A Michael Usi Inu Si A UTM - Lyton Mangochi

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 7 ก.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Lyton Mangochi says that the Right Honourable Dr. Michael Usi is not a true member of the United Transformation Movement.
    Pa Nyasa VoiceBox, Lyton Mangochi wati Wolemekezeka Dr. Michael Usi si membala weniweni wa United Transformation Movement.
    #malawi

ความคิดเห็น • 268

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h หลายเดือนก่อน +31

    Iwe mangochi umandibowa pazambiri koma leroli wakamba chilungamo ❤❤ the spirit

    • @tinigo-k8e
      @tinigo-k8e หลายเดือนก่อน

      😂😂😂

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 หลายเดือนก่อน +11

    This is straight forward talk and advice

  • @MEGANABIGAILMNTHALI
    @MEGANABIGAILMNTHALI หลายเดือนก่อน +8

    Munthuyu nthawi zina amalankhula zoduka mutu koma lelo walankhula chilungamo ndakukonda Mr mango hi for this audio.

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete หลายเดือนก่อน +29

    Galu ndi gula manganya siwa utm komaso anamupeleka chilima

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 หลายเดือนก่อน +11

    Uthenga opanda chigamba, apa ndiye chilungamo.

  • @user-bn8hh2wb5b
    @user-bn8hh2wb5b หลายเดือนก่อน +7

    Bwana Lyton mangochi lero mwakambako mfundo zomveka bwino ulemu wanu

  • @user-cy4pg1bo5o
    @user-cy4pg1bo5o หลายเดือนก่อน +4

    Apapa ndiri mbariyako or mntaniwa atanva audio yakoyi akunva kukoma mot utamatero anthu akukonda kwambiri the fact u hv say to day congrats Mr Layton big up tufuna chirungamo choncho

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 หลายเดือนก่อน +8

    Ndipo bwana Mangochi mwang'alula ulemu wanu akulu awa eeeish atipepelesa sure

  • @TheresaNtodwa
    @TheresaNtodwa หลายเดือนก่อน +5

    Mr. Mangochi awuxeni abambo amenewa chifukwa ndiye akupanga. Zinthu zobowa kwabasi.kasatana kachabe chabe kauzeni kamvetsese

    • @DysonUmali
      @DysonUmali หลายเดือนก่อน

      @@TheresaNtodwa exactly

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy หลายเดือนก่อน +10

    Ine umandinyasa heavy kma lero Mutu wako wayamba kugwila ntchito ❤zanzeru
    Someone hit Like for me

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx หลายเดือนก่อน +1

    Iwe Lyton Mangochi apa wanena mfundo osati yamasewera. Ndamvera each and every sentence looking for a mistake koma mwalankhula zaufumu weniweni.
    I love you

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow หลายเดือนก่อน +2

    Apa pokha Usi avomereza chilungamo kuti anthu alindi maso ndipo amaona ndithu iiiii

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo หลายเดือนก่อน +1

    100%. Usi si wa UTM. Angofuna kusokoneza UTM yo.
    Tilitonse mau olawura asiye.
    Ngati zolankhura alibe angosiya. zamadirama ife sitikufuna.
    Ine ndili wakwanu. Kumwitu koku Karonga. Komam'sasiye kudziwitsa anthu choonadi, monga m'nachitira pakatipa.
    Tinali kuganiza kuti nanutso mwagudwa.

  • @SolomonMbewe
    @SolomonMbewe หลายเดือนก่อน +2

    I think you are coming back to your senses Mr Mangochi.... Keep it up.

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h หลายเดือนก่อน +6

    Ndakuombela mmanja mangochi apa pokha chilungamo chimamasula usi ndi wa MCP

  • @laurentbutao4084
    @laurentbutao4084 หลายเดือนก่อน +3

    Chilungamo chimawawa koma izizi ndi zoona..Malumewa SI a UTM

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o หลายเดือนก่อน +4

    Apa nde wang'alula zeni zeni momveka bwino dziko akulitengela chibwana

  • @zulubeats1071
    @zulubeats1071 หลายเดือนก่อน +5

    Bwanji osakayendera ma office a NRB ku southern, eastern and northern regions kuti anthu alandire za unzika mu nthawi yabwino?

