He's real UTM....sakulimbana ndikuzinamiza kumagula nsalu za DPP or za UTM nkumaveka zigoba...iyeyu ndi mfundo zake zokweza Malawi 🇲🇼 typically SKC thinking....akuchita kuonetsa kuti SKC amamukonda ngakhale anali ku Blue camp! Kusiyana ndi enawa ochita kudzidzimuka kunamizila, kuzinamiza, komaso kuwanamuza abwana 😂😂😂😮😮
A😂😂😂 ongofuna kugwiritsidwa ntchito ndi chikangawa awa ndale zaku Malawi zomvetsa chisonitu zolankhula ndijungoti mpulumutsi uja wafika Soasidwe mpata 7 out of 100% Kufuna kusokonedza mitu a Malawi basi
Ilove the Guy Kabambe
My vote Kabambe ❤
I just love this guy Kabambe (he knows his staff)
Genius of economy and presidential tactics giant.
Kambambe president next
Nfundo zake nzabwino close to chilima uyu akunela
Big up Dr kabambe
UTM IS ONLY HOPE FOR MALAWI .
We are gone for age,, for Kabambe, you seem like SKC legacy
Ndi UTM yokha yimakhala ndi manifesto yothandizira Malawi uyu. UTM more fire
I like the way how Cathy is reporting
Kabambe sangapange kalikonse wachepa, mufuseni bakili afotokoze mwemwe anamusankhira bingu
He's looks like he can take Malawi
Work hard mayi upuzireko china chake kwa Brian Banda
He's real UTM....sakulimbana ndikuzinamiza kumagula nsalu za DPP or za UTM nkumaveka zigoba...iyeyu ndi mfundo zake zokweza Malawi 🇲🇼 typically SKC thinking....akuchita kuonetsa kuti SKC amamukonda ngakhale anali ku Blue camp! Kusiyana ndi enawa ochita kudzidzimuka kunamizila, kuzinamiza, komaso kuwanamuza abwana 😂😂😂😮😮
Fact man
Ndayamba kumukonda kabambe hvy
Kabambe ñdi ozitsata kwambiri ndipo akudziwa zomwe akunena komaso akuchita
Catherine maulidi ndiwe dhilu Banda akukusuladi
A😂😂😂 ongofuna kugwiritsidwa ntchito ndi chikangawa awa ndale zaku Malawi zomvetsa chisonitu zolankhula ndijungoti mpulumutsi uja wafika
Soasidwe mpata 7 out of 100%
Kufuna kusokonedza mitu a Malawi basi
Aaaa akutitayitsa nthawi ameneyu
Koman tamufusan kabambe ,at ndizoona kut mcp ikumunyengerera kt achoke ku utm?
Yeah akumunyengerera ndi dollar
Koma sangamuthe
❤
Ndale zikufunika panopa ndi izizi za reform osati zakale zothana ndi atsamunda.
Aaaa akutitayitsa nthawi ameneyu
Akutaisa nthawi iweo