Mr mtanyiwa mokupephani akamakusokonezani mungowulula zisisi zonse basi za if ya bale athu komaso chilima mukatelo ndiye kuti athu osewo mwawatha basi afiti amenewa , koma timakuyikizilan mapephelo basi ❤❤
How are you Mr Mtanyiwa, The fact is that we're in new generation we don't have any piece of time entice Chakwera government we're tired with him as soon as possible what happened in Kenya get prepared for Malawi
I think ndi ku sea point not sea port, Koma nde afera zainitu konseko kufuna ndlama? Koma nde ku Mcp kuli ndalama zogawatu m'malo mogulira mankhwala mzipatala
Kusunga ndalama zotero mu phone ndizotheka Inu. Sikuti zonse zingalowe pa kamodzi. You can have ma business and be doing transactions through Airtel money. Momweso amayendera madolo ndizabwino kukhala ndi dollar zambiri mu phone so that they can withdraw everywhere and anytime they need it than kudalira bank. Account siyimakhutatu kuti basi zakwana.
Athu aku Cape Town James yi musalore akhudze Comrade, ndipo tonse tieni timupange Comrade soak mu Mwanzi wa Yesu. A ndemvu za mwai it’s obvious anafumbatitsidwa, anasitha sakudzudzulaso, zoona kulolandalama za magazi kukutsekani pakamwa ? Shame !!! Mzimu wa Chilima uchita nawo athu amenewa
Eishhhhhh 15 million yongogawa kufuna kuchotsa moyo wa nzawo kodi nde kuti anthu amene mumapanga ziwembu zopha anzanu inuyo mudzakhala pa dziko pano mpakana kale kale? Koma ndalama zukugawidwazi ndi zabwino bwino???????????
Kodi Bakili Muluzi akuti chiani pa za Malawi Democracy imene anaibweretsa? Kodi Ithere mnjira imeneyi? Auzeni a Malawi zoona pa nkhaniyi Munthu wobadwa from 1990 mu Malawi akuti MCP ndi yabwino, A Bakili nenanipo kanthu zinthu zisanafike pa mwana akana phala
KOD antanyiwa tatifusiran kut kod a zodiaki omwe timkawadalira pa tiuzeni zoona program ndi kunena zachisisi bwAnj PANO kuli ziii ndipo akumaika chiprogram china chanchingrez chonyasa apo ayi akuzimitsa trassm8sions.tatifusiran kut bwanj kod mwakhala chete?
Let's act like Kenya Malawians..... Why we are sleeping
Koma ndipo live
Thats the only way
yes.. Koma amalawi mantha.. lets act like kukenya pls..
I support
Agree
Tiuzeni bho Za Uyo waku Capetown Ife tikamukonze tokha omrade
Boooon kalindo ndi muthu wa a Malawi ndalama waberazi wango zivutisa wabayo the dc ❤❤❤
Pa sea point ndipafupi timusaka james ameneyo ifeso tili konkuno ku capetown
Osadandaura zophebwa ambuye alinawe ntanyiwa 🙏🙏🙏🙏
May God protect you Mr Man we lv u ntanyiwa
Malawi kugona....i salute kenyans for standing up for there country
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you
Mr mtanyiwa mokupephani akamakusokonezani mungowulula zisisi zonse basi za if ya bale athu komaso chilima mukatelo ndiye kuti athu osewo mwawatha basi afiti amenewa , koma timakuyikizilan mapephelo basi ❤❤
For the next generation yet unborn, whenever you come across this comment section, just know that we once alive this day to witness this masterpiece.
Mcp boma la ma savage thats why amangolimbana ndi anthu malo moti aziendesa dziko thats why zawakanika zitsiru za anthu
Osaopa comrade tili nanu limodzi makapewo sangapange kathu
Get well soon comrade
Nthanyiwa God is neya with you 🎉
Ofunikano tiyambe kuwatengela a police ku court.
Amaonjeza amenewa, too corrupt. Abweze zimenezo
Sea point, tithana naye timuyedzeka mwana opusa
Proud of you mtanyiwa ❤❤
Q@a,
Trully our own independent journalist #The truth always on point
Fire hit!! Ntanyiwa umakwana keep it up more 🔥🔥🔥🔥
Tell us everything ntanyiwa because you are not talking about one country talk about other countri❤❤❤❤❤
How are you Mr Mtanyiwa, The fact is that we're in new generation we don't have any piece of time entice Chakwera government we're tired with him as soon as possible what happened in Kenya get prepared for Malawi
Ndipo Nzimu wa chilima uwanyetsadi anthu God will protect you
Ntanyiwa umakwana bro mulungu azikudalitsa always
We love you comrade ❤❤❤❤❤ keep it up
Keep up with good job, sir. Never give up.
Zikomo pa ntchito yomwe mukuigwila bwana. Praying for your safety. Be protected!!