    • @MEGANABIGAILMNTHALI
      @MEGANABIGAILMNTHALI หลายเดือนก่อน

      Akanangopanga za tikufzlanji asamasokoneze anthu

  • @user-bs8nk1si4e
    @user-bs8nk1si4e หลายเดือนก่อน +4

    AMangochi,apatu mwaonesa umunthu.ndipo mukukhala ngati siinu a Mangochi,koma zikomo. coonadi ncofunika

  • @FatimaSande-lb1hd
    @FatimaSande-lb1hd หลายเดือนก่อน +4

    Uku tu nde kuyankhula kopanda chigamba mau mau. pena nso atipeperetsa a Usi wa Aaaaa inu

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v หลายเดือนก่อน +1

    Mr Lyton Mangochi ulemu wanu mwayankhula chilungamo God bless you Mr Mangochi

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d หลายเดือนก่อน +4

    Lyton Mangochi apa walankhulatu ngati munthumuuzeni usi akutitenga ngati ife zitsilu hule wamunthu

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf หลายเดือนก่อน +4

    Madala madala tsopano, munasowatu😁💗💗

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 หลายเดือนก่อน +1

    Well composed speech keep it up Mr Mangochi. Teach him a lesson

  • @FelexMisolo
    @FelexMisolo หลายเดือนก่อน +4

    Apa ndiye wayanbapo kumeneko zanzeru

  • @RitaKainga
    @RitaKainga หลายเดือนก่อน +1

    Mwayankhula chilungamo malumee,May God bless you!!! Ameneyu adzazunzika nao mzimu wa Chilima

  • @user-ih7li3im4s
    @user-ih7li3im4s หลายเดือนก่อน +2

    Apa wayankhulatu za nzelu even BON Kalindo ajuyamikila

  • @ClementbWatches
    @ClementbWatches หลายเดือนก่อน +1

    Lerotu Mr Mangochi mwakambatu mfundo zomveka bwino. Ulemu wanu manganya komwe aliko amve. Chipan chathiko Ife ayi.

  • @user-ck7eb7tb7v
    @user-ck7eb7tb7v หลายเดือนก่อน +2

    Ife UTM sangatigulitse .... UTM yachilima ija ilipobe ija yachina Kaliati

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k หลายเดือนก่อน +2

    Koma apapa zikumveka bwino kwabas Mangochi walankhula mwanzeru chifukwa Manganya samamukonda Chilima .

  • @ZebronTembo-u6p
    @ZebronTembo-u6p หลายเดือนก่อน +1

    Mqngochi your right ukunena zenizeni congratulations bro

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 หลายเดือนก่อน +1

    Mwanena zoona Mr Mangochi. Manganya akufuna Kuba Chipani!

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu หลายเดือนก่อน +3

    Iweso ukuti musiyeni usi ndwe Galu team ya Mr chikangawa fiti agalu lnu

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk หลายเดือนก่อน +3

    Mangochi apa nde wandilankhulila ndithu angofusa kutisokoneza ife a UTM

  • @CharlesChamveka
    @CharlesChamveka หลายเดือนก่อน +3

    Ay Mr mangochi apa pokha mwayesesa kulakhula kwa nzeru

  • @CharlesKanuni
    @CharlesKanuni หลายเดือนก่อน

    Mr mangochi took his time to recharge and came back stronger 💪

  • @PartLupiya
    @PartLupiya หลายเดือนก่อน +1

    Lero wayankhula mwanzelutu a bro, more fire 🔥

  • @user-is5zi5rw8w
    @user-is5zi5rw8w หลายเดือนก่อน

    Today it's ur best audio mr mangoch best audio ever muuzenidi achose kachiwanda ka ma drama kkkk

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 หลายเดือนก่อน +2

    Well spoken.....

