CRUISE 5 WITH PROFESSOR YUSUF JUWAYEYI - ARCHEOLOGIST

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ส.ค. 2024
  • Professor Yusuf Juwayeyi akugwila ntchito ku America ku Long Island University, Brooklyn komwe adayamba ntchito mu 2002.
    A Juwayeyi ndi katswiri ofufuza za mbiri ya anthu ndi nyama, pachingelezi Archeologist. Iwo afufuza zambiri mdziko la Malawi komanso kunja - ntchito yomwe imakhudza kukumba pansi kuti apeze mafupa aanthu ndi nyama zakalekale, komanso ziwiya zawo kuti amvetse mmene zinthu zinkakhalira kalelo.
    Pano a Juwayeyi alemba buku lotchedwa Archaeology and Oral Tradition in Malawi: Origins and Early History of the Chewa. Bukuli likukamba za mbiri ya aChewa, kumene adachokera, kumene adafikila kuno ku Malawi komanso makhalidwe awo amakedzana. Iwo akuti adafukula mafupa a aChewa amene adakhala ku Mankhamba. Akuti adapeza umboni wakuti aChewa anthawiyo anali achuma kwambiri ndi zina zopatsa chidwi zomwe alemba mu bukuli.
    Professor Yusuf Juwayeyi adabadwa ndikukulira ku Malawi. Aphunzitsako ku Chancellor College, Hunter College ya City University yaku New York komanso ngati oyesa mayeso a Archaeology ku University of Dar-es-Salaam ku Tanzania mu 1993.
    Anagwilako mboma ku Malawi ku Department of Antiquities mu 1989 kenako ngati Commissioner for Culture mu 1992. Mchaka cha 2000 anasankhidwa kukakhala kazembe wadziko la Malawi ku United Nations ku New York.

ความคิดเห็น • 49

  • @junaidiwen3422
    @junaidiwen3422 3 ปีที่แล้ว +4

    Very interested story and Chakhaza is the best journalist of Malawi ever 🤣

  • @emcgraw4858
    @emcgraw4858 3 ปีที่แล้ว +2

    What a brilliant man!!! Thank you Sir Chakhaza for bringing this amazing man on the show, my daughter has already ordered the book on Amazon!🔥🔥🔥👍💪

  • @cedrickpatrick4852
    @cedrickpatrick4852 3 ปีที่แล้ว +1

    Great job achakhaza number one fan of cruise 5 from Zambia

  • @aggiesize5355
    @aggiesize5355 3 ปีที่แล้ว +1

    Great Job Mr Chankhaza..... tadziwa Zambiri za ntundu wa chewa

  • @paulmtoliro545
    @paulmtoliro545 25 วันที่ผ่านมา +1

    Great

  • @julazdopekid7856
    @julazdopekid7856 3 ปีที่แล้ว +1

    Mesa baxi lero ndavomerezadi kuti #Wa chiyao Wangalusa....One of the most touching Stories n the top most Professors in a Foreign nationalz but still speaking all tounges of our Motherland...Big up Mjomba!!! MORE CHEERS...Ayao opita zija😍😍😍💪💪

  • @jephternelsononepengmail.c97
    @jephternelsononepengmail.c97 3 ปีที่แล้ว +1

    Proud to be Mchewa😄Mbiri yosachtitsa Manyaz we need part2

  • @andrewngowe8836
    @andrewngowe8836 ปีที่แล้ว

    Mu yao akaphuzira amakharadi ophuziradi thanks for sharing this

  • @paulmtoliro545
    @paulmtoliro545 25 วันที่ผ่านมา

    Amdala mmwejo mkambako. RESPECT

  • @rossbank7248
    @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว +2

    That's true chewas came from eastern Nigeria and Cameroon before Congo, nyau still practice in west Africa till today especially igbo tribe and it's called masquerades.. when the chewas came to Malawi they established maravi kingdom which was one of most powerful empire in southern Africa...

  • @fynessgasalamu3078
    @fynessgasalamu3078 3 ปีที่แล้ว +1

    Thanks Mr Chakhaza for this interview... apapa ndiye tikuyenela kugula book ilili

  • @m.ak.a8401
    @m.ak.a8401 3 ปีที่แล้ว +2

    Zikuoneka kuti tili ndi ulendo wautali kuti tiphunzire mbiri ya malawi

  • @medsonboti1984
    @medsonboti1984 3 ปีที่แล้ว +1

    I need this book, I love history very much.

  • @luissalcedo6493
    @luissalcedo6493 2 ปีที่แล้ว

    Professor Juwayeyi, you are the man!

