A Brian Banda program yanuyi yalero ikanakhala album tikanangoti, the very best of Brian Banda Hot current because mwayankhula chilungamo, kaya nchifukwa choti IMF yavumbulitsa Bomba mukanakhala kuti m'mbuyo monsemo mumayankhula chonchi bwenzi mwina zinasintha komakayankhulidwe kanu m'mbuyomu mumanyengerera andale makamaka olamula achipani Cha mcp zimenezo ndi chifukwa anthu ambiri ngakhale kumamidzi amakonda kumvera pa social media , ngati kumamvera achina Limpopo , Ntanyiwa, Bakili Muluzi TV ,Bon Kalindo ndi ena amene amanena chilungamo mupotolize monga m'mene mwayambiramo thank you guys
Kkkkkkkk Jessei yemweyo,koma umbuli uli Ku a m c p iiiii chipani chochitisa manyazi Mai kabwira zomwe mukupangazi mudpitadi Ku school?mwasavuka Mai sinthani,mwabwera uyo, uve weniweni,sinthani
Akabwira ndimunthu wopita ku school, koma ndi mbuli ya munthu akakadayenderabe zomwe zija za Kamuzu ngati chipani chimodzi,sasiyanitsa ntchito za chipani ndi ntchito za boma ndichifukwa chake akufunanso kutengera dzikolli konkuja ku one party system ndiye za a Jesse Kabwira mbuli yophunzira
Inu ndinu ma journalists tell Malawians the truth for once….This govt is borrowing too much because it’s under pressure to deliver on its unrealistic promises
A malawi we dont know what we have to know!!! Dzik ili amalamula nda zungu, try to understand mmen dziko limayender la malawi kt anth muziwauza zachilungam coz pal zinth zambir zomw simaziziwa zimen mmaziona ngat ndiza normal coz munakula muzimenez km am telling you this organisation called IMF sindimaiona bwin.. try looking from the bottom of our mavut kt muth kuzindikira.... Let me ask you, azungu amatipats ngongol even when tili ndingongol ina kal y?
Man in the middle is just a rumour monger and not an analyst. Let only analysts continue to participate, otherwise the program will loose its usual taste
Mwasowa zokamba a Chafumuka. Ngati munthu akupanga chitukuko osayamikira ndi chiyani? Ena akumati bomali palibe la chita. Zitukuko zomwe akupanga a Chakwera 2:15 ena anawonongapp. Pena ena anangomanga za substandard. Analysis apo pokha yakuvutani bwana
Akabwira ndimunthu wopita ku school, koma ndi mbuli ya munthu akakadayenderabe zomwe zija za Kamuzu ngati chipani chimodzi,sasiyanitsa ntchito za chipani ndi ntchito za boma ndichifukwa chake akufunanso kutengera dzikolli konkuja ku one party system ndiye za a Jesse Kabwira mbuli yophunzira
Burkina Faso ndye chitsanzo cha africa ndizotheka kukhara ndikutukuka opanda azunguwa.... Nthawi ndikachitsiru
This too much chakwera and his cabinet they r taking us for granted...but 1 thing...this thing don't last for ever....
Truth well told. The situation on the ground is pathetic, and we as a country are headed for disaster. Hot Current is really hot 🔥 🥵 🔥 🥵
A Brian Banda program yanuyi yalero ikanakhala album tikanangoti, the very best of Brian Banda Hot current because mwayankhula chilungamo, kaya nchifukwa choti IMF yavumbulitsa Bomba mukanakhala kuti m'mbuyo monsemo mumayankhula chonchi bwenzi mwina zinasintha komakayankhulidwe kanu m'mbuyomu mumanyengerera andale makamaka olamula achipani Cha mcp zimenezo ndi chifukwa anthu ambiri ngakhale kumamidzi amakonda kumvera pa social media , ngati kumamvera achina Limpopo , Ntanyiwa, Bakili Muluzi TV ,Bon Kalindo ndi ena amene amanena chilungamo mupotolize monga m'mene mwayambiramo thank you guys
Mumagaza bho,jessie kabwira akunyanya kudzitukumura akuona ngt anafika
Kkkkkkkk Jessei yemweyo,koma umbuli uli Ku a m c p iiiii chipani chochitisa manyazi Mai kabwira zomwe mukupangazi mudpitadi Ku school?mwasavuka Mai sinthani,mwabwera uyo, uve weniweni,sinthani
I like the word tipatsane ulemu 😢😢 otsamangoti boma ndilomweri ngati ndi ufumu
Well done gyz kulakhuka moveka Bwino 💯💪
Tikadalibe muu kapolo. Mzungu akadatilamulira, akudawa ndizikwangwani...
