KU MCP KULIMBILANA MPANDO WAU VICE PRESIDENT 🙌🙌 21 July 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 63

  • @ChisomoMachowa
    @ChisomoMachowa 2 หลายเดือนก่อน

    May Almighty God make your dreams come true Mumba.

  • @mcdonaldchirwa3182
    @mcdonaldchirwa3182 2 หลายเดือนก่อน +4

    Influential and briliant Eng.Vitumbiko Mumba deserve to be MCP and Country Vice President

    • @WorriedNdhlovu
      @WorriedNdhlovu 2 หลายเดือนก่อน +1

      We don't need mcp

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 2 หลายเดือนก่อน +3

    IF ANY PARTY LEAVES GOD GOD WILL LEAVE THAT PARTY AND THE GOING TO FIGHT AMONG THEMSELVES AS A PUNISHMENT

  • @kachisuzimwale5641
    @kachisuzimwale5641 2 หลายเดือนก่อน +2

    Very confident young leader. God bless you

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 2 หลายเดือนก่อน +11

    Mukurakhura English kuti amalawi amve kapena kuti anthu akudziweni kuti mumatha English

    • @masakaunga4099
      @masakaunga4099 2 หลายเดือนก่อน

      Kusamva chingerezi ndi vuto lanu kusayenda eti

    • @lewisdicksonmlozi130
      @lewisdicksonmlozi130 2 หลายเดือนก่อน

      @@masakaunga4099 iwe galu iwe Wanda kutiko.ukumudxiwa amene ukumuyakha zaku kusi kwa mazila ... English yake itiyo kumalawi kuli.. English..iwe wayenda kutiko galu

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 2 หลายเดือนก่อน +8

    Iweyo Mumba ndiwe wakuba pamozi ndi chakwela

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 2 หลายเดือนก่อน +6

    Vuto ndiwe waku mpoto
    Chipani chikutemwera wa nyawu ichi mzala

  • @GordonMbale-f1b
    @GordonMbale-f1b 2 หลายเดือนก่อน +2

    He is speaking with his new vision to build the MCP party.

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 หลายเดือนก่อน +4

    Kodi nde kuti manganya ndiwongogwirizila?

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 2 หลายเดือนก่อน +1

      Akupanga za MCP osati za Manganya

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 2 หลายเดือนก่อน +1

    Bolako vitumbiko is still fresh than idi Amin zikhale Ng'oma

  • @georgengwira3152
    @georgengwira3152 2 หลายเดือนก่อน +5

    Wakuba uyu amaba ndi nick chakwela

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 2 หลายเดือนก่อน +1

    As long as ali clean ku corruption, he has my nod

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chokako chabe ku mcp mwana wakwithu mcp ndiyakuphatu

  • @GiboTakondwa
    @GiboTakondwa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Tikamati Malawi amene mumati ndinu ophunzi tikuona Ngati Kuti mbuli ndinu momwe uthengawu siukupita kwaanthu akuamerika ayi lankhulani yankhani Koma so funsani zonsezi gwilisani ntchito chilankhulo chathu mwina ndizofunikila Koma kwaine palibe chimene ndtolapo Koma so ndamvapo Koma so nkulu ameneyu siyemweuja timamva Kuti wakhala akusolola misonkho yathu ndi Nick siameneyu

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r 2 หลายเดือนก่อน

    Koma chi Wonder Msiska ichi 😂😂😂

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wanda ❤

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mungochedwerako ku mcp kwanuko

  • @GlynMhango-bk4hz
    @GlynMhango-bk4hz 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wanda ndi one 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂,,,,,, times ndi times

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 หลายเดือนก่อน

    Vitumbiko Mumba waba kwambiri. Mfitiyi ikufuna kupha anthu.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 หลายเดือนก่อน

    Ma plan ndiofuna kuti MCP chipani chomwe chapha anthu ofinika kwambiri a kumpoto chipitirire kulamulira. Ma plan akowo ndathetsa lero satheka. MCPigs yakoyo yatha lero. Pamtumbo panu a MCP afiti anyau nonse.

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk mwati akunthandiza anthu ndale pambuyo kod amalawi tikunyengera chani aaaaa asamatinyengerere chifukwa cha 2025 yayiii

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 2 หลายเดือนก่อน

    Limbikilani wabaliwinthu wakuno Ku mupoto mutukule chigawa chinthu.wachewa wakuderera

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb 2 หลายเดือนก่อน +1

    Uyooooo wapezeka uyu ndiye akukwanila osati zinaziiiiiii mmmmmm

  • @sandramkaligida1163
    @sandramkaligida1163 2 หลายเดือนก่อน

    Democracy at its stage ❤❤❤
    Mcp

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 2 หลายเดือนก่อน +1

    Akuzani zachichewa ndipo muzikapikisana ndi zikhale ng'oma akakumangani zanu amadalila uyolo

  • @JOHNMANDO-z4h
    @JOHNMANDO-z4h 2 หลายเดือนก่อน

    Vuto mwatchuka ndi mbili ya Kuba pamodzi ndi Nick.

