Nkhani yovetsa chisoni ya mwana wa Ibrahim swed ndi Angella

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 10 ก.ย. 2024
  • DNA YA IBRAHIM SWED IWUSA MAPIRI PA CHIGWA
    Mponda matiki wina yemwe amakhalira mu mzinda wa Lilongwe koma kumudzi kwawo ndi ku Nkhotakota, Ibrahim Swed lachiwiri pa 29 November anatutumutsa anthu mdziko muno atalemba pa tsamba lake la mchezo la Facebook kuti mwana yemwe ali naye limodzi ndi mkazi wake Angella si wake. Mwanayu yemwe zithunzi zake zakhala zikuyenda mmasamba amchezo pamodzi ndi mayi ake, akuti, ndi wa munthu wina yemwe Swed sanamutchule bwinobwino. Iye wadziwa izi akuti atakapangitsa DNA ku chipalata china chotchedwa Alpha Biolabs ndipo ma dotolo kumeneko anamutsimikizira kuti mwanayo si wake.

ความคิดเห็น • 48

  • @paulkatunga5738
    @paulkatunga5738 ปีที่แล้ว +2

    Nkhani zamahule izi zitayeni. Ambiri akulera ana omwe siawo mmabanjamu

  • @collinscolyman6730
    @collinscolyman6730 ปีที่แล้ว +2

    Zowawa kwambiri, koma mwanayo akupatsani ndiwanu bwana. Please take care of him as your own . God bless you sir

  • @Fatima-ck3mu
    @Fatima-ck3mu ปีที่แล้ว +1

    Mwana ndiosokholana onsewo muli chiwalo chao😂😂😂😂😂🙌 malawi🔥🔥

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 ปีที่แล้ว +1

    Hanifa tsopano watokota ndi ya Swed..Tamva nawo amzimai ambiri amakonda zimenezi..zikomo tamva nawo

  • @Emmanuelwilliams-ev2ys
    @Emmanuelwilliams-ev2ys ปีที่แล้ว +1

    mumakhala ndi nkhani zabwino ,, koma vuto you have low quality video pro ,,nanga nkhani ya swed muzikationetsa ku limbe osamationetsa swed ena amudziwe amene samudziwa

  • @benchilenje9856
    @benchilenje9856 ปีที่แล้ว

    Bro swed make sure keep ur blood ndwan mwanay

  • @lestermaide-yy4xy
    @lestermaide-yy4xy ปีที่แล้ว

    Good news

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 ปีที่แล้ว +1

    Sanalakwe swed wolakwa ndi kadzi polengezesa za mwanayo kuti ndi wa swed pomwe amziwa kuti tsi wa swed

  • @williamskondowe8795
    @williamskondowe8795 ปีที่แล้ว

    Ok tamvano achina angellawo eishhh

  • @stevinmuhone877
    @stevinmuhone877 ปีที่แล้ว +2

    Zikomo hanifa potipasa zinkhani

  • @muhammadimusitafa7545
    @muhammadimusitafa7545 ปีที่แล้ว +2

    Bwanj yathera panjira nkhaniyi??

  • @stansama8896
    @stansama8896 ปีที่แล้ว +3

    Brother swed keep the kid as yours just stay quiet just increase your security from today your Life is in danger just be ready to fix nicely the owner of the child under carpet,, so clean and you are big man zazing'ono izi deal with that idiot smart, stop using social media do things crean keep on investigating , you will get the guy , your money is your answer just be smart when you do your things bcz ppl are so jealous with you madam bwino nawonso ndi enemy number 1 mwawayalutsa koma sangakutayeni chifukwa cha ndalama zanuzo nde bwino nawonso amenewo

    • @jumakananjirazim
      @jumakananjirazim ปีที่แล้ว

      well said

    • @stansama8896
      @stansama8896 ปีที่แล้ว +1

      @@jumakananjirazim nkaziyo nde oyipa amafuna kuwadyela bwana swed wo now ndinthawi yawo brother swed awonetse nawo udolo wawo anthu anawapusitsa MASIKU ANO KUMAWAPATSA ANTHU ZOFUNA ZAWO , KULIBE KAPEE !!!! Asapupupulume nawo anthu amenewo chachikulu asamale nawo awasowetsa b4 complete the mission

