Mr Kabambe chonde taunikiraninso za chisankho pa nkhani ya 51%plus.For example if political part A has 40 % ,party B has 31% and party C 25 %.Then political parties A and B can form Government of National Unity that makes them to have 51%.Zinthu zobwereza chisankho in this case is waisting Government resources.Consider this and take this fact to the parliament for discussion.
Yes mwelani madzi bwana DK..... Faka mphweyaaaaaa
More fire DK kuswakuswa kopanda kunyengerera
Umakwana
My vote
Pls Dr Kabambe Insha Allah much effort in Agricultural sector also
Mr Kabambe chonde taunikiraninso za chisankho pa nkhani ya 51%plus.For example if political part A has 40 % ,party B has 31% and party C 25 %.Then political parties A and B can form Government of National Unity that makes them to have 51%.Zinthu zobwereza chisankho in this case is waisting Government resources.Consider this and take this fact to the parliament for discussion.
Kmatu uyu awina 2025
Akwapule anyani amenewa
Kabambe simunthu wamba
Tidzikhala limodzi ku nseuko tatopa ndi manyakawa
😊
Mwana wamzelu uyu
❤❤❤❤ DK 🎉🎉
Munthuyu ndi katswiri🎉
Zoonadi zenizeni osati manyaka alipowa
❤❤❤❤❤❤🎉
❤❤❤
Uyu ndi dolo
Kwabasi kkkkkkkk
Eeeeee muli mfundo
Pangolin
Oh yes powerful