BON KALINDO LERO PA 18 SEPTEMBER 2024 |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 78

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali วันที่ผ่านมา +10

    Boniiiiiiiiiiii kalindooooooooo the DC 💪 ♥ ❤ ❤❤❤

    • @SueWahna
      @SueWahna วันที่ผ่านมา +2

      Kom ndiye khutukuved iiiih 😮

    • @GraykuffaMwazaGraykuffaMwaza
      @GraykuffaMwazaGraykuffaMwaza วันที่ผ่านมา

      😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊​@@SueWahna

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule วันที่ผ่านมา +3

    Thé Dc Bon kalindo number one ❤ good message

  • @janniferkachulu
    @janniferkachulu วันที่ผ่านมา +1

    Truth shall prevail. Love u DC.

  • @GiftMasamba-g8m
    @GiftMasamba-g8m วันที่ผ่านมา +1

    The Dc umatiimirila keep it up

  • @CBABBAS
    @CBABBAS วันที่ผ่านมา +2

    Our best TV

  • @BilalAliyah-k1f
    @BilalAliyah-k1f วันที่ผ่านมา +2

    We do hv president in malawi,

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Atsogoleri athu ziwanda zinawatseka mmaso komanso makutu maso alinao koma sakuona makutu ali nao koma sakumva ndi chifukwa malawi ali mmavuto opsa

  • @EneyaKakhobwe-tq3uy
    @EneyaKakhobwe-tq3uy 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Booooooni kalindoooooo the DC

  • @augustMag
    @augustMag วันที่ผ่านมา +1

    Bwana Boooon Kalindo president Chakwera mwamuyankhula mokwanira koma kusava kuli ndi president Chakwera Ndipo munamukonda kumuongolera koma mmmmmmm palibe chichitika palibe chositha awa sindikuuziwa kuti potenga boma la Malawi amaganiza chani? Ndipo ine sindikupeza yankho Leni Leni koma Mulungu sakutitaya atiombola Malawi panopo 😭😭😭😭😭😭😭😭 the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥

  • @ThokozaniMaulana-oi5hz
    @ThokozaniMaulana-oi5hz 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Booooooon kalindooooooo kkkkk machine bigy

  • @FiskaniTonymahone-vl3og
    @FiskaniTonymahone-vl3og วันที่ผ่านมา +1

    Andale awa sangakwanitse kusintha zinthu,kuyambira kukhala m'boma nthawi ya a Kamuzu kufikira pano..amangotsatira,alibe change for the goodness n better world..🎉

    • @user-vm3fw8yi2o
      @user-vm3fw8yi2o 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkk karindo moto kuti mbu!!

  • @MagretSimbah-v1u
    @MagretSimbah-v1u 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ABoni Kalindo Mulungu azikudalitsani.Kunena zoona kuyankhula ndipo mukuyesetsa,ndipo ine ndakhulupilira kuti chipani cha MCP ndichoipa kwambiri.Ndipo amalawi sindikudziwa kuti tithawira kuti.Boma iri likawinaso amalawi tiziifa ndi nkhaza.Ndinabadwa 1990 koma simnaonepo umphawi wa malawi ngati panopa.CHONDE AMALAWI TIYENI TIVOTERE CHIPANI CHINA OSATI CHI MCP AYI PLS😩😩😩😩💔💔💔😢😢😢😢😢

  • @JunaKananji
    @JunaKananji วันที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤❤❤karido Dc

  • @ElizahMadi
    @ElizahMadi วันที่ผ่านมา

    The DC, Boma ili litipha ,dongosolo lothandiza amphawi lilibe

  • @PromiseAllie
    @PromiseAllie 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😢😢😢😢 kma malawi eeeeee ndipite kuti abale ine kma

  • @user-re8es1ib7l
    @user-re8es1ib7l 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The Dc Boni kalindo ❤❤❤❤

  • @LonjezoChitseko-lx4qb
    @LonjezoChitseko-lx4qb วันที่ผ่านมา

    I would wish to join you guys,the strong Malawian

  • @MenasKaliati
    @MenasKaliati วันที่ผ่านมา

    Dangerous child keep it up good working

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie วันที่ผ่านมา

    Ku Malawi tilibe strong opposition 😢😢😢😢

  • @HaroldChadza
    @HaroldChadza 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    K a m u n a 💪💥

