ISRAEL CHINGA MOFFAT - Interview On Makosana with Mary Moyo

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
  • #israel
    #chinga

ความคิดเห็น • 60

  • @miraclechinga5407
    @miraclechinga5407 ปีที่แล้ว +4

    Very true mwana wakwathu yu mmh ndimwana ovesesa ozichepetsa komaso olimbikira he is teaching me alot,he is special and talented Ambuye akufikitse komwe ukufuna iweyoo🙌❤️ Extraordinary Yahweh he is God

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว +2

    Mwana uyu eeeeeeeeeee anakoza ndi fire zedi ndiozichepetsa, wanzeru komanso ochezeka, keep it up bro

  • @emmanuelkampira6950
    @emmanuelkampira6950 ปีที่แล้ว +1

    I have learnt alot on this interview.
    Keep good work Israeli

  • @Loytee463
    @Loytee463 ปีที่แล้ว +2

    Adha awa muli nzeru ndipo amaziwa chochita analeledwa bho❤❤

  • @user-pm4wi8pb4o
    @user-pm4wi8pb4o ปีที่แล้ว +1

    Appreciate to you mwana wa ng,ono km uli ndipotetial and vision

  • @user-gs4os7cy5s
    @user-gs4os7cy5s ปีที่แล้ว +1

    I respect you my brother islael munthu oleredwa ndi agogo ake sakhala munthu wamba pitiliza kukhala ndi moyo ozichepesa ndiwe munthu okonda aliyese ndipo supasa anthu Bluetik 😂😂😂😂😂 mulungu apitilize kukusamalira kuti uzafikile pomwe iwe ukufuna much love from this side 🎉❤🎉🎉

  • @enockchinthenga894
    @enockchinthenga894 ปีที่แล้ว +1

    Mwanayi amasogozedwadi ndi mzimu oyera.. pitiliza kuika mulungu patsogolo young man

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว +1

    Ndipo ndendendedi Amai ake zedi eeeeeee thank to God anatisiira mphatso yabwino zedi ndithu

  • @user-frasernamaona14
    @user-frasernamaona14 ปีที่แล้ว +2

    Munthu wanzeru heavy; God bless you.

  • @miraclechinga5407
    @miraclechinga5407 ปีที่แล้ว +5

    Thats my brother❤️ ndiwe dolo

    • @israelchinga5068
      @israelchinga5068 ปีที่แล้ว +1

      Thanks alot sister yo so supportive and a loving sister

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว

    This guy is really amazing and he's blessed and God got more nlessings for coz he's hamble🙏🏿🙏🏿

  • @laurankhana9833
    @laurankhana9833 ปีที่แล้ว +4

    Munthu wokula ndi agogo amakhala wanzeru ngati mumene ulili iweyo ndiwe mwana koma uli ndizeru pitilizani kuwakonda agogo aja nose mumawakonda pitilizani kukondana mulungu akudaliseni

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว

      Ndipo koopsa zedi, Agogo ndi deal zedi or utati wakura ndi amama okhanso ndi deal

  • @wallycan
    @wallycan ปีที่แล้ว +2

    I can't wait 😊

  • @user-we7xg1mf7u
    @user-we7xg1mf7u 7 หลายเดือนก่อน

    I support ur desition,it happens also to me focus with your life brother

  • @user-qh5ib6ww7v
    @user-qh5ib6ww7v ปีที่แล้ว +1

    Keep being a humbled guy israel u r sensitive 🎉

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 ปีที่แล้ว +1

    Keep up young talented boy

  • @BestIcons-sh9lr
    @BestIcons-sh9lr ปีที่แล้ว

    This is great I like this boy he is so talented

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว +1

    In this interview i have learn a lot and thanks guys for organising this ❤❤❤❤❤❤

  • @UlondweSchool
    @UlondweSchool 2 หลายเดือนก่อน

    Very intelligent guy I like you bro, may God bless u

  • @user-pu6ym8ll1f
    @user-pu6ym8ll1f ปีที่แล้ว +2

    ❤fanai ndiozichepesa

  • @Chikuliffa
    @Chikuliffa หลายเดือนก่อน

    Mfana woganiza bho

  • @user-pm4wi8pb4o
    @user-pm4wi8pb4o ปีที่แล้ว

    Much appreciate to you big up uli ndi good vision and potential

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว +1

    Mama akodi palibeyi angawakwanitseyi Koma ndikanakonda Miracle akanalimbikira kuti azafikepo, ndikhumbo langa

