Amene timamunyadila Lulu ndi voice yake yabwino let's gather here with some like, each like or comment i will come back to watch this masterpiece again ❤
The song is so beautiful,very beautiful Koma Pena tikumvera makanitu makamaka koyambililako it needs more balance,production yadumphako moto,koma guys mwakunga...🔥🔥🔥🔥
Amene timamunyadila Lulu ndi voice yake yabwino let's gather here with some like, each like or comment i will come back to watch this masterpiece again ❤
We here ❤
Amatha lulu
Anabwela kuzakhala uyu mpaseni plot
Amatha adawa
Omwe tikuchoka ku mikozi let's gather here🔥
For the love of lulu being my favorite artist ❤🎉
Lulu the cool man with beautiful voice ❤️🔥❤️🔥💥
My best musician ever💥💥lulu
Kell kay fans let's gather here😎😎
Njovu zakumana, Malawi has talent, the kwambiri sisters ku backing vocals❤ 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Top fans from mikozi let's gather here 2024 to support our brothers 🎉
We here🎉❤❤
Ndipangeni like ndizibwerabwera kuzawonera
🔥🔥🔥…Ine ndikuona ngati Lulu pampandowo samafunapo… amafuna aime azivina zake zija!
Mwachidule azidikula
@@GP_memes36 Basitu lol
Team lulu ❤❤❤
The song is so beautiful,very beautiful Koma Pena tikumvera makanitu makamaka koyambililako it needs more balance,production yadumphako moto,koma guys mwakunga...🔥🔥🔥🔥
My best song from Lulu I love it
Here in USA I watch this always
Kall kay he did it right 👍 there.. same one kiss my cmnt
I know from day one I saw this kuti ikhala hit,,, two legends meet beat yafapo 🥳🥳💥💥💥🥳 Moyo wina 🙌🙌🥰
Ndaikonda nyimboyi 🥳
Team Lululu! Mwana Lululu.
It's Mathumela Babe. 🎉
Iyi yabwera munthawi yake
Nyimbo ndiya boh.. koma production nde sizinayendetu..... Zikuveka ngati mastering inavutirapo......
My all time favorite artist 🔥 ❤ 🔥
Ilibho koma production mbola ,beat ikuveka kwambili than voice
Tipangen like
🔥🌹🌹🌹🌹
Nyimbo yabwino singapose apa maka chorus mwaipha hvy hvy kell kay ulemu wakoso kachikrna 🔥🔥🔥
Ine kuonakuchedwa koma pot mbuye ndi okongola🔥🔥🔥
Kawale boys 🎉🎉🎉🎉
I can see myself dancing the tango with special someone on this one, it's 🔥🔥🔥
Nyimbo yaikulu🔥🔥🔥
Bumuuu.. Machine Lulu, keep the fire burning bro
Kawale 🔥🔥🔥🔥🥰
I love this song from 🇿🇲 (let's show love guys 🤩)
Pangolin ngat bakili muluz tv
Notify ikatuluka🥰🥳
Lulu panyapako nyimbo waimba bwino iyii 🔥🔥🔥
Aaah 🤣😆😆😆
Aaaaaàa kkkkkkkkk
Patiently waiting for this bomb🔥🔥🔥
Ndi zinkhoswe zatchukazi😁🔥🔥🔥🔥
Ikuchita kukoma 😍😍😍 welcome Lulu
Ilove you guys,mwapha hits apa🔥🔥🔥
❤❤❤❤❤always always and forever my favourite legend🤗🥳
I like how Lulu was changing styles
After a very long period of time, apapa Lulu wakhilanso.
Ife pheee kudikila inu Mfumu💓💓
Mukapitiliza maimbidwe awawa! I swear mafanawa sangapezeso mpata!
Very nice tune...but yeah production yavutilapo heavy...
Ndipo ingomveka phokoso
I wish to understand that
Yeah
Lulu is back 🎉🎉
We here🥰
Anamanyonyolo pamayimbidwe zakumana🔥🔥🎶🙌
Whosoever coming from mikozi kiss my comment 🔥🔥✊ so that ndibwereso
With dat voice or tune pliz tipangile ya gospel..
Master piece ❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥💃💃💃💃
Tikudikila katswiri kwambiri 🔥🔥
Lulu dolo ka 1000🔥🔥🔥 lets gather here lulu fan's
Hit lero ndinayilota🔥🔥🔥🔥
Nyimboi ili boh heavy for those using ma sets but without that ikumveka ngat zida zikupelewela ukali pobalansana ndi mau
Nice song ndinu madolo🔥🔥🔥🔥🔥
Nice one Lulu en Kell Kays❤❤❤
Moyo wina,true story of my life..nyengo zomwe ndadusamo.
Lulu has been my favorite since I was young
Waiting
Uyu bwanji sakufwifwa eehhh. Ndiwe dolo Lawrence 💥💥
Team Mathumela lets goooo
Nyimbo ya lulu sitiweluza 1st listening
Lulu ndi legend.
Koma the guy doesn't age ine lulu namudziwa 2003 ndili standard 3 wangonenepa basi.
Ndiye madolo akakumana ❣️❣️
I like ito
Patiently waiting 🥳
Waiting till it is out
Joyfully waiting for the song of the year🤗🔥💃
Another life 💝💝💝💝
Tivina chaka chonse 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Hope ndinyimbo of the year😂 waiting patiently 🔥❤️
This is so amazing! Yovinika❤
Ilibwino osati masewera❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤team lulu gather here 🔥🔥🔥
Waiting my best artist
My favourite 🔥🔥🔥 artist
🔥🔥🔥 matchamani akumana
This song is just a vibe 🔥🔥🔥🔥
Wapha aise🔥🔥🔥🔥🔥
Kanyimbo kodekha. Very beautiful voices
This will be my birthday song , coz in 14 that's my day
Chichewa ndachivutikila kuchimva ichi....nice nice
Team Kell Kay 💪💪💪
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥hit mbambande
inuo Guys ulemu wanu 🔥🔥🔥🔥
I like this man and his music , keep going boss
Nyimbotu iyii mfumu mmmmm MWAINU NDIKONDWA
Nice tune, legendary
Tune chili super ichi!
💥💥💥💥💥💥💥💥💥
Kawale yakumana ❤️🔥🔥🔥🔥
Moyo wina on 🔥🔥🔥
Patiently waiting for the song
Shasha ka 3 million
Lulu amaganiza zoopsa pa nyimboyi koma production silibho koma akuluwa ndi legend
Exactly 🎉
Anyamata awawa ineyo amandiwaza Lulu anandipangitsa kuyamba kuyimba ku primary nyimbo zake
My favorite Lulu🥰
Waiting my favourite artists
Wow great voices ikuvekaso mwawuzimu zimu nyimboyi
amene akuva ngt mmene ndikunvera inei abwele apa
Great song 🔥🔥
Ndayikonda 💯
Production eeeeeh .
Koma chi lulu ndakatundu
Za azibambo🔥🔥🥳
Kell Kay 🔥🥳
My all time favorite 🔥🔥🔥🔥