We are with you from uk ❣️❣️
YES 👍👍
Mavuto onsewa sikulina Mulungu azatiyankha ndithu wawa❤
You guys God bless you
❤ Mumakwana
Akuti nansonjola alipo m'bomamo kkkkkk😂😂😂
Akabwira ndimunthu wopita ku school, koma ndi mbuli ya munthu akakadayenderabe zomwe zija za Kamuzu ngati chipani chimodzi,sasiyanitsa ntchito za chipani ndi ntchito za boma ndichifukwa chake akufunanso kutengera dzikolli konkuja ku one party system ndiye za a Jesse Kabwira mbuli yophunzira
Speak truth to power Malawi
Tidakali pa thawi yakulila chilima mzimu wao uuse mmutende SK 😢😢
Well done
Job well done
Inu ndinu ma journalists tell Malawians the truth for once….This govt is borrowing too much because it’s under pressure to deliver on its unrealistic promises
Nde kt Wa bakili mulizi TV uja amakamba chilungamo
Kabwira akufuna kudyanawo ndalama kuba basi
Bomali ose saziwa kathu
🙏🙏🙏🙏🙏 All guys God bless you all
Jesse watengetsa anayenera kusiyanitsa ntchito zaboma ndi chipani
Good message Jonathan
Brian take care asakuphe
Kkkk nose ulemu wanu lelo mwafika ndi truth
mcp ngakhale yitatani yitatani yikutuluka boma basi
Anyamata mwandiyakhulira bwino Maka apo akumati boma ndilomweli pa mwalasa, tipatsene ulemu di, ndinthu fukwa choza mawa sichidziwika asamale mayakhulidwe awo
Azungu atigwira ufiti
Azibambo inuyo mumaona patali ulemuwanu
A malawi we dont know what we have to know!!! Dzik ili amalamula nda zungu, try to understand mmen dziko limayender la malawi kt anth muziwauza zachilungam coz pal zinth zambir zomw simaziziwa zimen mmaziona ngat ndiza normal coz munakula muzimenez km am telling you this organisation called IMF sindimaiona bwin.. try looking from the bottom of our mavut kt muth kuzindikira....
Let me ask you, azungu amatipats ngongol even when tili ndingongol ina kal y?
Amereka akayetsemula Malawi imagwira chimfine. N’chifukwa chiyani timayembekezera kuti atiuze zimene tikudziwa kale?
Man in the middle is just a rumour monger and not an analyst.
Let only analysts continue to participate, otherwise the program will loose its usual taste
Iyii idali mbambande
Chitukuko chakechiti chokuba ndalamacho😂😂😂
Adayedzeka kaye
Mofaya
Banda
Ndalamayo agoika matubamwawo akuba pamodzi ndiabaleawo
Boma silomweli tizasankha September 2025.
Tiyeni nazo ❤❤u guys
sangamuphe ase
Mpatseni traole dzikoli
😂😂😂😂❤❤❤
Otsogolerayo ndiye olephela
Muze wa mcpyo
Amereka yanenazona agobandalama
Program ikukoma kobasi anthu inuyo mumakwana kobasi
Kkk kwavuta
Palibe choyamikila
Hot current iyi ndiye inalidi hot hot😂
Mwasowa zokamba a Chafumuka.
Ngati munthu akupanga chitukuko osayamikira ndi chiyani?
Ena akumati bomali palibe la chita. Zitukuko zomwe akupanga a Chakwera 2:15 ena anawonongapp.
Pena ena anangomanga za substandard.
Analysis apo pokha yakuvutani bwana
Program ikukoma kwabas bwana muzimangilitu pitani pa TV 📺 mukasuse
Kaoneleni MBC malume
Aaaaaaaaaa chitokukocho akupangila kwanu
Awanso nde achitsilu bwanji
Kape uyu akatero wadya nawo
Chilima analichi vhitsilu wachabe chabe galu opanda tchoto mavuto osewa chifukwa cha iyeyu