History is best teacher ndizoonadi ndi aganyu a mcp, A zimai aja ndi mahule a munchesimu wina uja amagulitsa mpunga ena aja nde bizinesi yawo ndi kunyengesa alibe cocita ciliconse.A zibambowo nde ndi a mcp nawonso ali ndi masupada awo okhapila anthu.mzanga wina wa mu lilongwemu wanditsimikizilanso dza nkhaniyi cifukwa iyeyo anthuwa amawadziwa bohboh mpaka mmakomo mwawo inu a mcp ndinu makape.Kutukwana mabishop amene akunena zomwe ife a malawi tikudandaula nwashosha yolakwika mudziona
Abusa nawoso ndimunthu alindiufuluwolankhulazakukhosikwawo Abusa sanalakwise ,chilungamo ndi chofunikakuchinenapamasopa Anthu,well done abusa towork together we can make malawi better place for all Muwumozi mulimphavu Abusa musavutike mutima God will stand up for you and god will protect you from all ur enemy, and dont give up, AROMA 12 V 9 / masalimo 37 V 1 Abusa wosa tekeseka mphamvu ndi maso time kwamulungu.we all love u again God bless you and protect you all the time ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Archbishop,sanalakwitse kunenapo chifukwa report la ndege linachita contradict lokha .Silomapereka direction zoti Malawi angatolemo.limakhala ngati loudza ana okhaokha.
Aboma apenga misara akulimbana ndi munthu olakwika Kaya nkuyaluka ngati muli osalakwa chifukwa chani mukusowa ntendere ooooh yes muzasausika mpaka kare kare
Yense amene akudana ndi zoyankhula a msusa Ali mu umbuli wa mnanu komanso ndi wa satanic Palibe amene amasiya kudandaula kapena kuyankhulapo m'bale wake atamwalila ngakhale patatha zaka zilumika
Enao ndi azibusa a dyela ndi mantha iwowo anakangokhala chete mnao nkumakalalikila ku chipembezo kwao kuti report linali bwino osati zoti atchukile nkulemerera pa nzao Dyela lachoka kwa andale ma lawyer lalowanso church mmmmmh masiku omaliza
0:06 Ambuye Archbishop Thomas Msusa is the real prophet of God. He is very concerned the same way most of Malawians are. We are not bothered with Fake religious leaders who came to denounce His Grace Archbishop Msusa. Those have been given money by MCP’s Chakwera & Chimwendo to come and talk NONSENSE through the media. Tony Chisala. Jhb- South Africs.
I stand with Bishop Msusa may Good Lord bless u Papa
Im totally with you Bishop Msusa.
Olimbana ndiinu alimbana ndi Mulungu
Bishop Msusa honest person , leave him alone ,man of God
History is best teacher ndizoonadi ndi aganyu a mcp, A zimai aja ndi mahule a munchesimu wina uja amagulitsa mpunga ena aja nde bizinesi yawo ndi kunyengesa alibe cocita ciliconse.A zibambowo nde ndi a mcp nawonso ali ndi masupada awo okhapila anthu.mzanga wina wa mu lilongwemu wanditsimikizilanso dza nkhaniyi cifukwa iyeyo anthuwa amawadziwa bohboh mpaka mmakomo mwawo inu a mcp ndinu makape.Kutukwana mabishop amene akunena zomwe ife a malawi tikudandaula nwashosha yolakwika mudziona
Abusa nawoso ndimunthu alindiufuluwolankhulazakukhosikwawo
Abusa sanalakwise ,chilungamo ndi chofunikakuchinenapamasopa
Anthu,well done abusa towork together we can make malawi better place for all
Muwumozi mulimphavu
Abusa musavutike mutima God will stand up for you and god will protect you from all ur enemy, and dont give up, AROMA 12 V 9 / masalimo 37 V 1
Abusa wosa tekeseka mphamvu ndi maso time kwamulungu.we all love u again God bless you and protect you all the time ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndimadziwa ine kuti zoona timamva kuchokera kwa Bakili Muluzi TV
Anse wabakili muludzi uja osazamupweketsa waona sheheyo mmene wamusakila wachita kuoneka kut ndi mcp 😂😂😂😂
Osadandaula my bishop my lord is with you chilungamo ndi chopweteka mwawaponda pa chala stay protected
Thank you a Bishop. We are proud of you
M'busa osalakwa uyu kungoti chilungamo chimawawa nthawi zonse....keep it up Bishop Msusa
Waiting to hear more.
