ZATHU BAND - CHINZATHU ICHICHI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ส.ค. 2024
  • Yafika! Video yatsopano ya chinyamata a Zathu Band, yotchedwa ‘chinzathu Ichichi’. Vidiyoyi ikutionetsa momwe makolo angatengele mbali pa moyo wa achinyamata pothandiza kuti anyamata ndi atsikana azigwilila ntchito limodzi, komanso kuthandizana pa zochitika zosiyanasiyana monga zakusukulu komanso zina zambili zomwe zingawathandize kusintha miyoyo yawo. Muona momwe Agogo anathandizila Bambo a JP kumvetsa kuti Mphatso ndI JP amangogwilila ntchito limodzi ndipo panalibe chilichonse pakati pawo. Gogo awathandiza kumvetsa kuti kulola anyamata ndi atsikana kuti agwile ntchito limodzi kungathandize kuti achinyamata akwaniritse komanso kuchita zinthu zazikulu mu moyo komanso dela lawo.

ความคิดเห็น • 24

  • @kondwanijaykangwale6070
    @kondwanijaykangwale6070 หลายเดือนก่อน +1

    Here in 2024

  • @EsauMagalasi
    @EsauMagalasi 7 หลายเดือนก่อน +1

    Come on guys zili bwno hvy anthu sakhulupilira za chiuzathu ichichi

  • @samuelsimaolinguissoneling2884
    @samuelsimaolinguissoneling2884 3 หลายเดือนก่อน +1

    🎉🎉 zabwino zonse 🎉🎉

  • @cleopatranyirenda7958
    @cleopatranyirenda7958 3 หลายเดือนก่อน +1

    Agogo amawamvetsensa anawo

  • @user-vx8dv2vp5q
    @user-vx8dv2vp5q หลายเดือนก่อน

    Am still waiting u guys

  • @gracejeremiah910
    @gracejeremiah910 ปีที่แล้ว +1

    We miss you guys tabwelaniso

  • @aadammalijane1670
    @aadammalijane1670 6 ปีที่แล้ว +1

    Chizathu ichichi lovely story lines I think yourl should create shot story's yourl have beautiful cameras and sound it's lovely keep up

    • @zathu4731
      @zathu4731  6 ปีที่แล้ว

      Thank you so much, you can also follow our Season 3 repeats by visiting out website: zathu.mw/sections/chichewa-translation-of-our-show/

  • @kelvinscent7501
    @kelvinscent7501 ปีที่แล้ว +1

    Watching from Zambia
    I love u en I wish I join you
    Coz am also a guitarist

  • @jeanosworld6162
    @jeanosworld6162 6 ปีที่แล้ว

    watching from USA, keep presenting MW and Africa guys

    • @zathu4731
      @zathu4731  6 ปีที่แล้ว +1

      Thank you so much.

  • @blessingmango3749
    @blessingmango3749 6 ปีที่แล้ว

    Guys I love your music. Keep it lit💥💥

  • @besolo3916
    @besolo3916 5 ปีที่แล้ว

    Brave....ur cameras r real nice composure

  • @victoriabulirani3800
    @victoriabulirani3800 ปีที่แล้ว

    Love love you guys 🤗💖

  • @pamelasingini100
    @pamelasingini100 6 ปีที่แล้ว +2

    you guys are amazing..!!!!!!

    • @zathu4731
      @zathu4731  6 ปีที่แล้ว

      Thank you so much, you can also follow our work and Zathu Pa Wailesi Season 3 repeats by visiting our website: www.zathu.mw

  • @lumbanikamanga1074
    @lumbanikamanga1074 6 ปีที่แล้ว +1

    Great music

    • @zathu4731
      @zathu4731  6 ปีที่แล้ว

      Thank you so much. Follow our work by visiting our website: www.zathu.mw

  • @StanleyPhiri-mj2tk
    @StanleyPhiri-mj2tk 3 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤

  • @zadockwilliam4473
    @zadockwilliam4473 4 ปีที่แล้ว

    Chizathu ndchabwno ndthu

  • @InnosentNelson
    @InnosentNelson 10 หลายเดือนก่อน

    Zopambana

  • @user-rv1kx9gd8g
    @user-rv1kx9gd8g ปีที่แล้ว

    Guys mumandisangaratsa bwaji

  • @VanGift-cc9vp
    @VanGift-cc9vp 8 หลายเดือนก่อน

    Mbambsnde

  • @thoccobakali8070
    @thoccobakali8070 6 ปีที่แล้ว +1

    zilibwino