ZATHU
ZATHU
  • 16
  • 282 355
ZATHU BAND - CHINZATHU ICHICHI
Yafika! Video yatsopano ya chinyamata a Zathu Band, yotchedwa ‘chinzathu Ichichi’. Vidiyoyi ikutionetsa momwe makolo angatengele mbali pa moyo wa achinyamata pothandiza kuti anyamata ndi atsikana azigwilila ntchito limodzi, komanso kuthandizana pa zochitika zosiyanasiyana monga zakusukulu komanso zina zambili zomwe zingawathandize kusintha miyoyo yawo. Muona momwe Agogo anathandizila Bambo a JP kumvetsa kuti Mphatso ndI JP amangogwilila ntchito limodzi ndipo panalibe chilichonse pakati pawo. Gogo awathandiza kumvetsa kuti kulola anyamata ndi atsikana kuti agwile ntchito limodzi kungathandize kuti achinyamata akwaniritse komanso kuchita zinthu zazikulu mu moyo komanso dela lawo.
มุมมอง: 27 752

วีดีโอ

Zathu Band: Chinzathu Ichichi Video Teaser
มุมมอง 1.5K6 ปีที่แล้ว
Vidiyo ya Zathu Band, yotchedwa Chinzathu Ichichi komanso ma pulogalamu obweleza amu season 3 adzayamba kupezeka kuyambila pa 10 September.
ZATHU BAND ft Nyamalikiti Nthiwatiwa - MALAWI
มุมมอง 35K6 ปีที่แล้ว
The new single Malawi is a song that celebrates Malawi's diversity. In the video the Zathu Band embark on a journey through this beautiful country and discover how their differences make them stronger together. The song features the poet Nyamalikiti Nthiwathiwa and traditional instrumentalists, Madalitso Band.
Zathu Band - Malawi
มุมมอง 3.8K6 ปีที่แล้ว
Zathu Band is going to be releasing an album and a new music video on the 19th of February! As we wait, check out a teaser of Zathu Band's new music video "Malawi".
Zathu Band | Panga Zako
มุมมอง 37K6 ปีที่แล้ว
Nyimbo yachitatu ya achinyamata aja a Zathu Band yatuluka! Nyimboyi ikufotokoza za moyo wa achinyamata asanu ndi m’modzi amu Zathu Band komanso Gogo pamene akuthandizana pa zophinja zosiyanasiyana. Mu video imeneyi Chikondi akuvutikabe ndi Aunt Nelly omwe samaona phindu lililonse mu zochitika za achinyamata monga kuimba, kuvina komanso kukhala omasuka ndi moyo wawo. Kodi Chikondi akwanitsa kuwa...
Zathu Pa Wailesi Season 2 Photoshoot
มุมมอง 1.6K6 ปีที่แล้ว
Umu ndi m'mene zinalili pa photoshoot yokonzekera Season 2 ya Zathu Pa Wailesi.
Zathu Band: Panga Zako Video Teaser
มุมมอง 2.2K6 ปีที่แล้ว
Video ya Panga Zako ituluka pa 30 October!
Zathu Documentary
มุมมอง 10K7 ปีที่แล้ว
Iyi ndi documentary imene ikuyankha mafunso monga: kodi Zathu ndi chani? Kodi imachita chani? Kodi ifuna kupindula chani pakati pa achinyamata? Zabwino zonse pamene mukuonera.
Zathu Documentary teaser
มุมมอง 1.7K7 ปีที่แล้ว
Nayu Kalawe wa Documentary ya Zathu.
ZATHU BAND - SITIGONJA
มุมมอง 11K7 ปีที่แล้ว
Music video ya ‘Sitigonja’ kuchokera ku Zathu Band ili pano! Atawina mpikisano wanyimbo mu video yawo yoyamba, ‘Zimatere Zimatere’; Xander, Chikondi, Annetti, Mphatso, T-Reel and JP apeza thandizo kuchokera kwa a Gogo, nkupita kukajambulitsa kuti akakhazikitse band yawo. Koma akudziwa malo okajambulitsilakowo? Kodi akafikako nthawi yabwino? Oyimba otchuka, Lulu, akupezekanso mu videoyi.
SITIGONJA | ZATHU BAND | VIDEO TEASER
มุมมอง 2.4K7 ปีที่แล้ว
Here is a teaser for Sitigonja music video which will be out on the 24th of July, 2017. Be on the lookout!
WALL PAINTING: ZATHU PA WAILESI LAUNCH HIGHLIGHTS
มุมมอง 1.4K7 ปีที่แล้ว
Zathu Launch day Painting
Behind The Scenes: Zathu Cast recording the radio in the studio
มุมมอง 2.4K7 ปีที่แล้ว
Behind The Scenes: Zathu Cast recording the radio in the studio
Zathu Band with Inkosi ya Makosi Mbelwa and Inkosi Mabilabo
มุมมอง 10K7 ปีที่แล้ว
Zathu Band with Inkosi ya Makosi Mbelwa and Inkosi Mabilabo. #Zathu #ZathuPaWailesi
Zathu Band - Zimatere Zimatere (Chichewa) HD
มุมมอง 129K7 ปีที่แล้ว
Zathu Band - Zimatere Zimatere (Chichewa) HD
Behind the scenes: Zathu Cast's first photo shoot
มุมมอง 6K7 ปีที่แล้ว
Behind the scenes: Zathu Cast's first photo shoot