Kkkkk km ine ku Malawi 🤣🔥🔥🤣🔥 kokoma Bhola data
Eshiiii koma bakili tv mmmmmm ndi katundu 😂😂😂😂😂😂😂 kumalawi bundle azikhala wambili kkkkk koma ndaseka
Nsusa ❤❤❤we love ❤️ you daddy ❤❤❤c😢
Pali mau oti genda galu kt udziwe mwina wa galu apapa a bishop a msusa agenda galu
Chakwera ndi boma lake la Mcp eti kulimbana ndi munthu wozozedwa wa Mulungu kutha kwa ufumu waonjeza kwayandikira
Amene akuti busayo arafred mphoteyo adamunthamangitsa chifukwa chonyenga mkaxi wamwini amakhala kwabiwi pafupi ndi pakaufulu amkanyengelelaso wantchito wake kuti adzigonana naye ndibusa ameneyo
😂😂😂😂
I stand with my Bishop not iam catholic but the truth
Ayaluka a MCP akupha
God bless you man of God keep going with the true
Km guys mukulimbaana ndi busa uyu 😂🙌🙌🙌🙌😂 chakwera mutu sukugwira
Kamuzu anapanga zomwezi 1992 koma anawina. Awanso ali paulendo ndipo ochititsa manyazi ndipo sadzavetsa mmene adzaluziremo, landslide
Anyamata mcp awa makape msusa ndi one osati azibusa opanda mayinawa
Mdima udana ndi Kuunika. Chilungamo chimapambana nthawi zonse. Pa dziko lapansi palibe Chinsinsi. Ndipo palibe obisala kwa MULUNGU.
I second Bishop
Good massage from papa msusa
God ahead u my brother
I stand you bishop
Aboshop sanalakwitse kunena maganizo awo
Woseo ndiojia achakwera ' chilungamo chimawawa a bishop ayima pa chilungamo report ndi la boza/ mafuso alephelaso kuyankha momweka chibwibwi thoo:
I like your style my bro
Zomwe ayankhula a bishop zopusa kwambiri
Palipo abusa apa onsewa ndi andale
Ndipo bishop msusa is agood person
Aaaa nawonso a Bishop Ali ndi ufulu oyankhula Ambuye akutetezeni Abishop
Archbishop,sanalakwitse kunenapo chifukwa report la ndege linachita contradict lokha .Silomapereka direction zoti Malawi angatolemo.limakhala ngati loudza ana okhaokha.
My cometi olamula.dziko ndimulungu kotelo athu amulungu alinako kuthekela kutsusa zolakwikwa mopanda matho mosawophezedwa
Werting Bakili TV weni weni kuti atokota motani🎉🎉
Is true behind abusawo
Kd MCP bwanj ulindi ushisillu waboma ollesa mundu aliyense nkunenna sankukossi
Mcp zako zada olo ineso chokuopa chidandithe moti mantha ndilibe nawe
Oyankhawa nde awonjezera mkwiyo wathu
Libe
Azibusa amenewa ndiopusa kwambiri,ofuni muchitepo kanthu
Aboma apenga misara akulimbana ndi munthu olakwika Kaya nkuyaluka ngati muli osalakwa chifukwa chani mukusowa ntendere ooooh yes muzasausika mpaka kare kare
Zitsiru za azibusa,mufune musafune 2025 munya manyi muona
Apapa ayaluka mazobawa😅😅
Baterry low taikani pa charge mubwereso
amsusa analalika zoona,, mchakach tadusa mzowawa pankhan yangoz yandege chikangawa,,, muulalikiwu anaikamo so kt tisagawa mader,, mnthu alindiufulu opita kwina kulikose,, ati tikhare anthu okondana mziko lanthu lamalawi,,, pamene tikulowa mchaka chikubwerach,,, zoonad mchikond mlimtender,,,
Anishop saname aiiiiiiiii
Yense amene akudana ndi zoyankhula a msusa Ali mu umbuli wa mnanu komanso ndi wa satanic
Palibe amene amasiya kudandaula kapena kuyankhulapo m'bale wake atamwalila ngakhale patatha zaka zilumika
Azibusa ongofuna kuzadya ndilama zinsilu
Koma bwanji akatolika ndi zeru zawozi osakakamiza boma kuti anthu asamuke kumadera osefukila madzi to avoid unnecessary kupepmpha chithandizo?
