Mayi Yolamu Try To Protect Your Legacy: Lamulo Lisamawone Nkhope Concerned Citizen

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 24 ก.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen reminds Inspector General of Police Merlyne Nachulu Yolamu that her duty is to the Constitution of the Republic of Malawi, not to the presidency or ruling party.
    Pa Nyasa VoiceBox, nzika yokhudzidwa ikukumbutsa Inspector General wa apolisi Merlyne Nachulu Yolamu kuti udindo wake ndi kutsata malamulo oyendetsera dziko la Malawi, osati utsogoleri kapena chipani cholamula.

ความคิดเห็น • 4

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mayi Yolamu sinzungu ayi osangoyankhula chichewa bwanji akulu

  • @JovitastoloBridane
    @JovitastoloBridane 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Udindo umene amalawi mudampatsa chakwera ndiumene iwowa akunyadola lifika tsiku limene adzalole ndikukuta manu

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Musiyeni Jezebelo yoo azinyang'wa nthawi yake izakwana azaona polekera

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi iwe mayi yolamu I hope you could take Ben longwe to court whats the hold up he said Muli ndizokoka and he will pull it up kodi iweyo zokoka zanuzo anaziona bwanji kapena mumachindana ? If you not supporting MCP Why not take him in