Anthu akavota bwanji sakulembedwa ,olembawo akabwera olo mulipi 1 million akumalembapo anthu awili koma Ku central anthu 3 million akuuwamaliza tsikulomwelo
MA MPS OTSUSA AKUGONA KWAMBILI , ADPP LEADER OF OPPOSITION GORGE CHAPONDA ,WHAT ARE YOU DOING IN THE PARLIAMENT ? ANTHU OCHULUKA SADALEMBESE ZAUDZIKA ,KODI BILL IYIYO SIMUNGAIYAMBITSE KUMENEKO? TITHANDIZENI TIVOTE OPANDA CHAUZIKA AS LONG AS NDINE MALAWI AFUMUMU AKUNDIZIWA NDABADWA MUKUNDIONA OLO CHAUDZIKA PALIBE. CHOMWE AMEC AKUKAKAMILA ZOLEMBESA AKULEPHERA CHANI ? IS OUR RIGHTS TO VOTE KUTI TISHUZE PRESIDENT YEMWE TIKUFUNA ,KOMA AKATI AI MULEMBESE AKUSEKERA KUNJA MAVOTE AMUTHU WINA KT ASAWINE SPECIALY KUMWERA SALEMBAKO AT ADPP ASAWINESO AKUOPA MWANYAAAA TIVOTA WITHOUT CHAUDZIKA BOLA AMFUMU AKUTIZIWA
Amene mukutiuzanu mukapita ku Parliament, chonde, chonde mukamudzydzule GOTANI HARA pa ximene akuchitira ku Parliament posafuna kupatsa mpata ma MP a kumbzli yotxutsa kuti aziyankhula kspena kuperekz maganizo ao. AGotani Hara skutenga nyumba ya Parliament ngzti ya bambo ao( mskolo so. Chonde inu a concain citizen kageireni ntchito yanu mothandiza dziko lathu.
Good massage koma gotan Hala mukamuzuzule asamapange ngati kupariament ndikwaabambo Ake
Anthu akavota bwanji sakulembedwa ,olembawo akabwera olo mulipi 1 million akumalembapo anthu awili koma Ku central anthu 3 million akuuwamaliza tsikulomwelo
Good advise but time has gone😊
Good massage
Tha'ts what we need and your doing a good job.
Where is opposition parties after all of this scenarios?
Mfundo zenizeni izi .....Mr kambanje ....keep it up
Tisalole kuzavota pogwiritsa ntchito chawumzika please, tiwachitise manyazi agule amenewa
I salute keep it up
Thanks for the good advice 👍
You have spoken well ❤❤
Good message
Lets do it the way you said it's good idea
MULUNGU akudalitseni ndikukutetezelani
Continue
Zinezo ndimene zikufunika atsogoleni ngati inuyo tisanga mwamzelu
Good job mr Kambanje
We follow until the end , as Malawians we need action , not audio's , but mcp must out , enough is enough
Zikomo ❤❤
Zodya ena zimenezo we doing good
Chakwera akuyenela kuchoka basi ....chisilu cha munthu
Chonde chonde osarora kurandira chigumu mukapita kumeneko..chifukwa kungogona apa .tidziwe kuti agalu awa azabweretsa nkhondo mudziko muno chifukwa opposition siizarora
Zitayeni izi.Tili mmasiku omaliza palibe anakonzeka izi palibeeee
MA MPS OTSUSA AKUGONA KWAMBILI , ADPP LEADER OF OPPOSITION GORGE CHAPONDA ,WHAT ARE YOU DOING IN THE PARLIAMENT ? ANTHU OCHULUKA SADALEMBESE ZAUDZIKA ,KODI BILL IYIYO SIMUNGAIYAMBITSE KUMENEKO? TITHANDIZENI TIVOTE OPANDA CHAUZIKA AS LONG AS NDINE MALAWI AFUMUMU AKUNDIZIWA NDABADWA MUKUNDIONA OLO CHAUDZIKA PALIBE. CHOMWE AMEC AKUKAKAMILA ZOLEMBESA AKULEPHERA CHANI ? IS OUR RIGHTS TO VOTE KUTI TISHUZE PRESIDENT YEMWE TIKUFUNA ,KOMA AKATI AI MULEMBESE AKUSEKERA KUNJA MAVOTE AMUTHU WINA KT ASAWINE SPECIALY KUMWERA SALEMBAKO AT ADPP ASAWINESO AKUOPA MWANYAAAA TIVOTA WITHOUT CHAUDZIKA BOLA AMFUMU AKUTIZIWA
Tiyeni tiyeni anthu tonse tiwonese kwiyo wanthu anthu awa atitola kwambiri inu mukutiwunza moveka bwino
Ndizowona mawu abwino awa
ZOPUSA ZACHIDULE NDIKUCHOTSA CHAKWERA
Sure schoke ameneyi km amslawitu akuvutika mm