  • @JohnChinangwa-r2g
    @JohnChinangwa-r2g 2 หลายเดือนก่อน +2

    sangawene awa. aba kwambiri

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 หลายเดือนก่อน

    Iweyo sungawine kuonetsa odzitama komaso ndiwe tsotsi wakuba

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 2 หลายเดือนก่อน

    Ngat zili za MCP taiwalani baba

  • @BonnAdams
    @BonnAdams 2 หลายเดือนก่อน

    Why can't he answer chichewa in chichewa questions but he answered tumbuka to tumbuka questions this guy

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 หลายเดือนก่อน

    Asiyeni akhungu apikisane akhungu okha okha mapeto ake ku gehena mcp pamu kulibe anthu oganiza bo koma l
    Kuli ogula maudindo ndi ndalama za amalawi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 หลายเดือนก่อน +1

    Bingu angafanane ndi inu anakanyimbi

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 2 หลายเดือนก่อน

    Olo iyeyu atakhala vice president chingasinthe ndi chani poti iyeyo ndi mphava kale .

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 2 หลายเดือนก่อน +1

    Amabela limoz ndichakwera iyeyu kulibwanji kuti alowe boma mbudzi imeneyi yakuba zed

  • @bayanimponda8746
    @bayanimponda8746 2 หลายเดือนก่อน

    You have gone to wrong party. Sorry Mumba.

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di 2 หลายเดือนก่อน

    Otherwise 🔥💯

  • @JOHNMANDO-z4h
    @JOHNMANDO-z4h 2 หลายเดือนก่อน

    Vuto muli ndi mbili yakuba boss

  • @FrancisDominic-w1s
    @FrancisDominic-w1s 2 หลายเดือนก่อน

    Alankhule chichewa

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 หลายเดือนก่อน

    Kulongosola mwa ndondomeko ,uku ulongozgi nabo wungaba walwana mumawulongozgi

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 2 หลายเดือนก่อน +1

    Don't trust this guy manje alinakawalala mbamva zopemphera izi pamodzi ndi Rev chakwera..

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di 2 หลายเดือนก่อน

    Munamusokoneza mtolankhani tsitsi muzimeta izi zimafunika private chart ngati mukudziwana. Confusing atolankhani

  • @AliajoeAliajoe-vv1wo
    @AliajoeAliajoe-vv1wo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Achina BwenuBwenu

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 2 หลายเดือนก่อน

    Tikukufunirani zabwino mumba

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 2 หลายเดือนก่อน

    Times imangong'alula 😂😂😂😂😂

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mutu ngati tomato Ali trouser mwako umo

    • @spargomw
      @spargomw 2 หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkkkkkkkkkk mayo koto ine😂😂😂😂

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 หลายเดือนก่อน

    Ufuna iweso kuchikangawa😅

  • @Ushermchebe
    @Ushermchebe 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂🥱🤷🤷🤷🤷🤷🤷

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 หลายเดือนก่อน

    Wakuba lwe iyaa

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน

    Mbava yachabe chabe iyi akagwele uko

  • @YusufuAmini-r8r
    @YusufuAmini-r8r 2 หลายเดือนก่อน

    How can he cry for vp Malawi is rotten for sure vitumbiko useless wagain

  • @FungulanReuben
    @FungulanReuben 2 หลายเดือนก่อน +1

    I don't trust this guy, is a one akuoninga dziko, ndi mbava imeneyo

  • @JosephKawale
    @JosephKawale 2 หลายเดือนก่อน

    You deserve

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mumba ndi okuba akuba limodzi ndi chakwela ndi niki

  • @LabKazembe
    @LabKazembe 2 หลายเดือนก่อน

    Dziko la Malawi pano laloweka chbwana mwachidule mulibemo president lafika pa manyi I'm feeling pain where is my country going

  • @emmanuelkamwagha9364
    @emmanuelkamwagha9364 2 หลายเดือนก่อน

    Find other party you will win

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 หลายเดือนก่อน

    To know that this guy has evil plans for the country listen to his speach between 5:51 and 6:20. He wants to be stealing money to go to people who are running a party MCP rather than people who are working to improve lives of people. He is citing ANC, CCM, ZANU PF. Amene amati ndiwe mbava yaikulubsakunama. A Malawi amnzanga mumumvetsere bwino bwino mfiti ameneyu ndipo mupeza kuti akufuna kuononga Malawi. Musathamangire kutukwana mvetserani ndi chidwi video imeneyi. Tikamati MCPigs ndi afiti sitinama ayi. Pamtumbo panu a MCP afiti nonse.

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 2 หลายเดือนก่อน

    Crooks at it’s best

  • @AliajoeAliajoe-vv1wo
    @AliajoeAliajoe-vv1wo 2 หลายเดือนก่อน

    Nonsense