Hot Current Ubale wa Chilima ndi Chakwera Watani Lero

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ต.ค. 2024
  • #Hot Current Malawi#

ความคิดเห็น • 5

  • @Lawrencedickens
    @Lawrencedickens ปีที่แล้ว +1

    Mumakwana ,we love you too azibambo 🙏

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 ปีที่แล้ว

    Inunsotu apa muziyankhula zanzeru nthawi Zina mumayankhula mbwelela, mfundo yomwe ikubwela ndi Bon kalindo ndi m'mene situation ilipamalawi pano ndi munthu yekha opusa angamanganize kuti Kalindo akupanga zimenezi chifukwa choti akufuna udindo. Inu mungopwepweta apo mulaweluka on your table you will get food people they suffering here in village you don't know what you are talking about but we as the suffering malawians we need Bon kalindo and the Malawi first to help the country.

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 ปีที่แล้ว

    Pamkuku umandiwaza koma ndimadandaula kuseka kwa ranibo mmmmmmmmm koma izasegulidwaso

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 ปีที่แล้ว

    Rain bow ❤❤ ibwelerenso