Only my words goes to that woman katerina ,what comes around goes around. Iye analanda nzake ,nthaw yake yakwana naye walandidwa. Just the way it is nyimbo ikhale imeneyi by joe gwalad
I didn't expect this from DAN LU But I just want to share you my advice girls are dangerous don't just see the beauty Beauty is nothing But heart is what matters
Akaterina mumkat mwapambana 😂 kukwanisa kuononga banja laeni iiiiish nde paja tu amat wachake ndiwachake zimenezo mama zisapweteke chimakoma chili kwa zako yomweyo galu iwe
Banja ndi chibwenzi ndi zinthu ziwiri zo siyana, achina Gibo Pearson amazembera zibwenzi zawo osati banja, simungawa fanizile ndi Dan lu and Queen Sheba anthu oti ali kale ndi ma komo awo okhazikika.
Koma malawi timakonda kukamba za munthu emwe watchuka taonani Diamond platnumz ku tanzania akungogwila ti akaz kumeneko akumuweluza ndani koma danlu kupanga nao nkhan mpaka pa milandu inu osangozisiya bwanj ngati mukufuna inunso pangani akaz alipo m'mangochi bomamo ndiye kwathu kumeneko Wachiyao wangalusa bulasa une Muyawo
😂😂😂😂kukwatila sheba nchimozimozi kumwa chisime chosavindikila aaaaa mkazi osazilemekeza ngati uyu 😂😂😂mmemo wa gulu
Only my words goes to that woman katerina ,what comes around goes around.
Iye analanda nzake ,nthaw yake yakwana naye walandidwa.
Just the way it is nyimbo ikhale imeneyi by joe gwalad
Kuvuta
Kudandaula kwawina kumapeleka vuto kwa munthu winaso we hv to remember that
Amuna nda galu
Man a dog's
True eti
Zovutatu iiii
Amuna otchuka alibe chkond kwao nkudziwa kunyenganyenga. Katerina osalira ai coz mamunayo nd wa Emmie. Chaona mnzako chapita tomorrow chili pa iwe. Dan Lu chomwe akufuna sitikuchdzwa... Queen Sheba kunyasa kuli thooo kkkkk pulixin upole moto
Kama Dan amatha kukhumudwisa akazi mmmmm oko dikukonda ayi
God bless the first ex wife of Dan,mkuluyu ndifoyira basi ndikale zedi
Tsono achimwendo athana ndi uti pamenepa
Eeh kma tu Dan lu😂 kmaso a katerina amkati apeza mamuna ii chipwilikiti 🙌
I didn't expect this from DAN LU But I just want to share you my advice girls are dangerous don't just see the beauty Beauty is nothing But heart is what matters
Komanso acording to my experience sheba sangamake pa cate anzanga mukuwona bwanji
Akuchifunacho sadachipeze chikapezeka tizachiona ndinthu, munthu umati pasa malangizo kom iwe suchita nawo 😊😊ayi zikomo
Eeh ku malawi mkokoma 😂😂a Dan lu apapa mwatha ndukuuzani😑zagulu
Azibambo mukupanga zibwezi chosechi ndinu okwatila ndiye dun lu wapambana chani yeyo😂😂
Yaa timasangalala nanu mumaripasa nkhan zongochitik kumene koma sinathe coz ayimbas limodz zikut bwanj pamene pa koma headline Mwat Queen Sheba wasuma koma sitinamvepo
Komatu queen Sheba ndiwonsokoneza poyamba panja adatseketsa Church pano ndi uyu wansokoneza banja la munthu uyu akumfunika kumuchotsa ziwanda
100% Dan lu Katerina amawona ngati iye wapambana wayiwona Malawi 😂😂😂😂😂 wadya nawo makombo 😂😂😂😂😂😂😂
this guy done room was so good and tema
Asiye kuimba Za chikond angabalalise anthu maganizo
Ndimayikonda video yakho kwambili koma isikhala yayithali
Zonvetsa chisoni kwambiri and its ashamed for our dun mkazi alinayeyo noooooooo pls brother dun .
Akaterina mumkat mwapambana 😂 kukwanisa kuononga banja laeni iiiiish nde paja tu amat wachake ndiwachake zimenezo mama zisapweteke chimakoma chili kwa zako yomweyo galu iwe
Ayi nanexol waonjeza😂
Pat of life katerina don't worry uzampeza mamuna wabwino
😂😂😂😂ukalanda zako naweso umalandidwa nyekhweza
A Dan Lu apa ndiye mwatha basi mpaka queen sheba aaaa zaugalu
mupitilizetu siinathe sinanga aimba nyimbo limodz anthuwa
Dan lu ndi emy unapasa mwai wakulu pano sungafikepo paiye
Akazi onse oipa kwa bulu wawo 😂😂😂😂 ndaa amate, mkazi akunena yekha kut iyeyo ndi Q sheba, 😁😁ngat adasokoneza Solomon iwoso kuntha ndi kumwe ko bas 😏😏
Eeeeee koma zovuta Adan athela manja mwamahule sure
Kuthatu kumeneko😮
Akufunika mapemphero Dan Lu amvula akazi angati yooooo
Cholanda nawe umalandindwa pangatalike bwanji chifukwa chithucho chisako chamwini.