Boma lachikangawa ife tatopanalo pls chonde palibe chomwe chikuyenda malete all
Enao ndi azibusa a dyela ndi mantha iwowo anakangokhala chete mnao nkumakalalikila ku chipembezo kwao kuti report linali bwino osati zoti atchukile nkulemerera pa nzao
Dyela lachoka kwa andale ma lawyer lalowanso church mmmmmh masiku omaliza
Anthu ambili muchita manyazi ndi ifa yachilima mulakalaka kulowa pansi
Ndi zoona sitikunkhutira ndilipoti liii
Kkkkkkkk chikangawa chiseko Cha mupanadi, sheikh wazikwanje wayaluka
Abusa ometa m,mbali kkkkkk
ife Malawi chowona ndichimenocho ndinthu
Umakwana m'bale
Abishop msusa mulungu akudalitsen akatolika asayambe kuopsezedwa pano katolika ndiyomwe imatitsogilela please mcp musaipitse ma b shop ai vuto ndinu osat muchitaz kharan okonda dziko lanu la Malawi nyanja ikupita opanda chazelu akuyankhulap km bizy kulimbana ndi anthu osalakwa mudziko mwanu.
Guys pls achakwera anapaha saulosi koma zitayeni akuziwa ndi mulungu
Pitilizani kutipasa khani zobisikazi coz ena pamene mukutelo sakusagalala
Ndalama anazitenga kuti anthu oshota ngati amenewa anawatuma ndichimwendo Banda munthu oyipa kwambiri wadowado kapena kuti kamabonjo dzina lina la chimwendo ameneyo
Kodi a bishop wa atchula munthu kapena chipani?Kodi mukututumuka ndichani?
A bishop tili Nanu limodzi mulungu Ali mbali yanu
Asusa akunena zona abusa enawa ndi afisi koma susa akunena zona
Anthu adakalilabe adakakhala ena sadakawayankha amsusa chifukwa Pena munthu Umatha kupezeka kuti wankhula nkhani yoti sumayembekezela kuti uyjyankhule umapezeka wayankhula kazimu kakulowa tangoganizani ulaliki umene uja mpaka kufika kukhudza za ngozi ya pa 10 June umene uja si ulaliki koma kulila
Tili limodzi ndi aNsusa
Koma sayimaridza
Magazi a anthu 9 omwe anafa pa ngozi ya ndege aja, apanga zinthu. Tingoti pheeee! Tione
Zandikumbutsa munthawi ya Kamuzu banda ,
Ndima Bishop omwenso anathandidzila kuchotsa mcp m'boma after kulemba chikalata chawo chija kulidzudzula boma la MCP munthawi imeneyo chifukwa chamavuto omwe amalawi ambili amakomana nawo mu ulamulilo wachipani chimodzi .
Ndikukumbukila kuti boma la mcp mosogozedwa ndi kamuzu anayetsetsa kuopseza ma Bishop a mpingo wa katolika powamanga komanso powalanda katundu , koma anaima pachilungamo pofuna kuti malawi akhale pa mtendele ,
Ndizomvetsa chisoni kuti nkhamza zomwe anazithetsa zija ,lelonso zikufuna zibwelele , ndiye tikupempha kuti chonde ma Bishop , timenyeleni nkhondo yopulumutsa Malawi chifukwa inu mukayankhula MULUNGU amamva , kotelo imvani kulila kwa amalawi omwe akufuna thandizo lanu ,
Ife tili pambuyo panu, chifukwa dziko la malawi ndila anthu tonse .
History is the best teacher
Only God knows
Kkkkkkkkkkkkkkk koma ndaseka chilichonse chomwe akuyesesa kuchita chikugokhalanso pa mbalambanda kuyaluka kusanache kwabvuta kupanda chauta watuluka chikhoswe hahahahahahahahahah muona kuti mutani
Abishop akunena zoona
mcp ndi chipani cha anthu okupha zokha zokha
0:06 Ambuye Archbishop Thomas Msusa is the real prophet of God. He is very concerned the same way most of Malawians are. We are not bothered with Fake religious leaders who came to denounce His Grace Archbishop Msusa. Those have been given money by MCP’s Chakwera & Chimwendo to come and talk NONSENSE through the media.
Tony Chisala.
Jhb- South Africs.
History is the best teacher