Achimwene ameneo ndi mbali imodzi ya maitanidwe anu dzukani ndikupeleka moyo wanu kwa mulungu chotsani mantha pemphelo pakamwa landilani yesu akhale mbuye ndi mpulumusi wa moyo wanu iyi siya kwa sing'angaso ayi koma mwini chilengedwe
Mulungu amatha ndipo salephera mulandireni yesu kukhala bwenzi ndi mpulumusi wa moyo wanu coz singa'nga ndi mfiti net work yawo ndi imodzi komanso munthu amalephera koma mulungu salephera.mukatero pezani munthu wa mulungu akupempheleleni.zonse zitha mu dzina la yesu ziwanda zimanjenjemera,matenda amathawa,kalikonse ndikotheka iye amene anakulengani ndi amene angakumasuleni.
Achimwene musaganizenso za msing'ang'a, inuyotu midalire Mulungu pa moyo wanu. Mukangoyerekeza kupanga za sing'ang'a afiti amenewo akugonjetsani basi. Imani pa maso pa Mulungu ndipo muona akukupangirani zazikulu. Kumbukirani ana a Israel ali paulendo wawo opita ku dziko la malonjezano, aigupto amawalondora koma Yehova anamuudze Mose kuti awaudze aziyenda lupita chitsogolo. Ndiye inu mukangocheuka paulendo wanuwo, simupambana china chili chonse koma muimebe pamaso pa Mulungu ndipo mukuyenera kusala kudya ndi kupemphera. Mukumbukireni Estery mmene amafuna kupulumutsa mtundu wake, analowa pa emergency fasting ndipo zazikulu zinachitika
Inutu mungolimbikila kupemphela . Ife pakwathu pali za ufiti tayesa kuyenda mwa asing'anga zalepheleka pano timangopemphela basi ndipo zikutheka ndichikhulupililo mwa yesu khristu
Ase zimenezo za simple kutha and siku limodz km sitiyuz asing'anga paja sing'angaso ndi mfiti so ngt ukufuna ndyakhulen tikuuzen zochita zosezo zithu insha Allah nde ndyakhulen
Kuona kwanga musaikepo Zamakhwala chifukwa asing'anga ndi network Yao km pemphero ndy chida chothera vuto lonselo or amfiti atachuluka bwanji palibe angafane nawo ine ndi mboni wapemphero ndi pembedzero chifukwa pa 4 January chaka chomwechi ena amayesa zida kundimenya ndihamala yaumfiti km ndinachira Ndipo mwadzi wanga sanapindulile ndy inuyo muyang'ane kwambiri Mtanda imene Yesu waku Nazareth anafera
Musagwirise ntchito zamakhwara inu mukaikamo zamakhwara siziyenda ai taiman pa maso pa mulungu mulungu ndiye chida chachilichose iwe bare ili mbari it or mukanaperaka number zikufunika mapephero izi
pezani munthu amene ali odzozedwa ndi mzimu woyera akupempherereni mumasulidwe ndipo musaphstikize ndi kwa a sing'anga dalirani Yesu yekha. m Mukaphatikiza zitsamba ndi zauzimu palibe chimene chisinthe mapeto ake akuphani.
Uli mbari iti ya kuno ku south Africa ase tipatse number yako ngati uli kumarawi tikuthandize ngati uli kuno ku South Africa tikuthandizaso zimenezo zitha mu dzuna la mulengi mwini moyo
Pofunika ma pemphero achimwene chifukwa dziko ili laipa. Timaonana kunja kwa thupi koma zamumutima wazako zimakhala zochuluka. Koma chigonjeso cha zose ndikuyima pa maso pa mulungu siku ndi siku.
