Kodi Aphungu Athu Amatiyimiladi Ife a Malawi kapena Zipani Zao?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 8

  • @andsenJeke
    @andsenJeke 7 หลายเดือนก่อน

    Ma judge opepera nso

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 8 หลายเดือนก่อน

    Aphungu athu amaiwala ntchito yawo chifukwa iwowo amaganiza za family yawo basi, komanso umpawi ndiumene uma wakula pa aphungu athu.

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 8 หลายเดือนก่อน

    Amaimila amalawi koma chifukwa amangotenga mbuzi za wanthu,bola mbuzi koma titi nkhumba.chifukwa, amaimila zipani zao,kuli kusaziwa ndale.

  • @MaxwellChiwaya-tv7kn
    @MaxwellChiwaya-tv7kn 7 หลายเดือนก่อน

    Majudge athu sakuchita bwino

  • @andsenJeke
    @andsenJeke 7 หลายเดือนก่อน

    Hrdc plus pac akuyenda ndi boma sakupanga mokomera amalawi

  • @AronGolden-t8k
    @AronGolden-t8k 7 หลายเดือนก่อน

    majudge anthu salibwino amakonda kulandira ziphuphu kuchokera ku mcp kodi bwanji malamuloayanganidwe malamulo abwere re amene anachotsedwa komaso plungeu

  • @AronGolden-t8k
    @AronGolden-t8k 7 หลายเดือนก่อน

    komaso phungu akachoka chipani chake ndiye kuti nayeso aturepansi udindo wake ngati phungu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน +2

    Zonyadisa kuti PAC,HRDC ndi amipingo anapanga chiganizo chogwira ntchito ndi boma 😢😢😢