BON KALINDO 17 SEPTEMBER 2024 KUNG’ALURA PA TUESDAY

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 29

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y วันที่ผ่านมา +2

    Bon Kalindoooo.Ndipo tamuonadi munthu wake akungobweka,kuyenda yenda ngati wadya matako agalu.Akuchita kuoneka kuti mtendere alibe.

  • @VincentMagriva
    @VincentMagriva วันที่ผ่านมา +2

    Mulungu ndiye mwina chilengedwe and sangalole kut tizivutika nthawi izakwana sachedwa safulumira kungot anthu ndiye tikuvutika tiyeni tikweze maso kumwamba thandizo lichokela kwa yehova pot zambiri zomwe tiziona pa dziko la pansi pano ndizachabechabe Mulungu wathu musatikwile tiyanganene nd maso anu achikondi ndipo mutipulumuse

  • @FrankWaresi
    @FrankWaresi วันที่ผ่านมา +2

    Thanks the dc

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza วันที่ผ่านมา +3

    Bring moreeee!!!!! the DC. God bless You ❤❤❤❤❤❤❤

  • @Maxcarcare-g1d
    @Maxcarcare-g1d วันที่ผ่านมา +1

    The DC 💥

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 วันที่ผ่านมา +1

    Bwana Bon Kalindo please muneneko za MSCE. Akukhonza ana a anthu olemera okha basi.

  • @lyiemax
    @lyiemax วันที่ผ่านมา +1

    Powerful ❤❤❤

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm วันที่ผ่านมา +1

    Mtengeri ukungalulatu !!!

  • @GiftBonomali
    @GiftBonomali 2 วันที่ผ่านมา +1

    The DC number one ❤❤❤❤

  • @ShaibuYussufu
    @ShaibuYussufu วันที่ผ่านมา +1

    The DC 🇲🇼 inuyo mumatiimilira nditu osana inuyo ndakatundu ulemu wanu kungoti bwana chosava ndi chosava basi olo mutachiyankhula motani sichingave ayi

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu วันที่ผ่านมา +1

    The DC mwana ooooooopsa kwambili ❤

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv 2 วันที่ผ่านมา +1

    More 🔥 🔥 the DC

  • @MAsd-r8s
    @MAsd-r8s วันที่ผ่านมา +2

    Ndipo anthu kuno akuvutika kwambiri, kuzunzika ku prison ngati aba kpn apha munthu. Akudya anthu slice imodzi ya bread kuno. Mulungu azikupasani moyo bwana kalindo

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 วันที่ผ่านมา

    I LOVE YOU ❤❤ BON KALINDO

  • @flimited-rw5uw
    @flimited-rw5uw วันที่ผ่านมา

    Born kalindo zikomo mumatiimilira zed its not easy u work so done ever.l salute.🎉

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n วันที่ผ่านมา +1

    The DC

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 วันที่ผ่านมา +1

    Koma achakwela inuyo Koma munayamba mutamvapo mau amulungu chifukwa zomwe zikuchitikazi sizoona chifukwa Chan mumafunan udindo kuti muzingotizuza zosezi mulungu akuona ndipo siku Lina azatiyakha

  • @user-ew8rp7wb1g
    @user-ew8rp7wb1g วันที่ผ่านมา

    ❤❤ thanks mr winiko god bless you

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam วันที่ผ่านมา

    God ahead u my brother

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwela anadya kale chilope

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw วันที่ผ่านมา +1

    DC

  • @user-eb2yo9bc9k
    @user-eb2yo9bc9k วันที่ผ่านมา

    Tilankhuleni zogulisa likoma the DC

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm วันที่ผ่านมา

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi

  • @HopeLuwangakaunda
    @HopeLuwangakaunda วันที่ผ่านมา

    Munthu mulala, mwana oopsa kwambiri President of the poor people BK tulutsa ndodo chonde

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe 2 วันที่ผ่านมา +1

    Guys tiyeni tpange mademo

  • @BassaamJumah
    @BassaamJumah 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma ndasekatu😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkkkkkkkkkkk koma the DC

  • @constancemkandawire7378
    @constancemkandawire7378 วันที่ผ่านมา

    Kodi akumazikozelaso mmisonkhanomu??

  • @user-lr2wx5xd9d
    @user-lr2wx5xd9d วันที่ผ่านมา +1

    The DC