I like this man Joab Frank Chankhaza this man I like him naturally I wish to meet him personally I have a Gift for him much love from Zambia 🇿🇲 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲.
Mvuto ra anthu akudafe ndilomweri munthu wanena chilungamo pazomwe anapangapo kma she's still doing ,anamurandira yesu zas wy anabwera poyera ndizomwe wakhara akuchita asanamirandire yesu may his soul RIP
sindikuweliza ai koma baible limati mawonekedwe angakhale manvalidwe azilalikila za chauta. komanso tizikhala wochenjela matsiku wosiliza kuzabwela aneneli wonyenga ndipo azachita zodabwitsa mu dzina layesu koma mphavu yake adayikana
I like this man Joab Frank Chankhaza this man I like him naturally I wish to meet him personally I have a Gift for him much love from Zambia 🇿🇲 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲.
Mwapita Msanga Prophetess.. Rest in power
Wow Wow wow. You are the first Malawian to talk about an out of body experience.
Akutitu zimafunika renewal kkkkk what a life! We thank God for changing her .....
My name sake, Stella. School taphunzira limodzi , primary...dela lokuliranso limodzi, kawale 2. Rest in peace, Stella
She is late??
@peterchikwakwa8476 Yes, she is late. She passed away last year after a long illnesses
@@peterchikwakwa8476 we are neighbours with her parents in Kawale 2, Lilongwe. She was my childhood friend
Mvuto ra anthu akudafe ndilomweri munthu wanena chilungamo pazomwe anapangapo kma she's still doing ,anamurandira yesu zas wy anabwera poyera ndizomwe wakhara akuchita asanamirandire yesu may his soul RIP
Aaa adamwalira ! Ine ndikuionela lero pa 18 july 2023
"aliyense adagona ndi mwamuna waweni ndi hule"
hahahahaha spare me out
Rest in peace mama ooh story yosangalatsa kwambili
Zitsiru nonse amene mmanena kut mwachimwisidwa ndi mamuna atakupasani mimba mulekeletu mwina mukanati muziti mwachimwisana komanso zokut kupasidwa mimba ndi kuchimwa mmalemba mulibemo
Her voice is good in politics....
Kkkkkkkkk rest well madam prophetess,,,,,
Amayi awa atakumana ndi Ananyoni (Enifa Chiwaya) nkuyamba ndewu kkkk!! Kungavutetu😂😂😂
😅😅
Mulungu nde ameneyo amatembenuza zigawenga kuwapatsa ntchito ku ufumu wake
Programme yolimbikitsa ntchimo lingafiile bwanj adzaliteretsadi zili bwino
Rest in peace 🕊️
Kkk
Good lesson
To God Be The Glory
Rest well prophetess...
Anamwalira?
Chemwali bodza Bible linati m'masiku wosiliza kudzabwela aneneli wonyenga it's u guys
Tsano mmesa ngat priest samakwatilatu 😮
Joab amatha
Ankadwaladi even mmene ankapanga program
For own information from reliable source by Petro-Pen mwa anthu onse amene amapanga za soloon 99% amakhala okonda za uhule
I quit my marriage just to focus on Cruise 5 😂😂😂
Aaaaaaah 😂😂😂😂
sindikuweliza ai koma baible limati mawonekedwe angakhale manvalidwe azilalikila za chauta. komanso tizikhala wochenjela matsiku wosiliza kuzabwela aneneli wonyenga ndipo azachita zodabwitsa mu dzina layesu koma mphavu yake adayikana
Tik tok bought me here
God knows better about your spiritual life
Ada Joab mumaitha
Eeee anali ochenhera munthuyi
Mahule akuchita zinthu iiiiiiish
Koma anthu ngati awa amasowa olankhula chilungamo chonchi
Mulungu ndi wabwino nthawi dzomwe
Joab Joab munthu mpaka zibwibwi
Joab ndi katundu
Uhuletu sanasiye awaaa aaaah 😂
Kkkk koma joab mafuso ake mpaka kusindika kuti omwe mumapanga ndiuhule
Akuinekatu wamakani ngat nanyoni😅
Kikikikikiki
Mulungu ndiwa bwino amasitha nyengo zamunthu
Hahahaha Stella , I know this lady personal mnagwirako ku saloon kwake, ndipo nde sindikhulupilila
Chomwe sukhulupilira ndi chani 😂😂😂
Simukukhulupilira why?
😂😂😂mr joab mumatha
Uyu watambatamba
Uyu ndi fiti osati akunenazo eeeeeeh
🤣🤣aoneka ndiolimba mtima
Koma makeup 💄 ikutithandiza m zimayi uyuyu akuoneka kut anali wamkuru not pang'ono koma makeup 💄 ayi zikomo ikutiimirira 🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃
Koma amai inu musandikomole 😂😂 mwachitadi pslibe angakukanileni kkkk mudachenjelesa
Lol eish
Rest well Stella
Joab😂
Kkkkk misarat
😅😅😅😅
Kodi anthuwa mulungu amapedzana Naye kuti zayamba kuniopsa
😂😂😂mr joab mumatha
😂😂😂mr joab mumatha
😂😂😂mr joab mumatha