Ulore luti moyo wako uyikidze manja mwa mulungu osalore kuti chikhulupiliro chako chonse uchitsiye kwa asing'anga peleka zovuta zako zonse kwa mulungu basi mavuto Ako onse azatha
Muyenera kukhala mu moyo wa pemphero nthawi zonse, pezani anthu omwe amapemphera mu mzimu ndi mchoonadi, koma musankhe njira imodzi osati kuyangana kwa Mulungu komanso kwa satana, sankhani njira imodzi
God thanks ,mayi ako was ur prayer wourrior, Praise God
Achimwene ameneo ndi mbali imodzi ya maitanidwe anu dzukani ndikupeleka moyo wanu kwa mulungu chotsani mantha pemphelo pakamwa landilani yesu akhale mbuye ndi mpulumusi wa moyo wanu iyi siya kwa sing'angaso ayi koma mwini chilengedwe
Amen
Mulungu amatha ndipo salephera mulandireni yesu kukhala bwenzi ndi mpulumusi wa moyo wanu coz singa'nga ndi mfiti net work yawo ndi imodzi komanso munthu amalephera koma mulungu salephera.mukatero pezani munthu wa mulungu akupempheleleni.zonse zitha mu dzina la yesu ziwanda zimanjenjemera,matenda amathawa,kalikonse ndikotheka iye amene anakulengani ndi amene angakumasuleni.
Achimwene musaganizenso za msing'ang'a, inuyotu midalire Mulungu pa moyo wanu. Mukangoyerekeza kupanga za sing'ang'a afiti amenewo akugonjetsani basi. Imani pa maso pa Mulungu ndipo muona akukupangirani zazikulu. Kumbukirani ana a Israel ali paulendo wawo opita ku dziko la malonjezano, aigupto amawalondora koma Yehova anamuudze Mose kuti awaudze aziyenda lupita chitsogolo. Ndiye inu mukangocheuka paulendo wanuwo, simupambana china chili chonse koma muimebe pamaso pa Mulungu ndipo mukuyenera kusala kudya ndi kupemphera. Mukumbukireni Estery mmene amafuna kupulumutsa mtundu wake, analowa pa emergency fasting ndipo zazikulu zinachitika
Ndipo nkhaniyo ndiyoona mukuyenera mulimbe ndi mapemphera bac
Mavuto onsewa pitani Kwa mulungu ndipo zitha
Muzipemphera mosalekeza mulungu samalephera chifukwa imeneyo nkhondo mpaka kukusatani ku jon kuno ulendo ndiwa utali kaa
Aise umpeze sheikh amene ukumudziwa wapafupi umufotokozele akusomela surat ruqia ndi surah yamphavu kwambiri ziwanda zonse zichoka
Muzipemphera tsiku lililonse Pogona Mulungu amatetezera zimenezo
Mukamagona komanso 12am dzukani muzipephera zonse zitha musayerekeze kudalira amakhwala muluza nazo moyo wanu broo dalirani yesu basi
Zamakhawalazo ai, koma munfolimbika kupemphera kusala kudya ,komanso , pakati pausiku uzidzuka nkuyamba kupemphera, pemphero lachikhulupiliro , limamasula komanso umatetezeka
Inutu mungolimbikila kupemphela . Ife pakwathu pali za ufiti tayesa kuyenda mwa asing'anga zalepheleka pano timangopemphela basi ndipo zikutheka ndichikhulupililo mwa yesu khristu
Ine afiti adasiya kundidinikiza chifukwa chodziwa kapempheledwe kake ndisanagone
Pemphelo lokagona lidzikhala chonchi!
1.
Lapa machimo ako.
2.
Akhululukile onse okulakwila ndipo onse mwawalakwila mupemphele kuti akukhululukileni.
Yahuah ndi chikondi sichidani ayi
3
Wazani mwazi wa Yahusha munyumba mwanu.
Dzikutileni ndi mwaziwo.
"Dzina la Yahusha and Yahuah ndi moto onyeketsa"(nenani katatu)
Mangani mpanda wamoto kuzungulira nyumba yanu.
Kenako nenani "pemphelo langa ndikulitumizila moto wa Yahuah
4
Nena "chilichonse choipa chagonja". Chilichonse chogwila ntchito ya satana chisafike pamalo ano".
