BON KALINDO LERO PA 30 SEPTEMBER WADABWISA ANTHU AMBIRI NDIZOMWE WAYANKHURA ZOKHUNZA SAULOS CHILIMA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 29 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 64

  • @twaibupatrick-k1n
    @twaibupatrick-k1n 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Chilima anaphedwa alindizoyankhula zambili koma palibe wina aliyese amene amadziwa kuti amafuna kuyankhula kuti chani koma mary chilima akudziwa zomwe mamuna wake akafuna kuyankhula ndiye tiyeni timulimbikise apange ndale coz mamuna wake anali wandale

  • @jameslifah7909
    @jameslifah7909 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Justice for SKC and all fallen heroes who were in that plane💔

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +10

    Nkhani yoti Mary Chilima alowe ndale sindinagwilizane nayo koma iyi yokha yoti akusakasaka chilungamo pa imfa ya mwamuna wake, I support her 100 %

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Akukasaka kuti

    • @billymhoni9527
      @billymhoni9527 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

      Iye uja ndi wa ndale kale inu mukungomuoopa coz mai uja akadzuka nkupangisa mtsonkhano chingachitike nchiani we need mama mary to rise up

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

      Mutanthauza chani poti Mary Chilima ndi wa ndale kale sadalengezepo zoti adasiya ndale

  • @christinemudziviri8398
    @christinemudziviri8398 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    God of vengeance, please intervene for us. Be strengthened Madam Chilima

  • @favours8
    @favours8 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Ndipo Ndikupephela Kuti bushili , chakwera ,Joyce Banda , ndi team yawo yonse ya satanic sindikuopa I don't follow politics , But am warning them , fuko Langa , mtundu wanga akuonongeka, because of them , Prophet bushili prophecy Kuti anthu omwe anagenda chakwela amwalila , and am here to warm bushili he must stop his nonsense...and alape .. akupha anthu kuvala chikopa cha nkhosa kuja nkati Ali mkango .. prophet wa bodza am also a woman of God and am trying all my best Kuti ma message amufike bushili Ngati amapha anthu , ineso am ready to dies for God's work ..my life is useless if mfuko Langa , mtundu wanga , akuonongeka , let me warn dziko lamalawi , tilape anthu akuonongeka chifukwa of lack of knowledge, I send this to all bushilis followers, Ngati mulibe mzimu wachidziwitso you are following Satanism people...my heart bleeds ...

    • @Blessings-b7h
      @Blessings-b7h 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      There are so many people who don't know that Bushiri is afake prophet.Joyce Banda,Chakwera and many others they are in plot and may malawians are suffering because of these people.

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Bon Kalindo 🔥 sukunama. Mcp yamutukwanadi mary

  • @Maxwell-b6q
    @Maxwell-b6q 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Rest in peace SKC. Mary Chilima osaopa, osafooka, osatopa.

  • @PatrickMangochi
    @PatrickMangochi 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Commission of inquiry ndiyosafunikira,zikuoneka kuti Winiko ali kale ndi umboni choncho akuyenera akatsegule mlandu wa murder ku court

  • @favours8
    @favours8 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Tikupephela ma plan awo akumidima satheka .. ndipo i stop all the evil altars that wants blood mu dziko langa ..sindisatila ndale ayi , koma zikundiwawa zedi mtima wanga kusweka. Mulungu wathu atikhulukukile , tilapile malawi ndipo fear not , kudziko lakumidima , akupanga ma meetings okhesa mwazi pa zitsakho koma i stand on the holy altar of God , amwa magazi awo , adya nthupi lawo , yesaya 54 vs 17 ku dziko langa .mtundu wanga

  • @AnnieKalipo
    @AnnieKalipo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mai Mary chilima akuyenela kulimbika mtima , Ndi njila yokhayo imene ingapangitse Kuti chilungamo Komanso chipambano chioneka . Ambuye amusogolele Mai wathu ..

  • @AlijuMikayilu
    @AlijuMikayilu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bon kalindo kunena chilungamo chene chen mulungu alinafe amalawi osadanda chakwela timuonesa nyekwe pa 2025 ndiboma lakelo lakumpa

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ine misozi imangotuluka ndikamaona zithuzi za achilima,analakwanji anthu awa

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi zomwe wayankhula Mary Chilima a mcp zawanyasa chifukwa chani

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Vuto ayeni mtundu munafatsa nkhaniyi ikanatha kalekale koma inuyo munali duu ndie anthu sangachite kanthu popanda ayeni mtundu.Apapa ndie mwayamba kudzuka tsopano.

  • @BryantLusungu
    @BryantLusungu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Amaonangati akhalachete

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Marry Chilima To come out Can Shake the Whole Nation She Is Neutral last Minute MALAWI Could become Canaan. We are afraid to push her due to big loss, A Husband , not A joke But her response Can Raise The nation to EXPECTED CANAAN AS HER HUSBAND VISION
    MANY REFORMS WERE DONE BY SKC
    Looking forward to This proposal.