  • @sylviamsonthe
    @sylviamsonthe 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂
    Ati today here tomorrow there kkkkk
    Siku transport😂😂

  • @OliveaMapanga
    @OliveaMapanga วันที่ผ่านมา

    Big up kalindo

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 วันที่ผ่านมา

    Koma chakwera 😮😮😮 what kind of president is this 🤔🤔🤔🤔

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar วันที่ผ่านมา

    Andale akumalawi ndagalu

  • @patrickkapalamula2109
    @patrickkapalamula2109 วันที่ผ่านมา

    Ndi zomvesa chisoni zinthu zomwe zikufotokoza DC wina lero lomwe nkumati boma ndi pomweli. What a shame.
    DC mumatimilira ulemu wanu

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ambassador kusesa chilichose cha mnyumba kkk

  • @GeorgeKapito-um2wl
    @GeorgeKapito-um2wl 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thats very true...

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Za pension boma la chakwera ndi chiphinjo choopsa opuma ntchito mboma mpaka zaka ziwiri ena zitatu osalandila ndalama zawo shame on mcp government

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkk ambassador wà ku Malawi anaba katundu wa ku zimbambwe eèee zoòsyatu izi .kodi ndi a zikhale Ng'oma olo a cĥmwendo Banda !!, koma kusaukaku. Kùangitsà mànyàzi boma ndi dziko lomŵe

  • @user-tk6wf2eg4z
    @user-tk6wf2eg4z 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Why malawi no action mu boma iliri why malawi wake up malawi and let's to do action

  • @BandahLemos
    @BandahLemos 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Thanks mumatiimilira Akalindo

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tamusiyrni yekha born kalindo yo aziyankhula kaye nkumaliza osamaikapo dziwe online tv inw mmandibowa bwaanjii

  • @VanPaul-sv9yx
    @VanPaul-sv9yx 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vutoso ndi Amalawife tinagunata kwambiri chifukwa nkhalidwe lopusali timalionelera ndikumangodandaulira ma social media, uchisiru umwe umachitika kwathukuno mayiko ena anthu samayang'anira zopusazi

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw วันที่ผ่านมา

    Ndipo ndi owopsyadi that's why amaphana pa chibale

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ku Southern Region simulandila ntukula pakhomo chifukwa ndinu a DPP bwerani ku MCP

  • @IsaiahKapinga
    @IsaiahKapinga วันที่ผ่านมา

    Koma a DC m'zipatalamu odwalaso akuzunzika kwambiri komaso ku NRB ku Blantyre eeeeh kuli mavuto anthu kumangobwererako

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ADYERETU CHIKANGAWA KWAKE KWATHA

  • @lyiemax
    @lyiemax วันที่ผ่านมา

    Boma lomvetsa chisoni kwambiri

  • @EmmanuelMtonya-j7b
    @EmmanuelMtonya-j7b วันที่ผ่านมา

    Boni tamuona mdzako manganya pomwe Ali rero . Sidzimakupweteka mutima mwako ndalamatu zimadana ndi phokotso dzichepetse manganya akuthandidza apo ayi udzakalamba ulibe chilitchonse zivere chisoni zoona iwe udzigokhalira kuyendera ku Court thawi dzontse n

    • @Evancemdoka
      @Evancemdoka 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kod ukamaona akuyankhula izi umaona ngati amangona ndi njala? Fufuzani kaye muzabwelenso

  • @IsaiahElesoni
    @IsaiahElesoni วันที่ผ่านมา

    My Malawi kodi chenicheni ndichani?

  • @Schoolfees10
    @Schoolfees10 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ana anjoka

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er วันที่ผ่านมา

    Chakwera ndi mkozi yamunthu kwabasi

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ineyo Koma nkhawa zanga ndi zipanidi zotsutsa
    M'chifukwa chiyani azitsogokeri athu omwe timati mwina atipulumutsa 2025 Ku Satana ameneyu angoti nziii!