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 หลายเดือนก่อน +3

    Amangochi mukafuna mudye za ausi .

  • @DaveMakondetsa
    @DaveMakondetsa หลายเดือนก่อน

    mwayankhula bwino kwambili ngati zikadi wa Malawi❤❤❤❤

  • @CtvnMpina
    @CtvnMpina หลายเดือนก่อน

    Well said big man,thumb up🔥

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 หลายเดือนก่อน +1

    Anali ngati Petro yemwe amamuonera Yesu patali ali pakati pa adani kumfunsa uyunso anali waiwo amvereke akunama sindikumudziwa ine ameneyo.

  • @LamieTiger
    @LamieTiger หลายเดือนก่อน +3

    Apo Nde wanena zoona a usi Sia UTM

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr หลายเดือนก่อน

    Bravo, wayamba kuyankhula mfundo zenizeni, zamphamvu.

  • @AlexKamowa-u7m
    @AlexKamowa-u7m หลายเดือนก่อน

    Good speaking mr Lyton mangochi

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 หลายเดือนก่อน +2

    Well spoken 🔥🔥

  • @DaudKYSilindu
    @DaudKYSilindu หลายเดือนก่อน

    Mr Lyton excellent spoken keepitup

  • @asahelmachila3026
    @asahelmachila3026 หลายเดือนก่อน +1

    Long live Impi Biyeni

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน +1

    Good Message Mr mangochi

  • @DicksonMacheso-lr7oy
    @DicksonMacheso-lr7oy หลายเดือนก่อน

    Fundo zinazo za mangochi ndi zopoila, amalawi tikuyenera kudziwa kuti tonse ndi amalawi koma zinkhulupiro ndi zotsiyana,kutsapedzaeka a Micheal usi ku candle 🕯️ light sichifukwa choti anene kuti si wa utm koma anene zifukwa zina

  • @tobiasshalla
    @tobiasshalla หลายเดือนก่อน

    Let the Vice President be please !!!

  • @ThokozaniBilliat-im7lf
    @ThokozaniBilliat-im7lf หลายเดือนก่อน

    Manganya palibe akulakwitsa and zomamena kut sanali wa UTM kapena kut si wa UTM ndikulakwa chabe.Mvuto lomwe Malawi tili nalo ndi nsanje.Chilima anamutenga chifukwa chani Micheal usi ngat sanali ofunikila?.Amene akudzimva UTM kwambiriwo bwanj Chilima sanawaike pa vice president?.Nsanje kusavomeleza phunzirani makape inu

  • @dunstankgombezi2911
    @dunstankgombezi2911 หลายเดือนก่อน

    Apa mwayankhula big.
    Osaka asowa poyambira.

  • @ewn-mc6jv
    @ewn-mc6jv หลายเดือนก่อน

    Amanganya ayenela kugwetsedwa mmpingo chifukwa ana phwanya limodzi la malamulo khumi. (Bodza)Ndinamva akukamba bodza mu zoyankhula zao pa zokhuzana ndi UTM. Mwanyozetsa mmpingo.

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx หลายเดือนก่อน +1

    For the first time I am happy with you Mr Mangochi pa zanzeru zomwe mwalankhula apa.
    I'm sure kuti we're expecting more from you

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc หลายเดือนก่อน +1

    Respect

  • @slow-kkamanga4906
    @slow-kkamanga4906 หลายเดือนก่อน +1

    very true mangochi

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o หลายเดือนก่อน +2

    You. have said. the truth utsi. is not for utm

  • @user-ds6zj9um6g
    @user-ds6zj9um6g หลายเดือนก่อน

    Powerful message

  • @BensonMoyo-pf2ci
    @BensonMoyo-pf2ci หลายเดือนก่อน

    Mwayakhura fundo ❤

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz หลายเดือนก่อน +3

    Apo wabaya

  • @VictorCustom-my1nv
    @VictorCustom-my1nv หลายเดือนก่อน

    Powerful advice from Mr Mangochi.

