Nyimbo ya Mlaka maliro ndayimvesesa pano akuti si uyu ngakhale amapemphera koma si uyu David tidikira mpana David abwere meaning yake ndayiziwa onse awa takhala tikuwayika pampando si achina David plz tisatope kuyesa David adzabwera
Si uyu by Mlaka maliro amalawi mveserani mwachidwi nyimbo ija ikunena zoona si uyu ayi David tisatope kuyesa David abwera plz tisabwereze zomwe taziyesa kale fisi ndi fisi musatenge america ndidziko lachuma kale lija
Anthu aku Dowa mudzisiyanitsa ,Kuti Michael Usi ndi vice president wa dziko komanso ndimembala wa chipani cha UTM kutengera ndimmene anapangira convention
Kuwaina athu akewo otse a kuonekeratu kuti agona ndi njala komatso mitu yawo siigwira 😂😂
A Malawi Pena pake tidzidzimvera chison zilizonse zopusa kumangoyimbira mmanja zoona?
Usi ndidolo agwetsa UTM komaso DPP muona naye nyenkhwe simunati zayambika chonchi kabambe achoke basi zavuta
Kwasala mezi 9 Kuti u Vice President uthe mwina sukuziwa tikukumbuse
Awa ndiye mabodza usi si wa UTM so mumufunilanji
Manganya ndi mbuzi yamunthu ukulimba ndi UTM osangoyambisa Chipani chako bwanji galu iwe
Ndi a MCP anthu awa palibe wa UTM apa
Koma usi ndimfuti osati masewela
Zopusa aaaaa Ife tifuna kabambe emweyo zinazo ayi
Amenewo simasapota a UTM,amenewo ndi aganyu
Eeee kma ngati kulikusaka ndalama mwafikapo anyamata inu, zikuchita kuonesa. Holy ghost fire....manganya munthu oyipa ndipo usamatchure dzina la mulungu iwe.
Mcp idusa moyela chifukwa opposition yongona ngati imeneyo
Awa anangofunako ndlama anthu omvetsa chisoni they don't even know what they're doing
Kuvara makaka a utm kuti mwina a Vice angawanyemereko kangachepe.
Malawi police yomvetsa chosoni kwambili
😢kodi ausi ndinudi aseventh day?
ndifunsireniko
Chokani aganyu inu😊😊
Inose ndinu zisiru bwana chifukwa amagura masamba musikamo tikukuziwani ndi a m cp koma manganya sazaramuraso u t m
Ndezikutathauz chani
manganya ndiwe galu
Mbuzi ndianthuwa komaso yemweatuma sakusiyana
😂😂😂😂😂 Zoona pali chanzeru apa ndani angagwedezeke ndi izi zaziiii awapasa ma pin uko tiyeni akakujambuleni anthu akuoneni zaziii koma amalawi mavuto sazathadi tisaname Usi akukoka anthu wa kuti apite ku mcp anthuwa sakuziwa moti amalawi ngati tikufuna kusintha zithu onse anayima kale asayimise tiyese zina inu plz
Nyimbo ya Mlaka maliro ndayimvesesa pano akuti si uyu ngakhale amapemphera koma si uyu David tidikira mpana David abwere meaning yake ndayiziwa onse awa takhala tikuwayika pampando si achina David plz tisatope kuyesa David adzabwera
Si uyu by Mlaka maliro amalawi mveserani mwachidwi nyimbo ija ikunena zoona si uyu ayi David tisatope kuyesa David abwera plz tisabwereze zomwe taziyesa kale fisi ndi fisi musatenge america ndidziko lachuma kale lija
MCP party sakudziwa ndani
Kkkkkkk manganya wawapatsa tima 10 thousand
A Manganya zipaseni ulemu musasokoneze Chipani cha UTM inu ndimunthu wamba Ku UTM musiye kuwaveka anthu a Mcp Maka a UTM musazitukwanise chonde
koma awa afuna chani makamaka akuna kukangana ndazizawo
Kodi mangaya akufuna chani munthu opanda nzeru
Chifuwa akudziwa kut ndizawo wa mcp
Apasidwa ndalama awa
Zaziiii
Anyamata azikwanje yawa
Tiziona eeee chaka chake mchino
koma ifeyo nkhope yathu yimene mkuvara ifeyo takubanja chonde manganya ukutirakwira panga zako chonde please uziva ukufuna tikafike kuti
Anthu aku Dowa mudzisiyanitsa ,Kuti Michael Usi ndi vice president wa dziko komanso ndimembala wa chipani cha UTM kutengera ndimmene anapangira convention
Amenewo simasapota a UTM,amenewo ndi aganyu