Asanapagechoipapainu chiwachitikileiyowo paja yudasianaziona
Ma gardener boy amu seapoint amenewo
Tipaseni phn yamunthu ymwe Ali ku seaport pls
Timakunyadila ntanyiwa tili pa mbuyo pako
tiuzeni zooona bg tilinanu best tv ever 🎉
Mulunguakutetezani tilipokukupepelelani masalimo 91:1/15
Amakhala ku sea point
Tamuziwa ku capetown kuno,will show him
I salute you, Achalume , kumtunda
I think ndi ku sea point not sea port, Koma nde afera zainitu konseko kufuna ndlama? Koma nde ku Mcp kuli ndalama zogawatu m'malo mogulira mankhwala mzipatala
More fire
Why bon kalindo himself never raise this issue of 25 million
Mtanyiwa more fire
Kusunga ndalama zotero mu phone ndizotheka Inu. Sikuti zonse zingalowe pa kamodzi. You can have ma business and be doing transactions through Airtel money. Momweso amayendera madolo ndizabwino kukhala ndi dollar zambiri mu phone so that they can withdraw everywhere and anytime they need it than kudalira bank. Account siyimakhutatu kuti basi zakwana.
Athu aku Cape Town James yi musalore akhudze Comrade, ndipo tonse tieni timupange Comrade soak mu Mwanzi wa Yesu. A ndemvu za mwai it’s obvious anafumbatitsidwa, anasitha sakudzudzulaso, zoona kulolandalama za magazi kukutsekani pakamwa ? Shame !!! Mzimu wa Chilima uchita nawo athu amenewa
Ingong'alula kalikonse tikadziwa
A Malawi tinabadwa ndi kukula mwa mantha kwambiri komanso umphawi
Welcome back.!
Eishhhhhh 15 million yongogawa kufuna kuchotsa moyo wa nzawo kodi nde kuti anthu amene mumapanga ziwembu zopha anzanu inuyo mudzakhala pa dziko pano mpakana kale kale? Koma ndalama zukugawidwazi ndi zabwino bwino???????????
Abweze ndalama za bon kalindozo or else they will see Nairobi in Lilongwe
Ndipasengi number yake naneso ndine ntonga ndimagwira konkuno ku Cape town camp's sea point ndimafika ifweyo tithana nayo galu yoo
ine kupanda kumva audio yanu ndi abon kalindo komasso wa Bakili sindmva bwino plz ABOMA NDALAMA ZAKALINDO BOMA LIBWEZE
even voice isamanveke bobo ife ndiosangalala Nanu comrade komaso wa Ku Capetown tipatseni number yake
Comrade Ntanyiwa, amene akufuna kukugulisayo timuonetsa nyekhwe chifukwa pomwe akukhalapo ndikuoadziwa.
Awonatu nyekhwe ameneyu.
Mr Bon Kalindo, mwayenera kulimanga boma pamlandu okuberani ndalama zanu mwachinyengo.
Boma limangidwe
Tigaileni map please
James nkhala nsonga ameneyo ndi citizen wa nkhata-bay.kapena anachita kubwera ku nkhata-bay
Comrede Ntanyiwa tiwuzeni zakape amene alikunoyo ku SEA POINT CAPE TOWN
Tiwawuze kuno makaladi amukoze ameneyo ndi ngalu kwambiri munthu ameneyo
Ntanyiwa anthuwa achulukila manthha chifukwa chilungamo chikunenedwa ndipo akudziwa kuti zawo zadela,komanso Ntanyiwa sangaphedwe mwachibwana ngati m'mene anamuphela chilima ndipo nzimu wachilima ukuyenda paliponse mulungu simunthu
kukhale Ku (sea point) kumeneko kapena? kapena cos Ku sea port sinkukuziwa koma Ku sea point.
Ayaluka sanati akazizi amenewa,,, Chilima R I P
God bless you brother
I agree, chakwera must resign with immediate effect
Kodi Bakili Muluzi akuti chiani pa za Malawi Democracy imene anaibweretsa? Kodi
Ithere mnjira imeneyi?
Auzeni a Malawi zoona pa nkhaniyi
Munthu wobadwa from 1990 mu Malawi akuti MCP ndi yabwino,
A Bakili nenanipo kanthu zinthu zisanafike pa mwana akana phala
Acomrade Mtanyiwa ife aMalawi ochuluka tilipambuyo panu and Mulungu alinanu .ife tidzaimananu pamodzi.zaimfa yaa chilima ndyopweteka koopsa imene mmalawi izavuta kuiwala.
A cipriano mukuwononga dzina langa ndi khalidwe lá anthu amene ali dzina lá cipriano
Kawawa pitilizani kutidziwitsa zomwe zikupanga zitsiluzi kuphedwa simugaphedwe mr tanyiwa komano zikuzuzika zonkha zitsiluzi tikati tantsala ndi wayires Malawi muno ndi Limpopo bas zinazose zagulidwa ndi mcp
mapephelo anthu ndi misozi yanthu ikutetezelani A ntanyuwa uyuyu uyu Mulungu amuone ndikumudzudzula ayelekeze aone
Bambo Mtambo ndi HRDC yonse, bwererani mu mseu,
Zinthu ziipitsitsa kuposa mnthawi ya Pitala.
