UTM YAGAWIKANA MAGAWO AMBIRI / BON KALINDO-17 July 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 25

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l หลายเดือนก่อน

    Akalindo nthawi zina i judge you kuti ndinu wopanda nzeru koma lero mwandiyankhulira dzazeru kwambiri God bless you ❤❤

  • @AngungaThatcherNgoma
    @AngungaThatcherNgoma หลายเดือนก่อน +2

    Nkhani ndi dyera a bwana. I don't trust the politicians. U.T.M ikapusa itha ngati makatani.😂

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 หลายเดือนก่อน

    Kalindo usaononge chipani cha UTM ponena boza,,uzilangiza bwino osaipisa chipani

  • @walesbanda4959
    @walesbanda4959 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk I think akanafuna kukuphani Mr Kalindo akankuphani kale a mcp wa. Ndikale lija munayamba kutiuza kuti akufuna kukuphani.

  • @user-gj8td8pc4d
    @user-gj8td8pc4d หลายเดือนก่อน +1

    Yamakanduloyu2 ndiye yosalongosoka.coz ikupanga ziganizo zot olo mwiniwake sakadapanga.mmasewero muja kumakana kukhala wamisala

  • @farlenmkorongo
    @farlenmkorongo หลายเดือนก่อน

    Boza ili anthu onse amakhara ku misonkhano kuja kuwapasa 6pin nde pawonongedwa ndalama zingati

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire หลายเดือนก่อน

    Just imagine abare inu eti eti

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l หลายเดือนก่อน

    My vote for Usi

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel หลายเดือนก่อน

    Boooon kalindo pena ndimakutenga I ngt simukuwona koma wakuva wava osava akhare

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem หลายเดือนก่อน

    Our DC is the president. Nd you always tolk streat.

  • @LenzoLunga
    @LenzoLunga หลายเดือนก่อน

    Eeeeee zovuta kwabc bwana DC... Dyera basi ndi lomwe lakula .... 😢😢😢

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 หลายเดือนก่อน

    Patricia Kaliati and others are just going back to where they belong, dpp. They do so due to frustration.

  • @beakab2378
    @beakab2378 หลายเดือนก่อน

    UTM needs people, sizolakwika ena atsopano kulowamo. Convention ikasankha mtsogoleri. Chilima samaletsa anthu kulowa utm. Zonati kaye pheeeee nthawi ikupita ndizimwe zaphetsa chilimayo. Anzeru sinu nokha tu. Chipani chipitilira and it will choose a keader ku convention. Mumafuna asankhe inuyo? Mmesa munkadana ndi zipani za ku banja inu, lero??? Lekani kugwiritsa ntchitu imfa ya chilima ngati choopsazera anthu, mzimu wake suli yakaliyakali kufuna kukantha anthu ayi. Ukuusa mumtendere. Mmesa munkatinso dpp yatha nankhumwa akuvuta? Lero ali kutiko?

  • @walesbanda4959
    @walesbanda4959 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅😅 ndinu nomwe Mr Kalindotu mwalimbikiitsa kuti achoke ku alliance. Zotsatira zake ndizimenezo. Ena sanazimvetse bwino

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v หลายเดือนก่อน

    No alliance with MCP

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 หลายเดือนก่อน

    Bambo sikoni ngati akufuna kupitiriza za chilima achoke ku mcp. Komaso a utm musagulise chipani kwa anthu ena amene akufuna kulowa pano poti chilima wamwalira anthu ndi mikango kodi mu utm mulibe woti angakhale president?

  • @macmanyusa8242
    @macmanyusa8242 หลายเดือนก่อน

    A dpp mulipo 🎉🎉🎉

  • @DeemsonMataka
    @DeemsonMataka หลายเดือนก่อน

    George saonda .Chosa Petro Chosa alikuti

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 หลายเดือนก่อน

    Manganya yo mumuwuze asagwirise zina la chilima or utm akamapangisa musonkhano. Azinena za iye ndi mcp yo. ACB bwanji yowona ku immigration kokha nduna za boma zikugawa ma million chifukwa cha maudindo ndalama akuzitenga kuti? And zovota 50 +1 zithe sitikufuna law yopusa and sitiyendera ma ID po vota chaka chamawa please Mr DC tanyiwa bakili TV aliyese Malawian ngati ndizika yamalawi adzavota basi

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo หลายเดือนก่อน

    Aaaaa abwana DC anthuwa mumaunikira koma sakumva 😂

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 หลายเดือนก่อน +2

    My vote for Chakwera. Economic problems in this country emanated from dpp. You always talk bad about mcp because you're dpp stalwart. Some of us do not wonder about this. Mcp is trying to bring back the economy to it's feet.

    • @beakab2378
      @beakab2378 หลายเดือนก่อน

      Uwu nde umbuli wadzaoneni. Chakwera has messed up the economy olo mwana akudziwa. 2025 he is going ndipo sadzabwereranso. Screen shot this

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga หลายเดือนก่อน

      Kulankhula ngt mutu wakhalira which economy is he trying to bring back?? In 4 good years devaluation yosei muzinama kt mufuna kubwezeretsa economy aaaa u r joking too much , nthaw yatha obwerayo ngt Ali ndi mtima okonda dziko azakoza not nyau yakoyi 😅

    • @jemasmasimbi8109
      @jemasmasimbi8109 หลายเดือนก่อน

      iyi ndie mbuli yeniyeni yopandaso tsogolo,,,

    • @henrymedeliko8727
      @henrymedeliko8727 หลายเดือนก่อน

      Iwe galu kwabasi