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว +2

    Ambuye apitilize ntchito ayambayi kwa iweyo

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว

    Ndipo ndiozichepetsa koopsa zedi ndiosiyana ndi azibale ake onse ajaa uyuyu ndiwina eeeeeeeeee Mbambande zedi brother Israel iwe ndie ndiwathuwathu Mbambande zedi brother

  • @SandasonLuwemba-lh3hj
    @SandasonLuwemba-lh3hj 8 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ I love you so much my brother

  • @JerryNcube-gt3te
    @JerryNcube-gt3te ปีที่แล้ว +1

    Keep it up my boy timakunyadila always

  • @JamesKavalo
    @JamesKavalo ปีที่แล้ว +3

    The guy is so humble

  • @GanizaniBalon-ie2oq
    @GanizaniBalon-ie2oq 5 หลายเดือนก่อน +1

    Humble guy

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 ปีที่แล้ว

    Mwana wa agogo kkkkk grace mzimu wako upitilire kuusa my mtendere

  • @centrudasibande
    @centrudasibande 11 หลายเดือนก่อน

    The guy z amazing

  • @jimmyalumando3785
    @jimmyalumando3785 ปีที่แล้ว

    Ine pheee mundipeza pamenepo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 ปีที่แล้ว +1

    Nde nde nde a mako mwanawe kudzichepetsa ambuye akutsogolere mwanaweee

  • @jumakananjirazim
    @jumakananjirazim 8 หลายเดือนก่อน

    Cool guy

  • @winneschikwakwa
    @winneschikwakwa ปีที่แล้ว

    Koma nde kuchedwatu yakwana mesa

  • @chebuaarts
    @chebuaarts ปีที่แล้ว

    Nfana odekha

  • @Malambia
    @Malambia ปีที่แล้ว +1

    He is very hamble

  • @Malambia
    @Malambia ปีที่แล้ว +2

    Your ginius adha

  • @Kidbuba14
    @Kidbuba14 ปีที่แล้ว

    Nzathu

  • @user-bh4ge9ej5t
    @user-bh4ge9ej5t 6 หลายเดือนก่อน

    🙏

  • @israelchinga5068
    @israelchinga5068 ปีที่แล้ว +1

    ❤️❤️❤️❤️🔥

    • @EllamariaKaliya-tc2es
      @EllamariaKaliya-tc2es ปีที่แล้ว

      Mulungu apitilize kukutsogolera ndikukupatsa nzeru zodabwitsa mwana wanga. Pitiliza kudzichepetsa ndikudalira pa Mulungu. Kupemphera patsogolo.

    • @wezimandelumbe4013
      @wezimandelumbe4013 ปีที่แล้ว

      @@EllamariaKaliya-tc2es Amen

  • @paulmapepa9094
    @paulmapepa9094 ปีที่แล้ว

    But what ever happened to his face anazilakwira ...

    • @miraclechinga5407
      @miraclechinga5407 ปีที่แล้ว +1

      He dint do anything zinangobwera atayamba kukula so please mind what you say mungotenga nazo sambi chifukwa palibe zimamuwaza so the face will be ok with time mind you thank you

    • @paulmapepa9094
      @paulmapepa9094 ปีที่แล้ว

      @@miraclechinga5407 alright noted with thanks and now tadziwa

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว

      ​@@miraclechinga5407Fact boss

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq ปีที่แล้ว

      ​@@miraclechinga5407Thanks wayankha bwino coz Israel wafotokozatu bwino bwino kale nkatimo akuti sanafune sanachiteyi kupanga Koma zilonda Ndie Ku studio ko anangopanga okha mwina amafuna achotse sunguzo. Ndie uyoyo Kaya bwanji vuto kunva ena kumawavuta zedi