  • @ChristopherChapeta
    @ChristopherChapeta 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    De dc ndinu Katundu

  • @modestermafavouritedumadum2888
    @modestermafavouritedumadum2888 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndodo yasowa by mlaka 😢😢😢😢

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 วันที่ผ่านมา

    Chakwera ndi president osanva kulangizidwa

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude วันที่ผ่านมา

    Ankhutukumve😂😂

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmene chikangaŵa wachokamu. Matsoka ake asiya kuti apweteke / alodze / aphe amalawi otsalafe mmalawi muno..komatu zisatheke .ndipo ku ungako asakatenge devaluation wakeyò. Amalawi tàkana devaluation ili yonse ..wamva iwe chikangawa!!?

  • @EbrahimMastar
    @EbrahimMastar วันที่ผ่านมา

    Dziwe 1

  • @user-qu5ks3kk6v
    @user-qu5ks3kk6v วันที่ผ่านมา

    Ah koma chakwerayu guys ndi munthu oyipa mtima kwambri

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc วันที่ผ่านมา

    Akut screen yachombo 😂😂 Koma ziliko Chaka Chino

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 วันที่ผ่านมา

    Chisoni Chamuna achakwera

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj วันที่ผ่านมา

    Namayenda aona polekela

  • @VajraBanda
    @VajraBanda วันที่ผ่านมา

    🎉🎉🎉🎉🎉😮😮😮

  • @TonyMpate-by9gp
    @TonyMpate-by9gp 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma aMalawi tidzadzuka liti ?? Kweni kweni mukufuna tichite kufika podya dothi Kuti mudzadziwedi Malawi akuvutika???? I wish ukanakhala Kuti dzimatheka munthu kudzigawa pa 100 times ine nkanadzigawa ndekha popanda ondithandidza nkupita pansewu ncholinga achoke chikangawayi

  • @willardmasamba4639
    @willardmasamba4639 วันที่ผ่านมา

    Malawi alipa moto

  • @LovemoreCathy
    @LovemoreCathy 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tinkawona ngat m'busa atithandiza koma ayi manyakaaa eni eni amunthu!!🚮

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb วันที่ผ่านมา

    Ife kuno ku mzuzu dzulo mafuta tinalibe

  • @GiftMukhova-y1p
    @GiftMukhova-y1p วันที่ผ่านมา

    The DC

  • @SueWahna
    @SueWahna วันที่ผ่านมา +1

    Kom ndiye khutukuved iiiih 😮

  • @kaungabondera892
    @kaungabondera892 วันที่ผ่านมา

    The dziwe tv inside the speech of kalindo is always distracting and boring

  • @Chisomochimbiya
    @Chisomochimbiya วันที่ผ่านมา

    😢😢😢

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm วันที่ผ่านมา

    Munalakwitsa ndinu amene lero mwazindikira tsopano

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 วันที่ผ่านมา

      Kulakwa nde kwamunrhu

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga วันที่ผ่านมา

      Zimenezo nde zoona

    • @MarkGonda-qr4vm
      @MarkGonda-qr4vm วันที่ผ่านมา

      @@inessmsiyambiri8517 yaaa koma anachita mistake yaikulu pano akuzunzitsa amalawi

    • @MarkGonda-qr4vm
      @MarkGonda-qr4vm วันที่ผ่านมา

      @@AngolanChinga azunzitsa amalawi

  • @JonathanKamoto-h1p
    @JonathanKamoto-h1p 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Auzen Dc

  • @AndrewChilambo
    @AndrewChilambo 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera sazava

  • @LonjezoChitseko-lx4qb
    @LonjezoChitseko-lx4qb วันที่ผ่านมา

    Mr kalindo please number yanu perekani

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l วันที่ผ่านมา

    Andalewa sakhaniza bwino, uyu vuto anaipisisa kwambili ndi gulu lake lonse amene amamusatila , koma aaah Mulungu ubwino wake alipo akuona ikakwana nthawi yake yoti at least osauka azapezako bwino basi

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl วันที่ผ่านมา

    The DC