ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ngati ili funding ambiti tilipo just contact us. Ka two tamala kanga and other people we love this. I will just do a contribution not want recognition
A kalanka mwina ndi last born kwawo. Amanyanyala zilizonse kikikiki
Kkkkkk.mpakana 🐄🐄🐄🐄 ..vuto athilamo kale machaka,,azalamo amphonda..a Kalanka muli ndi phuma asaaaa😂😂😂
Bale wanga nthembwelembwe 😂
That is not sitting kumeneko sikukhala kkkkk 😆😆😆😆
😂😂😂😂 padela wakana kugwila tchito ya khola 😂😂😂, kalaka wakana kupereka 1 million lobora 😂😂😂😂
😂😂😂 padela siwopanga naye ma PG😅😅mwawona2
Third to comment. Ndalawila lero
I love padela's family 😂😂😂
Koma yaah pakana million 😂
Padera kkkkk
Namoyooo❤
Ati apa nde mwalasa kkkk kalamka😂
Akalanka kuopa mimba ngati wa std 8😂😂😂
Koma ine na padela yekha amandichosa khawa zochitika zake zimandiwaza umayitha padela ulemu wanu
That is not sitting kumeneko sikukhara mmmm 😂😂😂
Akalaka anakwatila ndikubuyo komwe
Keep it up congratulations ❤🎉🎉🎉
7:23 7:30 7:36 7:48 7:50 7:56 7:58 8:00 8:02 8:10 8:16 8:20
Kalamka ndiwe dolo
Kalamka
Mr chisime😂😂😂😂😂
Thanks admin.... tipasileniso inside diaries
😂😂😂😂 Koma kalankayo kubweraso namoyo anzawo akudya Iwo akuthila madothi😂
Eeeh hehedeeee!!!! Luuuuuu!!!!!Namoyo walangatu
❤❤❤
Kodi nonse ndi Alomwe 😂😂😂mmenemu- Heti?
Zinayambatu bwino..... Looks like amateur. Onjezani moto... I love you people... Don't lower the standards
Akalaka mumakwana mwava
Keep it up guys
Tidyetse maso basi😂
That is not siting 😂😂😂😂😂😂
Nafuneya amandiwaza
Koma padela😂😅
Mochedwa ndithu abale inu
Koma Anafuneya makhala ndi maganizo a banja ndithu
❤️❤️❤️
Oyeeee oyeeee oyeeee oyeeee gyz
That is not seeting kumeneko sikukhala iyayi
Padela paka sabola
Relo ndarawilila eshi
Dzulo inandiphonya dear pano kwandichela
😂😂𝙆𝙖𝙡𝙖𝙣𝙠𝙖 𝙠𝙪𝙠𝙖𝙙𝙮𝙚𝙩𝙨𝙚𝙧𝙖 𝙯𝙞𝙩𝙝𝙪❤

Eeeh hehedeeee!!!! Luuuuuu!!!!!
Namoyo walangatu