Sikuti ndizolesedwa mamuna kupeza chibwez alipabanja ayi,kma sinkaz wake ovulavukayu😅
Umve kusiya akazi okongola kukagwila khwangwa mmm dan lu mavuto ..amafuna azikaziwo azimphatsa ndalama
Wachyao asenemitala😊 9:05
Wow 😳😱😯
Dan lu akufunika mapephelo apadela dela otherwise sheba ndi nkhwagwa for sure
Queen sheba Ndiye Chan aaaaa
❤❤
Kod tv imeneyi Ingoweluza bwanji
Queen Sheba chiwanda chomvolamvola
Osadandawula mom.mutae basi zachitika
Koma dan ndi galu 😅😅😅😅😅😅
Sanapange chisakho cabwino zili ngat kusiya spesho ndikutenga kachasu kupenga nazo
Koma mpaka eish😂😂😂😂😂😂
Awa nda hule zedi amuna ena ndima hule indee kom awa eshiiii 3 much 🙄🙄😏, bwanji osakwatila or 10 mwina zikhoza kunthandiza
Olanda amalandidwadi
Komatu mwangokamba za ubwedzi wao
Why ximumanena kt anthuwa amapanga recording song yomwe yatuluka kumenei
Uhule ndi mtima anaimba ija anaziimba yekha coz Dan Lu ndi hule
Koma queen Sheba ngonyasa nkhope guys
Banja ndi chibwenzi ndi zinthu ziwiri zo siyana, achina Gibo Pearson amazembera zibwenzi zawo osati banja, simungawa fanizile ndi Dan lu and Queen Sheba anthu oti ali kale ndi ma komo awo okhazikika.
Kupedza Daniel usaikirepo mtima kt wapez mamuna uzadwara mutu wachingrangra
Wapepezatu uku😂😂😂
Nice
Achitabwino Danlu azimwa bwino ma ARV
Akakondana alekeni😂
Wow 😳
Wachiyao wangalusa zopano agwila sozagwilika😂😂
Wachiyao watha bs😢
Anatero kale part of Life musaiwale
Wachiyawo wangalusa
Mmmmmmmmm inu ok tapelekani mayina awoyimba amene Ali ndimabanja okhadzikika pamalawi ngati Pali anthu opanda tsogolo pamalawi 1 oyimba 2 mapuleya osewela mpila wamyendo amakonda zinjoyi amafuna akhalenso wochuka woziwika paliponse nawonso adzikazi amakhala akulunjika komweko
Lucius Banda
Umatiimilira Sam, well explained
Nice one
Koma malawi timakonda kukamba za munthu emwe watchuka taonani Diamond platnumz ku tanzania akungogwila ti akaz kumeneko akumuweluza ndani koma danlu kupanga nao nkhan mpaka pa milandu inu osangozisiya bwanj ngati mukufuna inunso pangani akaz alipo m'mangochi bomamo ndiye kwathu kumeneko Wachiyao wangalusa bulasa une Muyawo
kwachema😂😂😂
Kukwatila kwatila siudolo amwene?
😅😅😅😅😅Museka
Mmakwana
Kkkkkkkkkkkkkkkkk zama Love🤣🤣🤣
Queen Sheba ndi osakongola kunena zoona
Koma a Dan lu mumafuna chani kwa Queen sheba yo, Ufiti???
Life is so hard to you Katerina
Oranda arandibwe❤❤❤
Mamuna olanda mzako sanyadila chifukwa wina mawa adzakulandaso.
Kusaugwira ndima
𝐝𝐚𝐥 𝐥𝐮𝐮 𝐓𝐨𝐨 𝐦𝐮𝐜𝐡 𝐮𝐡𝐮𝐥𝐞
Kmt dan lu eeeeeeeèe kutosa tosa
Wow
Eeeeeee km yah 😂😂😂😂❤
Lu kuchoka mu mbale kukagwa mulichero lobooka
Wataya nkhuku ataona mawanga ankhwali
Koma olanda zake nayeso azalandidwa
Ngati.mkotheka.bwelelan.zinazi.mmm
Dan lu ndigalu kwambili ndithu
Dan amaonjeza
Apa nde wapanga zachamba aaaaa
Dan luu wasiya mkazi wake
Ndixoveka ndiye mamunayo ameneyo
Mesa akuti ndinyimbo
Ndimomwe zimakhalira wolanda azalandidwa
Wayiphonyatu apa Daniel
Eeeee zafikapo
Paja wapepesa tu Dan lu
Olanda naye amalandidwa
Dan Lu waonjeza
Uchitsiru nde umeneu
Dan lu ndi galu
Poto ndi Mkati mbuyanga Mabvita
Kumalawi mamuna ndi onyengaye
Koma Dan lu nayeso abale
Your not serious
❤