ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Lipoti limeneli ngati chakwela , Richard chimwendo banda , zikhale ng'oma , kumkuyu , chithyola , valentino phiri komanso mai yoram , asakhuzidwemo that means kuti its totally fake .
Awuzeni abusa achakwela asunge basi,,,2025 kudzakhala commissions equally yeniyeni not manyakawayi
Ine ndiseka makutu anga ndisamve .zili menemo.
Zomatulutsa pakati pa uskuzi bwanji
isabwereso we don't need it
Watiuza kale Bakili muluzi TV kuti fake report likubwera ndiye aaaaa
Sungani report ilo tidava kale lfe
Undedi ngati sakupexekama achimwendo,autsi,kamajekete,kumkuyu chikangawa Hassan opanda duridwe dambwe, ose apezekemo anthu akupha
Fakis 😂😂😂😂
TIMVE MABODZA
Bola mupezeke chimwendo chakwela kunkuyu anthu okuphaawa
Ndipo totally fake