Pomaliza musanene kuti "amen", "Jesus", "God". Ayi
Ntchulani original names "Yahusha and Yahuah" basi
"
You can pray for 5 minutes and over
Brother yambani kupemphera kwambiri usiku muzidzuka kupemphera
Koma pezani zaitumiki enieni azikupemoherrera
Tiima Nanu a Jojo Yesu Yekha ndeyankho
Mulungu akuyendere bro sataya wake
Ase zimenezo za simple kutha and siku limodz km sitiyuz asing'anga paja sing'angaso ndi mfiti so ngt ukufuna ndyakhulen tikuuzen zochita zosezo zithu insha Allah nde ndyakhulen
Tiuseni amwene
Kuona kwanga musaikepo
Zamakhwala chifukwa asing'anga ndi network Yao km pemphero ndy chida chothera vuto lonselo or amfiti atachuluka bwanji palibe angafane nawo ine ndi mboni wapemphero ndi pembedzero chifukwa pa 4 January chaka chomwechi ena amayesa zida kundimenya ndihamala yaumfiti km ndinachira Ndipo mwadzi wanga sanapindulile ndy inuyo muyang'ane kwambiri Mtanda imene Yesu waku Nazareth anafera
Pephelo limatha zose
Inenso ndadutsapo nyengo zimenezo broo akazi awa mmmmm koma ukaima mmapephero zonse zimatha,inuyo ziperekeni kwamulungu broo zonsezo zitha ndipo mwayi wanu utseguka umboni ndilinawo
Komano ndiwe opusa kwambili chifukwa chiyan u
Maziyamba zankazi wina pamene mavuto azankazi wina sizinathe
Musagwirise ntchito zamakhwara inu mukaikamo zamakhwara siziyenda ai taiman pa maso pa mulungu mulungu ndiye chida chachilichose iwe bare ili mbari it or mukanaperaka number zikufunika mapephero izi
pezani munthu amene ali odzozedwa ndi mzimu woyera akupempherereni mumasulidwe ndipo musaphstikize ndi kwa a sing'anga dalirani Yesu yekha. m
Mukaphatikiza zitsamba ndi zauzimu palibe chimene chisinthe mapeto ake akuphani.
Pempheran kolimba mulungu ndiye amatha basi osadalila asinganga koma yesu basi
Akumiji tipaseni # yanu Kuti timuthandize nyamayi
Munthu or atakuikizani mapemphero koma ngati mtima wanu simunazipereke ndisovuta kuti muthandizike inuyo ngati mukuti mukamapemphera zikumasiya ndiye bwanji osazipeleka nokha pamaso pamulungu ndikumapemphera kuti Mulungu akumasuleni komanso izo zisiike? Pemphero ndi chida ndipo pemphero silinama amene amapemphera ndiamene amapemphera wamva mimba amasegula chiseko inuyo sinu mwana mukuziwa choyenera kuchita pempherani ndipo muzipeleke Mulungu nayenso sakhala chete
Pitani kumapemphero brother
Uli mbari iti ya kuno ku south Africa ase tipatse number yako ngati uli kumarawi tikuthandize ngati uli kuno ku South Africa tikuthandizaso zimenezo zitha mu dzuna la mulengi mwini moyo
Uli mbali iti ya South Africa?
Pitiliza kupemphera chifukwa asing'anga sakuthandiza mulingu akukutetezera mzonse wadusazo mulungu Ali namwe akanakupha kalekale anthuwo uzitsalaso kudya
@@Esther-r8cNdipo zoonadi
Za mankhwalazo ayi annon pempherani kosalekeza mpakana china chake chitachitika
Anthu akunsanje ndioopya chonde pempherani molimbika musaelekeze kupita kwa sig,anga
Nkhaniyi ndiyoona kuti afiti alipodi, mazi aunt, uncle amaopsya nthawizina, pemphero ndi chida dzina la Jesus ndilamphamvu kuposa zonse.
Mmmmmmkoma
Sunganimwana Bola moyo palibevulo Mesa azilerayekha😮
Kkkkkkkkkk aisey dzimachitika koma kumusiya munthu chifukwa chaufiti its big mistake 😢
Not nice
Nkhani'yosakhara bho.
Ndikanakhara ine kut kuthekera kofika kumalawi kuno ndilinako..
Ndikanabwera kuzakonza anthu 4 amenewo then nkumabwelera ku SA..
Nomakanjani kubulalaizinja!!!
