😂😂😂mumakwana inuyo giling'ande u r legend,gututu ali pa campaign yofuna mkazi,we are proud of u likiliki mukutiponyelaso munthawi yabwino,welcome queen and tadeyo,watching from durban
Queen mwafikaso uku😂kwavuta mai chitsime mulipamavuto ndithu, Amfumukadzi upezeni mtimawo wanu ndi Ngiring'ande basi 😂 next Guys mutimvetsa kukoma kwabasi
😂😂😂mumakwana inuyo giling'ande u r legend,gututu ali pa campaign yofuna mkazi,we are proud of u likiliki mukutiponyelaso munthawi yabwino,welcome queen and tadeyo,watching from durban
Queen 🔥🔥🔥🔥🔥🔥Apadela inu muzafa ndiumohawitu ndi nsanje yanuyo mpaka kukathawa kuntchito
Kodi Amene aja anakharapo Nyamata pena anango badwa chonchi 😅😅😅😅😅😅
Kkkkkkk Mfumukazi.... Ndapulumuka kamwa mwa mkango.
Hahahahahahahha koma gututu wanji uwu asa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Atii rero mundikandira Pa Sitting Room 🤣🤣🤣🤣🏃🏃💨
Gututu guys walusa ndi ubatchala, akumafunsila akazi aeni I love u a Nagama 😂😂😂😂😂😂
Nafuneya zasathekaso..
Bip up guys so proud of you❤❤
Mfumukazi yesetsani kusiyanitsa momwe mungayankhulire ndi Amunanu Giling'ane sipali ponse mukhoza kumangokalipa ndipo chepesani kumanena kuti zausilu .
Kkkkkk Padela ndi nkadzi wake ndi diru moto ku buuuuuu
Kkkk Koma next ichedwa bwanji
Kkkkk koma anafuneya akuzionatu
queen woye
Komatu Gututu ndi mzako Giling'ande mukukankhira kwakuya kkkkk
😂😂😂😂😂😂 Gututu guys sazatheka. Akuti amene aja anakhalapo mnyamata
Enawo sangabwele jz sanje zachuluka ndithu kusiya ntchito kuganizila tulo tofewa 😅😅😅
Kkkkk koma padeoa ai palibe munthu sanje yanji iyi yolowesa umphawi mnyumba
Gututu yemweyo wayesa kwafumu kazi zakanika kwanagama zakanika aaaa kukani kufunsila uku 😂😂😂😂
Komadi gututu linabwera bwanji🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 koma gututu sazatheka kuyambila kufusila Amfumu kenako nagama 😂❤ mwamuna azitelo wosawopa😂
Queen chonde umu usamayankheso chidule, uzitolele
kkkkk Gututu achisime sanakhalepo nyamata 😂😂😂
😂😂😂😂😂😂chiwanda chachikulu ndi Padera koma padera 😂😂😂😂😂😂 ndaseka
Queen mwafikaso uku😂kwavuta mai chitsime mulipamavuto ndithu, Amfumukadzi upezeni mtimawo wanu ndi Ngiring'ande basi 😂 next Guys mutimvetsa kukoma kwabasi
Koma gututu ponya mbalume mozungulira😅😅😅
Kkkkk koma padela umphawitu ndi nsanje siziye delana
Koma lero nde ndinali okwiyaa kenako gululu ndi gututu mastress onse balala 😂😂😂😂😂😂
Ati apadela ndi chiwandatu 😂😂😂😂😂
Ine mungondipatsa mkazi WA chitsime pls
Ati amene aja anakhalapo mnyamata kkkkkk
Eeee here comes queen🤗🤗 kwachema
Next episode zikoma, welokamu Tadeyo tipanikizeni ndiphwete 😂😂😂😅
Apadela kukanika kugwila ntchito chifukwa chansanje l like this guy😅😅😅😅😅😅
Kkkkk koma kukanda kunsana ukuku ayi ndthu bola osanyulana chikopa
🤣🤣🤣😂vomelani musakhale awido
Komaditu paderayu munamudyetsa zungulira khonde aaa
these guys are too talented hahahahahah
amathothoka koma Sasoka
Chiwanda chinabeleka ana atatu 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Komatu banja la Fumukazi ndilosangalatsa la a Padela nalo ndi 1
Keep it up
Alikuti jemason amuthandize gututu?? Amunzunza azimai kuno!!!!! Luka Zulu from Zambia am behind you guys!!!!
Sasokaa😂😂😂
Inu l love you 🤣🤣🤣🤣
Nice 1❤😂😂
Nanyoni aphesa anthu chifukwa nde giling'ande salola tu😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkk guys iyi nde mwakoza
Koma sasoka kkkkkkkkkkkkkkkk
Giling'ande ndi 1
Mumakwanila mfumukazi
Kukandana kwavuta uku kkkkkk
🤣🤣🤣 Padera ndi deal.
Kkkk
Komaso amfumukaz chomwe mukukanila giling, ande Chan???
Cant wait to see queen mu mfumukadzi now it's Nanyoni kkkkkkkkkk umatha sweet pie wanga kkkkkkkkkk
Amfumukaz pitan mukamukande giling, ande please
Kom enifa Chiwaya mbambande azikande ndi khoma
queen ukuzatani kuno? in mai shokoshoko accent 😂😂😂
Koma anakuneya anakoza😂😂
lelo ndye unyela gedetu 😂😂😂😂😂😂 mfumu kazi
Mr Padela your number 1😂😂😂
Girinandi akumukanda.kkkkkk,ha koma
Anzao tili mokanda iwo akugogoda🤣🤣
😂I love you yemweyo😂😂
Gututu and Giling'ande kpt up
😂😂😂😂 Welcome Queen..... Koma Jemason tamusowa ife plz
Kkkkkkkk welcome queen😂
Gututu kufuna mkazi wamwene
Koma apadela amandigwetsa ulesi
A Chitsime anakhalapo mnyamata
Anagama😂😂😂😂 lov u yankhan
Gututu ndi machine
Kkkk😅
Queen welcm
Queen ❤️ 🇲🇿
Mlandu umunewo nd wesh out
Akukande pompoo 😂😂😂😂
Mpaka chitsononkho😂😂😂
🤣🤣🤣🤣Lero akandana pabalasa
Muku koma guys ❤❤
Kkkkkkkk I love you nagama
Kodi Mgututu ndi mfunda eti😂
😂😂😂😂😂
Eh ur welcome my Queen from mdyangu comedy ... What is your name here?
Agili amakukandilani nchiyani?
Anagama avomereni agututu😂😂
Koma gututu 😂😂
🤣🤣🤣
🔥🔥🔥❤️💕💘
Gututu😂😂
Gututu 🤣🤣
Apadela bodza lake sanje ikuphani
😅😅😅😊
Gili'gande khututu anafuneya anagama mukwqna
❤😂
Welcome Quine😂❤
Anagama kuno🤣🤣🤣🤣🤣
Koma giling'ande ndidolo,
Hipster
Inu l love you 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