MCP ndi mkango wakudya nyama,
Kodi isinthabe pano.
Mwambi
"Mhpaka samuuika mu jaketi, akupala mwiniwe"
KOD antanyiwa tatifusiran kut kod a zodiaki omwe timkawadalira pa tiuzeni zoona program ndi kunena zachisisi bwAnj PANO kuli ziii ndipo akumaika chiprogram china chanchingrez chonyasa apo ayi akuzimitsa trassm8sions.tatifusiran kut bwanj kod mwakhala chete?
Antanyiwa kod mulibe mfut ija amat snaiper chonde ngat mulinaayo ndibweleken. Asatijaile
Timakunyadira pazomwe mukuchita
Koma uyu otchedwa James Khalasonga akuseweratu. Wangoona kudziyamba sea point no where to kubisala
Muchile nsanga akulu chifuwacho inu patali ndi anzanu wose pano kwabweraso arwale more fire
A Police kuba ndalama za Booon Kalindo? Zopatsa manhazi, manhazi, manhazi a Malawi. Zafika apa?. Kulira Kamuzu.
KODI AZIKHALI ,CHIMWENDO,KUKUYU CHAKWERA, KUFA KWA CHILIMA SIKUNAKUKWANENI ,MUKUFUNASO KUMAPHASO ANTHU ENASO KODI INU KUPHA SIMUMAPANGA MANTHA MUZAYANKHATU IZI KWA MULUNGU IZI AGALU INU
KOMA PLEASE NDALAMA ZA BON KALINDO MPASENI MUSANAFE OSAKOZA SITIPANGASO ZA KUPOLIC CHIFUKWA KUMALAWI KULIBEKO POLICE KOMA MUSOWA TIKUTI BWEZANI NDALAMAZO TIKUTI AGALU INU
Takunyadilani antayiwa inu ndi athuathu❤❤❤❤❤❤❤
Koma James ameneyu ampatse mabody guard amphamvu athera konkuno ndi kape ameneyu
Osaopa ntanyiwa tili kumbuyo kwako chotigwera chitigwere titsatile chilima
Ulibho iweusazafeyi uzangosowa umaitha t
Amtanyiwa ajems woo azisiya ndalama zomwe alandilazo jst send the number ifeso tilikuno ku captown mazula amati bonke lawo bebathi bahlanganiphile basematuneni
Mtanyiwa big up
ndalama mwatchulayo siyilowa mu phone mmm boza basi.evin kunoko ku RSA KULIBE EWALLET YA 50PIN AMALAWI CHEPESANI BOZA
Tingokonza dzinalo ndi Sea point not sea port l know the place
Ka James ndi muzeleza so ñganya leka kopa
Ndipo mamulungu yeka atimenyela nkhondo ntanyiwa mulungu akudaliste kodi Boma limabanso
Kodi katundu wa a Malemu a Chilima momwe anapemphela Aku banja Lao kuti awabwezere Aku banja, zinathekadi.
Mulungu si jemus ayise mtanyiwa uwoloka nafe limozi ndichikhulupiliro
There is no secrete under the sun. Chilichonse chizaulurika
Mwana ameneyu akanandiyandikila ndikanakoza ka James komakasamale ifeso tili kokuno tikafufuza kameneko
Tikamati uyu amangopeka khani moti 25 mita ingakhale 4n ya kalindo 😂😂😂😂😂😂😂😂 abale ndiye poti amalawi timasangalala ndimabodza ok tiye nazoni
Ntanyiwa iweyo ndi one
mbambande
Tiri pompano ife mtanyiwa kudikira kwa Inu koma nyimbo yomalizayo imandiwaza kwabasi komaso imandilirisa zedi
Asamale jemus makaladi athana naye kuno achita masewela ndipo ayelekeze tiyambapo ndife kuthana naye....
More fire,more
Mbambande Comrade ❤
Kunama amenewo ataya thawi yawo pachabe. Inu denkhani sangakupezeniyi.
Tipatseni number yakhe kuno jozi
Koma boma ilili ayi zafika posauzana koma mukanazilemekeza matsiku akuthera ku chiseko
Lipopo FM number number one
25 million ilowa mu fon? Azanthu airtel tiyakheni
Iwe national Bank more sukuidziwa et ndalama zikakhala mu fon
Kdi Layton Mangochi Ali kti sakumveka mawu Comrade ?
Akudya ndalama zaboma
Seapoint not seaport
mulungu akudalitseni boss
Ife tili mu gugs ndiye wa sea point sitimamuwopa ndi ana akumpanda