U T M is stlight people and with excllece people I'm proud with them,, sure truly surely thanks go on,,,,, Osaopa Osafoka,no fear no favours, but to stand on the bright side ❤❤❤❤❤❤
Mai kaliyati akutulutsa m'mfundo zeni zeni zogwira mtima bola asakupheni ifeyo tikusapotani ndi chipani chanu cha UTM limbani mtima nonse ku UTM gwiranani manja ambuye ndiwamoyo.
Mai Kaliati ulemu wanu.Chitani mgwirizano ndi DPP and other parties. After getting into the government partner with Russia ,EU ndi West are not there for good will of Africans.
Eti ase zosayenda angonamapo apa.akut ndalama zimayeneka kukhala kwa DC how ngat office ya Dc sikusamalidwa kuchita kumvesa chisoni ma office onse Malawi.koma zoona boma ingalephele kupempha ndalama ndikunga ma office a DC a standard ndikuwakongolesa bobo ndi kuikamo ma computer abwino aja za technology koma ine kumva chisoni kwambili nditafika ma office a DC.komanso ma office onse aboma ngosapasa chikoka kulowamo ngati usanze akut ndioffice ya munthu wankulu iyi mxiiiiii dziko lathu lansanje kwambili anthu akenso ife omvesa chisoni.sakhala chidwi ndikutukula dziko lathu koma kuba.amalimbana ndizinthu zopanda ntchito akut chitukuko kkkkk
U T M is stlight people and with excllece people I'm proud with them,, sure truly surely thanks go on,,,,, Osaopa Osafoka,no fear no favours, but to stand on the bright side ❤❤❤❤❤❤
Stay strong mother 💪💪 inuyo pitilizani ntchito yomwe Dr Saulos chilima amafuna kupanga.
You're my president, Mayi Kalia❤
Acheya aja osamawaphwekesa ulemu wanu acheya komaso mayi kaliati❤❤❤
Mai kaliyati 👏 umakwana keep it up 💪💪💪💪💪
Mbewu ya UTM itha kumela paliponse ndikuchita bwino.my vote.
Ndizoona
Inu mumatha mai wanga ulemu UTM oyeeeeeeeeeh moto kuti boooom🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
UTM my vote 🔥🔥🔥🔥
THAT'S MY MAM
Go on mama
Am the second one to comment
Mai kaliyati akutulutsa m'mfundo zeni zeni zogwira mtima bola asakupheni ifeyo tikusapotani ndi chipani chanu cha UTM limbani mtima nonse ku UTM gwiranani manja ambuye ndiwamoyo.
My vote
Mai Kaliati ulemu wanu.Chitani mgwirizano ndi DPP and other parties. After getting into the government partner with Russia ,EU ndi West are not there for good will of Africans.
Manganya ndiye anapha chilima ndi chakwela koma ife tilipambuyo pa utm nganganga
UTM ❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Supporting MCP is already a sin, so why stay in alliance with the devil 😈?
timakudalirani Mayi
Chakwera Chikangawa Lazaro osazayerekeza kuvotera agalu a Chikangawa
Amayi tikudalira inuyo, yigwireni utm
Ok
Potuluka ku dpp Umawoneka wochenjela,wakumana nawo Anzako,Akuwonetsa politics
This is not interview too much talkative kaliyati 😂😂😂
Ndipo palibepo chomwe chikumveka
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
UTM 💪
Atchewa amati yauka kutacha
Zoveka
Mayi ndimakunyadilani kwambiri mumaposa azibambo enafe ndinu odula mtengo wanu palibe angaufikire more.
She is all mixed up about China!!! Poor analogy!!!
Ine ndine wa dpp km ku utm ndikakonda chilima 😢😢😢😢😢😢😢
Khani yabwino kuyakhula kosawopa utm wooye
Good message Mayi kaliyati❤
Going back to dpp.
Kudekha kwanu kunaphesa munthu 😭😭😭
Kaliati more fire!!
Mzeru kupotsa president wa mcp
Wayakhula chani chomveka?
Kkkkkkk
Tell me how much money do you have in your pocket 😂😂😂😂😂
The same question asked by born kalindo to lea malekano 😂
utm akufuna kuchigawa ndi uyu yidasi sindimutchura ayi mukumuziwa
Vuto mayiyu wakhala pa bench osampasa unduna nthawi yayitali
Palibe chazeru apa muumoyo wanu mwakhara unduna kwabakili , bingu ,piter , tonse , sopano kunena zinthu zoduka muntu mupusise mafana mwaziwa liti?
Eti ase zosayenda angonamapo apa.akut ndalama zimayeneka kukhala kwa DC how ngat office ya Dc sikusamalidwa kuchita kumvesa chisoni ma office onse Malawi.koma zoona boma ingalephele kupempha ndalama ndikunga ma office a DC a standard ndikuwakongolesa bobo ndi kuikamo ma computer abwino aja za technology koma ine kumva chisoni kwambili nditafika ma office a DC.komanso ma office onse aboma ngosapasa chikoka kulowamo ngati usanze akut ndioffice ya munthu wankulu iyi mxiiiiii dziko lathu lansanje kwambili anthu akenso ife omvesa chisoni.sakhala chidwi ndikutukula dziko lathu koma kuba.amalimbana ndizinthu zopanda ntchito akut chitukuko kkkkk
She's just making noise palibe chomveka chili chonse.
Penapake mmmm zipani zose kuyendako nchani Kodi???
Palibe zomveka zomwe akuyakhula mayiwa. Akweni mwatani kodi aaaaa
chakwera is mr chabwera ndi chikangawa
Mum mumatha palibenso
5:09
Usi undisamale kwambili
Kukalamba nazo ndale
🤣🤣🤣🤣🤣
Anthu oyipa a mcp
the stupid presdant in malawi since ever
Mbuzi iyi
Itiyo kaliyatiyo kapena inayo
Mbuzi yake iti; iweyo kapena Chakwera?
Kaliyatiyo@@actuarialscience2283
Tambasulani mukuoneka mukumvanaye kutenthatu kaliyati.