuyu undisamale kwambiri umandinyasa kwambiri
Topic anyamata akundilande
Takaliporeni asamapange zopoira asaaaa
Ndipo let me tell you chakwela resign live 🇲🇼 malawi alon pls plz chakwela no sense
moses kumkuyu ndichiwanda yooo....
Machende akeso mnyamata ameneyo ndi chakwela wakeyo
❤
Kodi ndale zake tidzingomva zophana basi?
Comrade Ntanyiwa iwe ndimachine
BOLA ASAMUOMBELE MKAMWA NATASHA YO
Angotimaliza bax
Koma mtanyiwa umakwana tikuzuzika kuno nnnnnnn
Zavuta ku malawi tilibe chonene
Mulungu Alipo kunja kuno..kunkuyu akanakhapidwa Ku ndirande kuja zikanajhala bwino
Weil come back
Bp inakwera mr
😂😂😂😂😂😂 Natasha Loja
25%? Ndi 35 %
Kuwaona akumkuyu akewo usipa wabonya weniweni😂😂
😂😂😂😂😂 akungokhwima ndebvu zokha kkkkkkk
Tiwuzeni bwana
Kkkkkkkk kma iwee ndi 1
Koma thanyiwa umandiza ngalazae😂😂😂😂mwati boma lo nyenga nyenga😂😂
acomred mutatisowa mumakwana
❤❤❤❤❤❤❤
😂😂😂 mwat mukhoza kuwinda nd chakwera
Zoona mukhoza kuwina
Mmm bc asiyen ingweyose bc😊
Munasowadi bwana
Munasowatu mulipo kod?
Ndicifukwa akuonda ndi masaya omwe inu simuona? Nkhope yakenso ili makwinya makwinya ulendo uwo kwasala mkufa.
𝙒𝙚 𝙖𝙨 𝙢𝙖𝙡𝙖𝙬𝙞, 𝙬𝙚 𝙖𝙡𝙡 𝙡𝙤𝙫𝙚 𝙮𝙤𝙪 𝙗𝙧𝙤𝙩𝙝𝙚𝙧 𝙉𝙏𝘼𝙉𝙔𝙄𝙒𝘼