  • @saulbipa6882
    @saulbipa6882 10 หลายเดือนก่อน

    If they can do this to Swed, a rich guy, who are we akapopangolo

  • @PeacefulWildFlowers-sl8er
    @PeacefulWildFlowers-sl8er 7 หลายเดือนก่อน

    Azimai kukonda kuchinditsa iiiiiiiiiiii

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 ปีที่แล้ว

    Ndachisilu akasamalira mwanayo imagine mupangidwa chisilu fo such long and still taking care of mwana my foot

  • @obreljkumbuna5976
    @obreljkumbuna5976 ปีที่แล้ว +1

    Zovuta kwambili,ofuna sazipezad ndatsimikiza,

  • @adamabiyen5079
    @adamabiyen5079 ปีที่แล้ว

    eish vuto lopeza mahule ND chocho 😆😆😄 nawenso amafuna akubere ainse

  • @thomastenes949
    @thomastenes949 ปีที่แล้ว +1

    hanifa TH-cam channel here 😂😂😂 don't trust anyone

  • @HAWAHANDRWE
    @HAWAHANDRWE ปีที่แล้ว +1

    Swed siolakwa km chilungamo

  • @jumakananjirazim
    @jumakananjirazim ปีที่แล้ว +1

    ndie nkhan yaku lilongwe chokajambulila Ku Limbe mchaan??/😎😎

    • @girlmama265
      @girlmama265 ปีที่แล้ว

      😂😂😂😂😂imagine

  • @norahdausi6017
    @norahdausi6017 ปีที่แล้ว +1

    Nde mukuyankhula bwanji abale anzanga😄

    • @lu3366
      @lu3366 ปีที่แล้ว +1

      Ndipotu😭😂kukokomeza

    • @norahdausi6017
      @norahdausi6017 ปีที่แล้ว +2

      @@lu3366 za pa Malawi kkkkkkkkkkk

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 6 หลายเดือนก่อน

    Zachisoni azimai mmm😂😂😂😂😂

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 ปีที่แล้ว

    Hule uyo

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 ปีที่แล้ว

    Ndikumva phokoso la minibus yokha kkkkkk

  • @innocentpmangani2777
    @innocentpmangani2777 ปีที่แล้ว

    A zimayi kukonda ndalama samakhutisidwa ndi mamuna mmodzi

  • @shaibukeakeni6224
    @shaibukeakeni6224 ปีที่แล้ว +1

    Mumatiimilira hanifa

  • @girlmama265
    @girlmama265 ปีที่แล้ว

    Suwe alibe masewela😂😂😂😂

  • @richardlulanga8900
    @richardlulanga8900 ปีที่แล้ว

    Hule lamzimayi

  • @Eliasiwhite-foreveryoung
    @Eliasiwhite-foreveryoung ปีที่แล้ว

    Kkkkkkk koma

  • @jonasbanda5605
    @jonasbanda5605 ปีที่แล้ว

    Mwanayu loko chaka sangathe malume.

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 ปีที่แล้ว +1

    Mahule

    • @giftmaliwa2385
      @giftmaliwa2385 ปีที่แล้ว

      Kodi simutha kuyankhula bwino bwino mauwo? Zimandimvekera mwa chimidzi

    • @Lialibra2166
      @Lialibra2166 ปีที่แล้ว

      Kod basi?😂

  • @gladyschimwaza6111
    @gladyschimwaza6111 ปีที่แล้ว

    😅😅😅

  • @mumdekmkwinda1923
    @mumdekmkwinda1923 ปีที่แล้ว

    Mmmmmmm ndiye kukajambula ku limbe 🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @ickbwoy6123
    @ickbwoy6123 ปีที่แล้ว

    😂🤣😂🤣😂🤣

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 ปีที่แล้ว

    Hahahahahah

  • @austinphiri9000
    @austinphiri9000 ปีที่แล้ว

    😂😂😂😂😂😂