Bwelani kumalawi kuno muzathandizidwe
Ine ndikuvutika kom iwe zanga wapambana ine
Munthu ameneyu andiyankhule ku inbox kwanga
Eishhhhhh koma nde zowopsyatu
Yambaso ufwiti nawe
Ufiti ndiye entertainment ya kumudzi.😂😂. Masalamusi
Pena pali ponse osati kumudzi kokha
Lakhula nane tinzathetsa dzonse
Undipeze ku inbox zone idzakhala mbili yakare ndikuljmbira pamaso pamulungu sikuti ndidzapanga ndine koma Alison katswili
Hello
@MosesTangwe ndiponyele #yako
Ikani Mulungu patsogolo mapeto ake mudzingokumana ndi mfiti zokha zokha
dziko liziti Ufiti kulibe kumsunu Kwa_____
Pofunika ma pemphero achimwene chifukwa dziko ili laipa. Timaonana kunja kwa thupi koma zamumutima wazako zimakhala zochuluka. Koma chigonjeso cha zose ndikuyima pa maso pa mulungu siku ndi siku.
boma limatidi ufiti kulibe komachosecho ufiti uli ndiiwowo safuna kuti ufiti usionekela bwapadela guys
Muli kuti inuyo kujon kuno tipite kuchurch 😊
Ndinazionapo ine izi ndili wang'ono, ndipo ndimadabwa boma limati ufiti kulibe
Ufiti ulipo
@@yandisialufan9711 .moyo wako uli pachiopsezo
Ulore luti moyo wako uyikidze manja mwa mulungu osalore kuti chikhulupiliro chako chonse uchitsiye kwa asing'anga peleka zovuta zako zonse kwa mulungu basi mavuto Ako onse azatha
Zose akunena ndizowona ufiti ulipo ndipo anthu akutamba
Muyenera kukhala mu moyo wa pemphero nthawi zonse, pezani anthu omwe amapemphera mu mzimu ndi mchoonadi, koma musankhe njira imodzi osati kuyangana kwa Mulungu komanso kwa satana, sankhani njira imodzi
Mulungu salephela kuwaonako ndimphavu yamulungu
Ngati munyozere izo nzanu koma ndiimbireni
Koma zosakhala bwino
Akungopanga matha awa maganizo chabe iya...enafe timatukwana asing'anga kuwamenyaso mambama kma osatilodza bwanji😂 ndiuzeni ndipite kwa mkazi wanuyo ndikamuhede ine iyah😂
Ndiye kt inuso mumatamba😂😂😂
@ReginaMandawala 😂😂ufiti kulibe
Kunjakuno anthu ambili amakhululupilila za ufiti kwambiri
Tapitani kwa prophet chitete
Mmmmm zandikhuza bwanji.....ine kumbali yanga nditha kunena kuti ukangule extra virgin olive oil ndipo...akhale wa original ukasambamo uzizola thupi lose ndipo mafuta ako kuyambala siku lomwe ungagulelo akhale amenewo....ndipo anthu amenewo asiya kukulonda usiku pogona ukuenela kumadzola uzandiuzaso mapeto ake
Zoonad aziika nyumbambo sadzilowaso komaso kudzola
Koma Anthu
Koma zinthu zake
Upte kwa asilam akuthandiza
Jesus
Eeeee tidzakwatiwa nazo ndi afiti tisakudzwa....ambuye azititetezera
Ineyo ndikuthandizani baba
Tiyakhuleni amavuto tili ambiri
Koma añthu amapanga zinthu mmm
Eish ndip
Sono zosezi umaonaz sumapephera bwanji mulungu salephera ndipo sanarepherepo muzina ra yesu khristu
Chonde musanyozere
Sed your number
Ayi pepani limbikirani kupemphera basi
Eeeeee koma nde zowopyatu
Ndipo akazi ambili mukasiyana amapangadi zamasenge kuti asazakuwone zako zikuyenda
Muli ndi mwai okwatira mfiti
Mmmmh abale😂
Ambuye akumenyele khondo thawi zonse
Malodza
Tithokoze mukuyitha kwambiri
Muziponyabe pa youtube