  • @chimwemwemorris6827
    @chimwemwemorris6827 หลายเดือนก่อน

    Zangongore zakezo tilibenazotchito koma asamatinamizekuti ndi wa UTM ai sitikumudziwaife

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga หลายเดือนก่อน

    Michael Usi the big man

  • @mrcool531
    @mrcool531 หลายเดือนก่อน +2

    Amangochi mwalankhula zanzeru kwambiri mu audio iyi

  • @GladysBanda-h2w
    @GladysBanda-h2w หลายเดือนก่อน

    manganya watikwana kale.Mr Mangochi mwabwera

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko หลายเดือนก่อน

    Manganya ndichisilu galu ndi mozi mwa anthu ogwesa ndege ameneyo😮😮

  • @AishaChipande
    @AishaChipande หลายเดือนก่อน +1

    Ndinalutuluka kale koma yapa pokha wayankhula zazelu ngati siukufunaso kupepha kwa manganyayo

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m หลายเดือนก่อน +1

    aLyton APO mwalankhu zoona avaice si a UTM ayi

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l หลายเดือนก่อน

    Paja amalawi pomwe munthu akupadula muwombela mumanja. But utm be careful once a party is divided into two no matter mbali yona ndi yochepa the conclusion will be a big space. Believe me utm usi and kaliyati please just sit down together and agree united and peace and friendly....utm yitha kutha mosavuta pa dziko lathu ndi into Three no matter what.
    Ya Papa kumwera yikhala usi utm pakati chilima UTM kupoto ndidela lovutitsisa don't relax with people from north they are chameleons... You can't trust northern region

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg หลายเดือนก่อน +1

    Kodi Usi akamayenda m'mene akuyenderamu ndie kut ntchito ya nduna ndi chani? Akungofuna kupeza credit koma akutionongeranso misomkho yathu.

  • @user-ck7eb7tb7v
    @user-ck7eb7tb7v หลายเดือนก่อน +1

    Mwayamkhula bwino sure

  • @StoneckJali
    @StoneckJali หลายเดือนก่อน

    Mumafuna muzidya naye ngati achipani muziyenda naye mwauponda. Musiyeni zanu agwire ntchito ya boma mufune musafune president wa UTM ndi Usi

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o หลายเดือนก่อน +1

    Lyton. mwalankhula zan,zelu. Kwambiri kwambjri. takuyamikila kunokuchitipa

  • @DysonUmali
    @DysonUmali หลายเดือนก่อน +1

    Mangochi wandigwira mtima koopsa

  • @GabrielMzich
    @GabrielMzich หลายเดือนก่อน +1

    Manga NDI Yudas weni weni munthu opanda manyazi opanda chifundo ngati uyu mizimu ya Chikangawa Ili pa mutu pake fiti iyi

  • @milliambandah1939
    @milliambandah1939 หลายเดือนก่อน

    Yudasi sikaliyoti Manganya siwa UTM angotaya nthawi yache pachabe munthu oipa

  • @SoldierWilison
    @SoldierWilison หลายเดือนก่อน +1

    Leroditu alangula zaseru

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 หลายเดือนก่อน +1

    Nkhani iyi ya Straight forward 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 ulemu wanu uku kulakhura mwabnzeru manganya or tsiku limodzi lopedzeka pa mwambo oyasa ma candle yoooo or tsiku loyakhulapo zokhudza imfa ya chilimba mmmmm Ambuye akukhululukireni iwe ndi mpeni othwa konse konse iiiih Chilima Rest well tidzakulirani mpaka kale 😭😭😭😭😭😭

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน

    Very good Mr Mangochi good Message ❤

  • @Gwedeza-oz3jv
    @Gwedeza-oz3jv หลายเดือนก่อน +1

    Zanzeru ndizochepa umu kuti mumumvele bwinobwino statement yakeyi yachoka kwa iye manganya mwini kuti awuze mtundu wa anthu kuti akazamati ndine wa mcp anthu asazazizimuke kwambili,
    Ndipo chakwera ali mommu this is propaganda of mcp