  • @chimwemweshadrick5972
    @chimwemweshadrick5972 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bon Kalindo....... !!! the national speaker to the cursed country with the innocent blood of the late VP and other fallen heroes. Justice.... Justice

  • @Mbeta-q8v
    @Mbeta-q8v ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine si Mngoni koma tsiku lina tilalamulidwa ndi mayi wa Chingoni
    Hee heee sindikuseka koma kusekerera
    UTM
    Doctor Saulos chilimaaaà
    Tonse amalawi pambuyo pa U TM nyomiiiiiii

  • @augustMag
    @augustMag 10 นาทีที่ผ่านมา

    Mai Mary Chilima Ambuye akuona kulira Kwanu ndipo Mulungu woziwa Chilungamo ndiye amene ayankhe mafoso anu ndi a Malawi pa ifa ya anthu amene anatisiya pa ngozi ya ndege imeneyi the DC Boooon Kalindo the truth of Malawi

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma. Nzoona. Mayi. Chilima. Muyimbe. Ntima. Ife. Tili. Pambuyo. Panu

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ife a malawi tikufuna Mademo a nyoooo...mpaka tikafika ku parliament konko..ndipo azakhala mathero a anthu amenewa..💪💪💪💪💪

  • @LovemoreCathy
    @LovemoreCathy 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chikangawa party(MCP) mapwala awo ndithu asalowelelepo pa nkhani iyi coz nafedwa anawasiyila nkhani yimeneyi nthawi yayitali koma pali chomwe apangapo nde pano nafedwayo wabwela kuti apeze chomwe chinapha mwamuna wawo nde MCP yisalowelelepo apa....

  • @lindadzaoneni
    @lindadzaoneni 24 นาทีที่ผ่านมา

    Chilungamo chidziwike sure

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC..More Fire 🔥..akatundu ❤❤❤❤

  • @SherifDouglas
    @SherifDouglas 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zokuti wina sazapezeka pa ballot paper akhala atafa ndi mapemphero komaso kukwiya kwa mizimu ndizionadi

  • @chikublea8982
    @chikublea8982 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kupita kukaona pomwe anafera Bale wako ndi kolakwika kapena kulira maliro abale wako ndikolesedwa ndiyakheni amalawi ndiyakheni

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 35 นาทีที่ผ่านมา

    Mcp muona nyekwe chake chake ndi Chino

  • @nzotakilango9578
    @nzotakilango9578 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo agalu amenewa atitopesa. SKC rest in peace

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoonaza abiye akalido mwayakulazo zichitika

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Just for SKC AND VIVA MAI CHILIMA

  • @MussaNgoma-r2k
    @MussaNgoma-r2k ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Very good we need rotation ❤❤❤

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dipo akumanadimoto ahebili 12:29

  • @IsaacMumba-er5hu
    @IsaacMumba-er5hu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    All MCP members pa mtumbo panu

  • @CalistaPeter-e9o
    @CalistaPeter-e9o ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kma ikhale nyekhwe lizimu 😅

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sitisiya kulira mpaka wina agwe.

  • @EliaSiska-n6r
    @EliaSiska-n6r 49 นาทีที่ผ่านมา

    Bravo mayi Chilima

  • @SargentZimba
    @SargentZimba 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nga'aluraaaaaaaa nthawi yathaa

  • @HezelChisi
    @HezelChisi 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine ndiiii Bonnnnn kalindoooooo

  • @AlijuMikayilu
    @AlijuMikayilu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wakupa chakwele😢😢

  • @AlijuMikayilu
    @AlijuMikayilu 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wakupa chakwele😢😢

  • @MichaelKachiboo
    @MichaelKachiboo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    I follow you mam

  • @LucyEndmond
    @LucyEndmond ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DC woyeeeeeee motsoooooo kut buuuu

  • @justinmchenga1387
    @justinmchenga1387 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    SKC🔥🔥

  • @NefteryKamowa
    @NefteryKamowa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoonazake

  • @MussaHaji-f9h
    @MussaHaji-f9h 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

  • @LightwellMunthali-x7r
    @LightwellMunthali-x7r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Onse amene sakugwilizana nanzo zoti mery chilima ayimire ndi a MCP andi alindimantha

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@LightwellMunthali-x7r sangawine mary ndale sangazithe ndi mwana maganizo opusa basi

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Auzeni anyapapiwo agulugunyintha tizawadula mitu Peter akazalowa m'boma.mutisamale

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zopanda mzeru izi osamufunsa mwini moyo bwanji kuti munalileranji kuti chilima afe akuyankhani osati zanuzi anthu onsewa akufawa chilima apambane osewa kukomera kwake wakufa sadziwa kanthu biiiiii bible likunena osati munthu akutero ayi munthu ndi wabodza zazii musiyeni chilima lake anatseka nanga lanu mudzakhala mukutani

    • @MichaelKachiboo
      @MichaelKachiboo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kufa ndi kufu koma tikufuna tidziwe zoona chifukwa kufa ngati ifa yake ingakhale choncho tintha psweeti

    • @temwarachaelkhonje3733
      @temwarachaelkhonje3733 6 นาทีที่ผ่านมา

      Mpaka tizaziwe amene anapanga zimenezo...kaya ndinu amwene.....tizamva tsikulo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaaa koma MCP pena mudzikhala ndi dzelu mai chilima kupita kumawona pomwe anafela mamunake pamenepo pali mvuto iiiii kutsamvuatu MCP dziwani kuti mulungu simunthu dzotse akuwona kupanda chilima munali ndani inu a MCP aaaaa uchisilu basi

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@hanifahmponda8711 nanga ndi MCP mesa ndinu a DPP munagwetsa ndege?

    • @HadijaKamwenendo
      @HadijaKamwenendo 27 นาทีที่ผ่านมา

      ​@@alexandermeke6994achimwene tsekani kuchikamwa 🙏

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 18 นาทีที่ผ่านมา

      @@HadijaKamwenendo yambani ndinu zikuphani ndale inu mumadya ndale inu umbuli ukuphani

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Deliberate policy ndikugwilizana naye

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DC woyeeeeeee ❤❤❤

  • @LightwellMunthali-x7r
    @LightwellMunthali-x7r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ife tili chete kudikila Mary Chilima kuti azayimere.

    • @johnnyirenda5848
      @johnnyirenda5848 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      GOOD LET HER HEAR OUR PROPOSAL MALAWI CAN SHAKE HEAVILY