Tiye nawoni awa atikwana ife eni dziko tikuti chonde basi mwalamulira lisiyeni dzikoli mwawononga,mwapha,mwaba ndalama zathu,mwalemera pitani mukadye ndalamazo mukatha mukalowa mu ufumu was Atate, shame on you MCP
Munthu odzindikira sangangakhale nawo mugulu la anthu ochimwa , mwatumidwa ndi MCP agalu inu musiyeni namiwa, anthu akhupha inu, achina gadama adafa choncho ndi MCP yomweyi kuwagwira akuchokera ku parliament ku zomba nthawi imeneyo, but you still don't believe that MCP is bad
Iwe choka uko akanakhara kuti anakanira zopanda zelu sibwezi alipano koma amaziwa kuti chilungamo palibe kod athu ose anafa aja ndi andale uzikhara ndi Muthu Muthu oyipa iwe
Inshort , we don't have any report yet , Original report will come with the death penalty for the following people , Lazarus chakwela , keneth zikhale ng'oma , Richard chimwendo banda , Valentino phiri , mrs yolam , coreen zamba ,
Mr NamiwA your totally fool You had all opportunities to give us full confidence for how these tregidy occurred but Your pride yet your here with the same stupidity 😊l
Galu iwe namiwa, chitsilu, usamayese ife opusa, unakanilanji,,, iweyo,,, umafuna upezelepo,, zifukwa,,, uzinamiza, Ana amako,, u kana nkhala azelu, ukanapanga nawo kafukufuku,,,, usamanamizile,, a Malawi,,, iwe, a Malawi ake ATI,,,
Professor Lumumba said if you ask someone what he has done and he's taking 15 minutes to answer, he has done nothing to show Someone who does something people don't ask because they already see what he has done 😂😂😂
Namiwa may God continue protecting you
This Namiwa guy needs support
I wish would receive a miracle money and support this brilliant man
Powerful, Amen 💪🤝🤝
Kkkkkkkkkkkest
You will succeed if what you are saying is true.. I am also a Malawi
Quick action, cos kumangolankhula, akumangothatha ma chance
Tiye nawoni awa atikwana ife eni dziko tikuti chonde basi mwalamulira lisiyeni dzikoli mwawononga,mwapha,mwaba ndalama zathu,mwalemera pitani mukadye ndalamazo mukatha mukalowa mu ufumu was Atate, shame on you MCP
Eeeee Koma namiwa siwosewera nao Ayo💪💪💪💪💪💪
🌟💯Namiwa
Bravo Namiwa
Inu nusatiwonongere bandle misa munakana kupanganawo kafukufuku mulibezeru iwe namiwa
Wakutuma ndani kut uyatse data yako nyani iwe ulibe nzeru
Pano sitikukamba za data. Kumachangamuka pilizi
Angosusula zilonda zomwe zimapola ndipo angowononga ndalama zathu anyani amenewa
Nkulu chilungamo chizaziwika one day koma palibe chisis
Infa yowawa res in peace Bhiyeni
Munthu odzindikira sangangakhale nawo mugulu la anthu ochimwa , mwatumidwa ndi MCP agalu inu musiyeni namiwa, anthu akhupha inu, achina gadama adafa choncho ndi MCP yomweyi kuwagwira akuchokera ku parliament ku zomba nthawi imeneyo, but you still don't believe that MCP is bad
From Bloemfontein namiwa mulungu azikudalisa mbili yanu sizaiwalika ai amalawi tikuvutika ndithu
Mr Namiwa khalisani kwambiri
More fire Namiwa!!
