Ma delegates ali ndi mphamvu ku DPP , wabodza iwe kuwawidwa. Chipani cha anthu ndi DPP. muone nzako Nankhumwa waleka kunyoza DPP. Akutuma zifwamba za MCP zazikwanje. Chitsiru cha munthu
Everyone must keep in mind.... His exllence professor Peter muthalika The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🌹The winner of 2025 general election 🌹 No mistake allowed this year
Ufune usafune APM MY VOTE 💙💙💙💙💙
Abotoman kuzimva cholinga chanu kunali kuukila,kd mukuganiza kt Nakhumwa akanantha kupikisana ndi Chakwela? Zina kumaona kt mphepo zikuyenda bwanji?munali ndi cholinga kt mumphe Dpp osati muwine lero taona wekha mmene zilili chikoka chake Apm
To according you're statement ndiwe wa mcp
Muthu onyoza DPP kutha kumakhala komweko be careful
Achimwene muzipatse uremu timakondan APM my vote
APM my vote
Ng'oma yolilisa siyichedwa kung'ambika Botomani ndi kape
Mulungu salakwitsa kalikose aliyese wokhudxiwa pa ifa ya chilima awona pomuyika
Chilibe nzeru ichicho Zina lamunthu likakhale botoman fodya wapasi
Botomani ndichitsiru kwambiri
Usaname apa sitikukufuna ife aku chisi
Achisilu inu kwachilumpha ndiye mcp yakuthandizako chani umaziona ngati ndiwe wochenjela
Oro mutanyoza apm bwanji koma ife tikuti boma🎉🎉🎉🎉
Ndipo constituency ya kwathu ku matiya sitikumufuna
Botomani ndakuda komanso uzingopanga za mcp osati za DPP
Chilungamo mcp number one achinyamata alamule myko usi chakwela number one
Awa matama anawa kulira ndipo anachita bwino kumuchotsa amaipitsa chipani ndi timatako taketo akamayenda ngati nkazi akuti amafuna kukhara ngati nkazi ndye bolaso antie tiwo
Botomani APM anakunyamula kukuika in several positions including ministry of information lero ukuzinva ngati dolo mulungu akulange
Zoonadi munthu osayamika iwe, anakuchotsa chifukwa anakuika ndi APM
Tamuuzen KT APM ndi dolo kwambili end. Apite Ku Blantyre akawone lelo end sikuvaso KT mwat Bot. o ndan uko
Uko mkulira ndithu😂😂😂
Km ndaseka mwachikakhazi, chiyambi chakutha mutha ndkumeneku 😮
Inde dpp sichidziwa democracy
Or mutanena zoipa zotani za DPP palibe angapse ntima sitikufunaso MCP
kod kupandatu kumupha chilima apm sanakayimatu koma wayima chifukwa chot atichosele nyasi zilibomamu
Mbimbi 😂mutu yodalilika ya chikangawa pogwetsa Kwacha olo kwanu no chance
Zoona waona kuti yomwe wakwerayo anthu akwao sagwirizana nazo
Ameneyi eee ndiye chokuba komaso kopanda nako manyazi,anachootsedwa, chifukwa amagawana ndi azake za COVID-19 alankhula chani uyu
Ndiwe wabodza ukanakhala munthu wamzeru ukanakhala chete
Chaka chomaliza kutchuka ndichino APM akuthamangitsani pa September apa
Ngati mukufunabe abwerera ingobwererani
Pitani kwa anankhumwa ambwiye musaipitse mbiri ya apm
Zonama izo iweyo uluza tikungofuna kukudyera
Olo atainena motani dpp sapindula kanthu , dpp yatenga kale boma kusinthana ndi okupha
Anakuchosanibeni amwene musanyoze dpp
Mm mm mm adawachotsa akumva kuwawa kkkkk
Anthu adyela awa. Mipando muzatengabe koma lero ndi lero zimavuta
Ndiachilu amenewa
Ulendo uno ndi mcp yakoyo tione ngati ungaduse bwanawe
Ndiopusa awa
Wa bodza Botoman phungu ojiya ku MCP
Chipani chakuba kwambiri ife sitikufuna dpp kulowa m'boma
Kulamtima ameneyo wosokoneza
Munataya mwai inu
Eya mesa umanena zomwe umaziona zoipa
Kodi ndiye kuti akumva kuwawa ngati chipani ndi dpp yokha mmesa anayambitsa chipani Chao?
Kodi iwe Botomani akutuma eti? Ukunamatu, chayambi chamathero ako ndichimenecho, zomwe akufumbatitsazo ifika nthawi zitha zonsezo, ukagwere uko
Ife tiwavoterabe a APM wo
Watha bas kutukwana dpp ndekut watha pa ndale suwina or waimapawekha
Za ziiii
Nonse munachotsedwa Ku DPP mulibe pogwira..
Amasikini amaona ngati DPP itha, akunama DPP ndi ya anthu. Wa Congress.
No shame Ngati kumene muli zili bwino cholakhulira Za DPP ndichani mind ur own business
Zoonadi zikuwawa
Ma delegates ali ndi mphamvu ku DPP , wabodza iwe kuwawidwa. Chipani cha anthu ndi DPP. muone nzako Nankhumwa waleka kunyoza DPP. Akutuma zifwamba za MCP zazikwanje. Chitsiru cha munthu
Iweyo ingokamba zakozo basi
Bible likuti mwana onyoza kholo afe ndithu awa kwao kwatha basi
Iwe chenjera ukuyankhula nayeyo pomaliza afuna number yako cholinga akudye ndiokondatu akazi botoman chenjera chenjera alinafe maliza kuyankhulana naye
mcp,bomaaaaaaa
Kaloweni ku Utm muthandizane ndi Daliso Kabambe kugwira ntchito
Kaloweni kwa kondwani nankhumwa 😂😂😂😂😂😂 independent simuphura kanthu munampusitsa nankhumwa Inu anthu oyipa kkkkkkkk
KODITU OLO MUKUTUMIDWA NDI MCP MUSAGANIZE KUTI MUIKWANITSA AKUKUNAMIZANI DPP NDI BOMA MCP YATHA
mutha,kuona,apapa,amene,akulemba,makomedi,kwao,nkunyoza,akut,botomani,ndichitsilu,asanena,uchitsilu,wake,,a,dpp,akat,alemba,,amangodziwa,,zonyoza,,avekale,botomani,ndichisilu,basi
Chala sichiloza mwini inuyo batumikilani anthu amdela la kwanu,,,Ngati simukudziwa kulakwitsa kwanu ,,khalani chete basi ,,musayambe kuyalutsa DPP, leroli app mukatero tiona Kuti ena akutumani inde mwatafuna chi banzi😂
Ndipo inuyo Botoman ndikuuzeni lero Ngati simudziwa mwambi woti dzuwa salozelana
Anthu amuuza APM kuti awachotse mu Moto umene tikuuona mu dziko lino
Tiyeni uko zopusa zokha zokha
A journalist limenelo nfunso? Akati president ali ndi executive power zimanthawuza chani? Cream ya Malawi inuyo ....
Everyone must keep in mind....
His exllence professor Peter muthalika
The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
🌹The winner of 2025 general election 🌹
No mistake allowed this year
Mac botomn anakangot akufunaso kubwelela gonjan bas amwene ada ndi muthu wa ntima wa bho