ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Maliro mpaka kuvula chipewa after mfumukazi kuonesa luso😂
Aku konsoma mungoyambitsa program yanu yamagule😅😅😅😅
😂😂😂😂 Koma Gututu nd Jemason ndinu madolo
Komatu magulewa aaaaa mfumumkazi yayambaso kubowa
Mfumu Muna wakoka mfumu kazi😂
Kom zamagulez zubhowetsa sewero lasiya kukoma aaaaa
Magule akubowetsa drama yabwino ija aaaa
ipatse moto
Kkkkk koma mercy uli mwano
Padera wavala nyau
Km magulewa sakundiwaza this comedy or zamagule
Proud of you Gututu and Jemason 😂😂😂 too much of traditional dances in this comedy please remove them.
Drama yabwino ija mwayiwononga why?
Padera waiphula
Mfumu nkazi mumatha,??
Apadela akufuna kubela munthuyo
Km magure too much why 😮 it's boring
Very boring 😑
Mangani malamba chibale sakokera mangani malamba😂
Ayi poti cosoma eti
Zakwathu?Too much of zamagule.If you value feedback, sinthani ndithu sizikukoma
Drama ngt Indian film mpka nyimbo ndye zachamba to ndisiyato ine kuonera
Magule too much
Maliro mpaka kuvula chipewa after mfumukazi kuonesa luso😂
Aku konsoma mungoyambitsa program yanu yamagule😅😅😅😅
😂😂😂😂 Koma Gututu nd Jemason ndinu madolo
Komatu magulewa aaaaa mfumumkazi yayambaso kubowa
Mfumu Muna wakoka mfumu kazi😂
Kom zamagulez zubhowetsa sewero lasiya kukoma aaaaa
Magule akubowetsa drama yabwino ija aaaa
ipatse moto
Kkkkk koma mercy uli mwano
Padera wavala nyau
Km magulewa sakundiwaza this comedy or zamagule
Proud of you Gututu and Jemason 😂😂😂 too much of traditional dances in this comedy please remove them.
Drama yabwino ija mwayiwononga why?
Padera waiphula
Mfumu nkazi mumatha,??
Apadela akufuna kubela munthuyo
Km magure too much why 😮 it's boring
Very boring 😑
Mangani malamba chibale sakokera mangani malamba😂
Ayi poti cosoma eti
Zakwathu?
Too much of zamagule.
If you value feedback, sinthani ndithu sizikukoma
Drama ngt Indian film mpka nyimbo ndye zachamba to ndisiyato ine kuonera
Magule too much