  • @user-qh5jo5qh3b
    @user-qh5jo5qh3b หลายเดือนก่อน +1

    Layton magochi lero wayesetsa utamatero mwina anthu ayamba kukukonda

  • @mphatsomalenga
    @mphatsomalenga หลายเดือนก่อน +1

    Anatha awa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 boma ili silikufuna kukhala ndi opposition ai,kusafuna kukhala ndi opposition zimasonyeza kuti ndiwe otayilira and sufunaso kudzudzulidwa.

  • @user-gu3sp8ci6v
    @user-gu3sp8ci6v หลายเดือนก่อน

    Wayankhula za nzeru koma awa itha kukhala njira yopemphera ndalama kuti awapatse kenakake akhale chete

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 หลายเดือนก่อน

    Apatu Mangochi walankhula zanzeru, tikumudziwa Manganya kuti ndi betrayer wankulu ndipo ndi mthira kuwiri

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 หลายเดือนก่อน

    Listening Keenly .....kambani ndithu

  • @JanetJamesMachila
    @JanetJamesMachila หลายเดือนก่อน

    Kumva kumakuvutani amalawi manganya si wa utm anali ndi chipani chake anapanga ngwilizano ndi chilima amalawi mwatani kodi

  • @giftedmshan6779
    @giftedmshan6779 หลายเดือนก่อน

    Ngakhale Mangochi ndiwamisala koma apa ayankhulako zanzeru

  • @anusahjenala1063
    @anusahjenala1063 หลายเดือนก่อน

    Ndende ndende ndipaseni acount yanu mukatenge sweat muike mkamwa mwalankhula zoona zeni zeni ndipo inuyo mulungu alowele pa nzeru zanu

  • @ibrahimdyman4356
    @ibrahimdyman4356 หลายเดือนก่อน +1

    Wayakhula ndithu za zeru

  • @PatrickMbenje
    @PatrickMbenje หลายเดือนก่อน

    Well spoken

  • @JamesKamtedza
    @JamesKamtedza หลายเดือนก่อน

    Lelo mwayakhulana zazeru Mr mangochi ndalam zathano et

  • @user-lu6nq9bs6w
    @user-lu6nq9bs6w หลายเดือนก่อน

    Nsokhano uliwonse ine nali wakut nali wakuti Inu anthu ambili anasinthika kuchoka ku umphawi kumene koma sikut ukachita bwino basi history yokha yokha pa nsokhano.

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน

    Akulipira zingati amene akutuma? Koma wayankhula mfundo zabwino. Zikuomeka ngati MCP yikufuna kuti Usi angopanga declare kuti walowa MCP osati zakabisalira ayi. Lyton Mangochi wapeza profession yabwino nawenso, yamalipiro abwino koma a temporary.

  • @OsmanYassin-co9ye
    @OsmanYassin-co9ye หลายเดือนก่อน +1

    mangochi ulemu wanu

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e หลายเดือนก่อน +2

    Mangoch wabwelanso ukufuna akupase ndalama zina mwatitola et😂

    • @EllahChikwatu
      @EllahChikwatu หลายเดือนก่อน

      Colinga chake usi amuitane mwapadera apase ndalama kt asamu kambe

    • @thomasphiri7799
      @thomasphiri7799 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita หลายเดือนก่อน

    UTM inatha guzy lero uyipa uja wasanduka wabwino lyton

  • @KingsleySomanje
    @KingsleySomanje หลายเดือนก่อน

    Ndipo zoona zenizeni mzimu wa chilima uwakathe amanganya pazomwe akuchita posokoneza chipani cha UTM

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg หลายเดือนก่อน

    Akatelo mangochi ndalama zamuthera akufuna Zina kuchokera kwa manganya koma wanena pakati aise