Apaneni agulugufe amenewo Mr namiwa
Musamusiye
Namiwa ndi wanzeru kumene
Angotiwonongelaso ndalama zanthu,
Kodi mumat mukutumikila amalawi kapena mimba zanu? Cimene mudasiila tchito panjira yofufuza nawo adakutumaniso ndiamalawiwoso? Mupange zomwe amalawi amakutumani ndale zisalowe apa. Mapeto ake amalawiwo sakuvetsani zimene mukupanga
Tachokani simudziwa kanthu amenei zoti ntchito zake ndi omenyela ufulu wa amalawi sukudziwa including you if you dnt get it forget about it
mwangosowa chonenatu Manu musiyeni namiwa .muyalukatu
Iwe choka uko akanakhara kuti anakanira zopanda zelu sibwezi alipano koma amaziwa kuti chilungamo palibe kod athu ose anafa aja ndi andale uzikhara ndi Muthu Muthu oyipa iwe
Dziko la Malawi needs a dictatorship rule, like Bingu, anthuwa akuzolowera kunyoza kwambiri
Inshort , we don't have any report yet ,
Original report will come with the death penalty for the following people ,
Lazarus chakwela , keneth zikhale ng'oma , Richard chimwendo banda , Valentino phiri , mrs yolam , coreen zamba ,
Tiuzeni zoona mumakwana a Namiwa opha mzake naye aduwe
Vuto la uyu amangoyakhula koma action satenga
Kodi HRA inalowaso m'boma ngat hdrc 😂😂😂
Atolankhani mumamusata mumasowa zochita
I think these guys are playing with people's minds
Anthu anzeru
Kod iwe mesa unali ndi mwayi kut uyende nawo pano bwezi ukuliuza dziko zomwe waona
Kkkkkkkkkkkest
Kutukwana Namiwa you can say it well
MCP yachibwana amaganiza mopisa ngati anthu alibe ubongo oganizila pa zomwe iwowo akumachita
Achakwera koma inuyo mwapambana pati kumwamba kuli wakuthwa diso ngati lupanga let's wait and see
Uyutu mpena zôchitika zake zotsamveka bwino
Ine ndinaziwa kt iwe upezelapo zifukwa
Mr NamiwA your totally fool
You had all opportunities to give us full confidence for how these tregidy occurred but
Your pride yet your here with the same stupidity 😊l
Ndichitsiru Mamiwa
Sawancha kwa NAMIWA ndakuvanì tikuthandizani pazonse munene kuti tichite
Galu iwe namiwa, chitsilu, usamayese ife opusa, unakanilanji,,, iweyo,,, umafuna upezelepo,, zifukwa,,, uzinamiza, Ana amako,, u kana nkhala azelu, ukanapanga nawo kafukufuku,,,, usamanamizile,, a Malawi,,, iwe, a Malawi ake ATI,,,
Iweyo ndiye chitsiru sukuona kuti lipoti lake lachulutsa chibwana
@AbdulsharifulKalipinde-m6u anachokelanji iyeyo, ndiye uchiluwo, akanankhalako, tikanadziwa zambili,,
ndiwe opusatu
Yambitsani nkhondoyo u are worried imfa ya anthu 9_ in Mozambique people are dying, mukadangozisiya izi, you don't kno what you are doing
ANamiwa muchedwa umwalira adayamba Nchilima
Namiwa is not normal
More 🔥🔥🔥 Namiwa , we know the truth
Namiwa apane agaluwa akujayila
Iwe ndi oduka mutu kwabasi
Mcp mwatitola kwambiri
He is just saying nosense here
Nkhani zonse anayankhu Chakwela ndi Kumkuyu sadzikhudze why?
Fiti yamunthu iyi upenga nazo
Kodi ukuyakhula chani iwe 😡😡
Namiwa mutu wake sugwira ngopenga uyu mapazi ake kkk
Kd kukanakunja mumafuna muzapeze zifukwa cholinga muzalakhulepo kkkk km namiwa unabwera
Zamanyazi
You lost an opportunity Namiwa, ndiwe kape. Only fools can take you seriously
Keep quiet
Atseke nkuchikamwa kodi 😂😂@@Calvin_isaacPhiri-cw7fi
He is a coward uyu mlomwe wa DPP
mupusatu malo ochenjera iwe nde ndani.
Eee kwavuta
Professor Lumumba said if you ask someone what he has done and he's taking 15 minutes to answer, he has done nothing to show
Someone who does something people don't ask because they already see what he has done 😂😂😂
Namiwa wumafuna kuwoneka ngat wazelu wumway wunali nawo wokawona wekha ndeye wumakwana ndiwe chitsilu wuzikanamiZa Ana Amako wamako
Uyesere ku panga ma demo azako atengerapo phuziro tsopano
Ine ndinaziwa kt iwe upezelapo zifukwa