  • @fatwelljacobphiri
    @fatwelljacobphiri 4 หลายเดือนก่อน

    Veey intelligent professor

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 3 ปีที่แล้ว +2

    A Chakhaza kulankhula chiyao 🤣🤣🤣u r very best journalist we hv these days in Malawi. Keep it up bro

  • @sendeza7696
    @sendeza7696 ปีที่แล้ว

    Very interesting

  • @morrisbwanali3524
    @morrisbwanali3524 3 ปีที่แล้ว +1

    This guy is great

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 3 ปีที่แล้ว +1

    Interesting wise man

  • @user-kx2pv9kd7y
    @user-kx2pv9kd7y ปีที่แล้ว

    Mmmm muyao sazatheka

  • @alickbanda6257
    @alickbanda6257 3 ปีที่แล้ว +1

    Mr Yusufu nipatali

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo1987 3 ปีที่แล้ว +1

    Very interesting man!

  • @hopezidana6851
    @hopezidana6851 ปีที่แล้ว

    Professor wanzeru uyu, speaking chichewa osati ma professor enawa amakhala akutiwalira Kaya, chizungu mbweeee

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 3 ปีที่แล้ว +1

    CRUISE 5 💪💪👊👊👍💕

  • @rossbank7248
    @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว +3

    Achewa si mtundu wamba ai that's why mitundu yambiri ku Malawi imapanga nsanje ndi achewa chifukwa amadziwa kuti achewa are more powerful than their tribes.....ndipo onse amadzinena kuti ndi angoni ku ntcheu,balaka kaya mwaza ndi achewa ambiri koma samadziwa ndiponso amang'anja akumwera ndi achewanso...

    • @victorkhonyongwa131
      @victorkhonyongwa131 3 ปีที่แล้ว +3

      Palibe mtundu wa wamba,every tribe is unique in a way

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 3 ปีที่แล้ว +1

      Zowona mkulu wanga achewafe samatifunila zabwino

    • @rossbank7248
      @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว

      @@victorkhonyongwa131 imagine ukulembatu chiyankhulo cha achewa apa pamene achewa samadziwa chiyankhulo cha mtundu wako

    • @rossbank7248
      @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว

      @@robsontyg3928 imagine 500 years ago azungu asanabwela achewa anali ndi government yao mu maravi kingdom...no wonder mitundu yambiri ku Malawi imadana ndi achewa chifukwa cha nsanje

    • @victorkhonyongwa131
      @victorkhonyongwa131 3 ปีที่แล้ว

      @@rossbank7248 Paja mtundu wanga ndi uti?

  • @user-hi3fb8ex4k
    @user-hi3fb8ex4k ปีที่แล้ว

    Ku nkope mu phili muja olo miyala ku nyanja kuja
    Bwana professor

  • @rossbank7248
    @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว

    He's right,Bantu came from eastern Nigeria and northern Cameroon....and chewa came from west Africa before Congo..

  • @luciuschigoga2607
    @luciuschigoga2607 3 ปีที่แล้ว +1

    Educated man

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 3 ปีที่แล้ว +1

    💙💙💙💙

  • @kassimjuma8822
    @kassimjuma8822 3 ปีที่แล้ว

    Ineso ndimuyowo wakumulanje koma anthu ndikawauza kuti ndine muyao amasusa chifukwa cha umbuli

  • @rossbank7248
    @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว

    Komanso kumpoto kuli achewa ndipo senior chief kabunduri in nkhatabay is chewa by tribe..

  • @rossbank7248
    @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว +1

    Those akafulas were pygmies and they are still in Congo forest today

  • @melodybashiriahmad914
    @melodybashiriahmad914 11 หลายเดือนก่อน

    I need the book

  • @bsowani5645
    @bsowani5645 3 ปีที่แล้ว +1

    Ngati palowa ndalama Za ma British mu book limenero mulibe zachilungamo

    • @rossbank7248
      @rossbank7248 3 ปีที่แล้ว

      Akulu vomelezani kuti mtundu wanu ndiotsalila no wonder mulibe chiyankhulo chanu ndipo mumalemba chiyankhulo cha achewa..nsanje idzakuphani ....

  • @rodgersmalemia4782
    @rodgersmalemia4782 ปีที่แล้ว

    sound yanu siribwino

  • @MrMwaiwathu
    @MrMwaiwathu 3 ปีที่แล้ว

    Could you please bring in Nanyoni....I actually don’t know her real name

  • @andy4christ991
    @andy4christ991 2 ปีที่แล้ว

    Audio ikupanga "echo"

  • @luciuschigoga2607
    @luciuschigoga2607 3 ปีที่แล้ว +1

    Very interesting