Plz tangotenga system yaku south Africa for example misonkho ya kumupoto yikhale konko yipange chitukuko konko, pakat choncho ndikumwela choncho Malawi akhoza kusintha
Blessings chilungamo ndichimecho mwina malawi angapulumke , koma so asiye zo pempha mayiko ena zopanda ulemu, siungayendese banja ndizopemphesa ayi, tizidalire tokha, taonani, Donald Trump waturuka mu (Who) world health organization, a Malawi mkalowa muboma siyan Kuba tukulani dziko lanu plz ndapaoata
Dziko la malawi lizasintha nthawi yomwe lizasinthe malamulo onena kuti president akalakwa he needs to step aside for investigation akapezeka osalakwa step in again apo bii aliyense aziba chifukwa akudziwa kuti sindingayimbidwe mulandu
Mugwirizano zipani zikuwopa chifukwa cha Chikangawa party inachita nkhanza kukana after atawina kuti panalibe mugwirizano. Koma Chikangawa party NDI a satana okha okha kaya akukatani Kuma church
You are talking on behalf of someone's interest. I suggest if there should be an alliance it would be good to the following party's to come together: UTM AFORD Nankhumwas Party This would be a powerful force.
Plz tangotenga system yaku south Africa for example misonkho ya kumupoto yikhale konko yipange chitukuko konko, pakat choncho ndikumwela choncho Malawi akhoza kusintha
Koma , shot one , nkhumba , black box ndi chikangawa ziliko
Nkhaniyabwino kwambiri,, APM VIC KABAMBE
Kweni mwayankhulatu za nzeru kwen ulemu wani zimenezo ndie nzeru osangotukwanapo ai koma fundo ndi zimenezo
Chikangawa party....tsongoleri wache mbusa dzina lake Chakwera......wationongera Mother Malawi 🇲🇼 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
M'busa uziwa kupakula nyemba
Boma ndilomweli sitisintha opposition ndiyomweyi sitisintha mpaka 32yrs woohoo
Mr Brack box chileka nkhumbe
Zakeyu ,yudasi Mulanje
Mr chikangawa lilongwe
Namajekete
lilongwe
Mai kasikha lilongwe chikangawa
Chikono banda chikangawa
Masten yo......
Valentine's soldier soldier chikangawa
Nanga kamadjekete aliposo😂😂😂😂😂
Plz tangotenga system yaku south Africa for example misonkho ya kumupoto yikhale konko yipange chitukuko konko, pakat choncho ndikumwela choncho Malawi akhoza kusintha
Blessings chilungamo ndichimecho mwina malawi angapulumke , koma so asiye zo pempha mayiko ena zopanda ulemu, siungayendese banja ndizopemphesa ayi, tizidalire tokha, taonani, Donald Trump waturuka mu (Who) world health organization, a Malawi mkalowa muboma siyan Kuba tukulani dziko lanu plz ndapaoata
Ndiye kulankhula koziwazasogolo 🇿🇲
Mbuzii za mcp
Kkkkkkkk Mr Blackbox😂😂😂😂😂😂
Chikangawa government 😂😂
Chilungamo wakamba mubale
Both APM and DK are lhomwes sikubalansa
Dziko la malawi lizasintha nthawi yomwe lizasinthe malamulo onena kuti president akalakwa he needs to step aside for investigation akapezeka osalakwa step in again apo bii aliyense aziba chifukwa akudziwa kuti sindingayimbidwe mulandu
Iweyo izizi Kaya wumazitenga Kuti. Ma President sangachokere mu region yimozi, uwu si ufumu. Mistake iyi ndiyomwe anapanga kusankha CHIMULILENJI.
Mugwirizano zipani zikuwopa chifukwa cha Chikangawa party inachita nkhanza kukana after atawina kuti panalibe mugwirizano.
Koma Chikangawa party NDI a satana okha okha kaya akukatani Kuma church
You are talking on behalf of someone's interest.
I suggest if there should be an alliance it would be good to the following party's to come together:
UTM
AFORD
Nankhumwas Party
This would be a powerful force.
😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮
Ndiye walunkhula bwino,bola kusiya zakale zoyipa.
Si m'busa Inu anangovala chikopa cha khosa awa ndi mimbulu iyi
I recommend you Blessings in all you have said
Amanganya.sibasi.mwakala.pasi.mumati.mutani
Plz tangotenga system yaku south Africa for example misonkho ya kumupoto yikhale konko yipange chitukuko konko, pakat choncho ndikumwela choncho Malawi akhoza kusintha