Zilibwino akumudzi kwathu m' mbali mwa mtsinje wa Nathenje apo tinkadyerapo mbatata yosasenda kale ife tisakudziwa kuti pali ulaliki wathoo. Mwandisintha kwambiri ndi nyimbo maka maka yoyambayi. Andipatse mtima wopilira zonse zondipinga dziko lavuta ili. Masiku ano ndi gwira bango madzi angakutenge kikkkkkk Alleluya.
Zodalitsa pitilizani osabwerera mmbuyo ❤❤❤❤❤
Zilibwino akumudzi kwathu m' mbali mwa mtsinje wa Nathenje apo tinkadyerapo mbatata yosasenda kale ife tisakudziwa kuti pali ulaliki wathoo. Mwandisintha kwambiri ndi nyimbo maka maka yoyambayi. Andipatse mtima wopilira zonse zondipinga dziko lavuta ili. Masiku ano ndi gwira bango madzi angakutenge kikkkkkk Alleluya.
Amen and amen azimai
Watched this from Lundazi Zambia 🇿🇲
Best regards!!! God should really impose on us a perseverance heart 💓
So nice do good keep it Nanthenje women choir thank you as lot
Amen tikuyenda ndiyesu Koma osawa
Mwatikumbutsa a Busa a CHIRWA. Mzimu wawo uwuse mu mtendere.
Amen amen mundipatse mtima opilila wakukana zonse zondipinga ,azimai akwathu mulungu azikudalitsan mthawi zonse
Amen 🙏🙏🙏🙏
Zilibwino mupitirize zikusintha moyowanga
Nice music , we enjoy ur music here in Zambia
Thats true we walk with God but we don't know him, Family of God let us walk in the right of God and we should know him
Amen n amen 🙏
Nathenje moto kut buuu ..A yahweh iziii
Wow!!! What a song go ahead mothers union ambuye akudaliseni.Amen
Nice singing azimai God bless you all
Amen Amen am still blessed grory be to God Haleluya more fire ladies
Zili bwino za kwathu. May God bless you azimai.
Ndayikonda kwabasi 💃💃💃💃💃💃
amen azimai akumudzi mmm mukuveka ndipo mulungu akudalitsen,ine adnes namamo kalumbu
I can see you from Zambia nice song
Nice. Good. Singing bless. All
Very nice keep it up ladies
Nice song and so touching be blessed
Keep it up azimai akwathu mumatha
Amen azimai
Akhristudi alero tikuyenda ndiyesu komadi osaziwa nyimbo yosisimusa
Praise be to God.
Zili bwinooo
Amen and amen opilirawo!!!
Pitirizani azimayi UK kumudzi kwathu apollo pa Nathenje kwa Kalumbu
What language they sing
Chewa from Malawi
Chichewa
Amen