Psalm 23 v1-6 delivered & Simplified ❤ To DE PUBLIC for Edification !! I like it ,Kp De Fire Burning Masintha CCAP Chotsitsimutso Choir !! U R Indeed Another Tool /Arm to Revival to The Nation & Society!! Kp on Igniting De Flame !! May God Anoint & Equip U more 4ExtraOrdinary Service !! UP! UP JESUS !!❤❤💪🙏🙏🙏🙏
Amayi mumandidalitsa. Ambuye akutsogolereni tikayimbe ndi Angelo pakutha pa zonsezi. Koma kukakhala chimwemwe chosatha. Ambuye ndisadzatsale ine nkayimbe nanu nyimbozi
Proud to be a Presbyterian
The best version ever, the backing vocals sweet and calm. Glory be to God. Makes me proud to be a member of C.C.A.P
Nyimbo yaimbidwa bwino kwambiri ngati siyomwe ija yotchuka timaidziwa ija. Well done azimayi
Komatu zoonaaaa
If I may see heaven, this choir will have a 70 percent contribution to my holiness. God continue blessing these mothers.
💃💃💃🥰🥰🥰God bless these songs
Ndidzabwezela yehova chiyani
True my brother 😊
Beautiful singing
Ambuye azikudalitsani Azimayi mumaimba nyimbo zotitsitsimutsa mu Uzimu😭😭🔥🔥🔥❤️❤️❤️
This song dedicated to my mom and dad. If there's phone in heaven please I want to sing this song with mom and dad
Continue resting in peace dad
Great , melodious ,sentimental, and spiritual !
I almost listen to every song of this choir. Well composed, with deep spiritual message. May God keep blessing these women and choir abanduntly
Mulungu apitilize kukusogoleran kufalisa uthenga wake kuzera ku nyimbo zokoma zopasa tanthauzo amen
Ambuye akudalitsen mumatitsitsimutsa kwambili amen nyimbo imeney aaaaaa ndilibe mau🙏🙏
This was mum's best song, every time I hear it I remember my mum.
Much love and blessings from Vila-ulongue Angonia- Mozambique.
Mumandivetsa kukoma nyimbo zanu azimayi ngati ndafika kale kumwambako ❤❤❤❤❤
Wow l want to sing this song in heaven, my lord you are my protector gide me right way to pass through
Much love from Kenya East Africa
Honestly,I feel so deeply blessed whenever am listening to this song.Ooooh Jehovah you are my God.
I feel strengthened with this song. May God almighty bless these ladies in Christ our Lord
Mulungu azikudalitsani
azimayi nthawi zonse pitilizani kuyimba bwino nyimbo zotsitsimutsa GOD bless you all Amen
So touching and inspiring song.Well composed with spiritual maturity 🙌 🙏 ❤❤. God bless you all beautiful women ❤️ watching from zambia 🇿🇲 ❤️
❤❤❤❤❤❤
Nyimbo koma iyiiiii,, achmanyamata munayilingalira iyi, Ambuye apitirize kukutetezerani muutumiki wamayimbidweu.
Zoona dziko lapansi limadana ndi chilungamo ❤
Kumwamba kuzilemekezeka. This is so amazing
I feel like heaven is hear on earth with these women. Their singing heals my broken heart. God bless you mamas
Azimai awawa amatha..I was once a church elder for their ward in Lilongwe kawale 3 under masintha CCAP.
On repeat and getting blessed, so grateful to YAHWEH ❤❤
Pali nyimbo zina ngat wafika kale kumwamba ukamaimba kapena kuvera mulungu azikusogolelan mukundidalitsa kwambili azimai
Tikutsitsimuka kobasi kuno ku Capetown south Africa ambuye akudaliseni nomse azimayi ❤❤
May God the almighty bless the wemen of this choir
❤
Psalm 23 v1-6 delivered & Simplified ❤ To DE PUBLIC for Edification !! I like it ,Kp De Fire Burning Masintha CCAP Chotsitsimutso Choir !! U R Indeed Another Tool /Arm to Revival to The Nation & Society!! Kp on Igniting De Flame !! May God Anoint & Equip U more 4ExtraOrdinary Service !! UP! UP JESUS !!❤❤💪🙏🙏🙏🙏
Azimai amatha kuimba pitlizani timadalitsika ndi nyimbo zanu amen
Powerful massage 🙏🙏 the lord is my shepherd well composed song may God bless you all for preaching through singing lam listening from Zambia
I miss this church alot azimai ndimakunyadilani kwambili ndi kawale two pafupi ndi mrs Chadewa
Azimai inuyo Mulungu akupatseni miyoyo yaitali mumandidalitsa ndisaname 😭❤❤❤❤❤🔥
My dad and mom, grannies inclusive I think you are in the house of the Lord!
Amen nyimbo zanu ndidalitso wanga nthawi zonse mulunugu adzikudalitsani ❤❤😊
Amai Chikaphonya ku Dowa atsogoleri achigwilizano anatsogolerapo nyimbo iyi mu Limbikani choir Mulungu anawadalitsa ndimau abwno❤
She has a good voice indeed.my mom is a former limbikani choir member.We transferred out od Dowa
The blessed woman's of God I love this spiritual songs.
❤ this song was well cooked
May God continue giving you wisdom and more talent🎉
Best song , i like the bass ladies, l miss that bass lady, may her soul continue resting in peace
I'm saying Mrs chigwani,
May her soul rest in peace 😢
Which one😞
@@Joy-in-chaos-rc9ff Mrs Chingwani
Nice
May Lord bless this choir ndipo amayimba bwino kwambil
May God enlarge your territory mamas i always blessed with your songs
Nyimbo imeneyi 👆 imandipanga ine kukhulupila Yehova koposa chinthu chilichonse Amen
Thank you our mother for the sweetest song am here in south Africa proud of you
I'm proud about this spiritual song,God be you masintha women
This is a nice song keep it up dear mamas you are the best
I dedicate this song to my sick grandmother wishing you a quick and speedy recovery ❤
Mmm this is really owesome may the almigty God richly bless you my Mothers
This is my prayer this night 🌃psalms 23 vs 1 to 6🙏
Keep on nice singing our Mothers listening from SA
Amayi mumandidalitsa. Ambuye akutsogolereni tikayimbe ndi Angelo pakutha pa zonsezi. Koma kukakhala chimwemwe chosatha. Ambuye ndisadzatsale ine nkayimbe nanu nyimbozi
I remember my dad...he likes gospel songs
Just in love with the song keep up ladies its my every day morning song
Masitha , am always blessed with your songs ,amen
This song reminds my young brother THEODORE may his soul rest in peace 😢😢😢
I love the creativity, the content of the song, powerful song
Always am blessed with your songs, keep it up
Wow you ladies mmmm God bless you with this nice song
Beautiful singing with encouraging message. Keep it up mamas n stay blessed
Always reminds me me of my dad,, hope he is in God's hands resting
Ilike the song,is international song keep it up mums
Azimayi inuyo mumatha. God bless you all.
Yehova mbusa......wangadi....................wandigonesa!..................mumsipu x2
Yehova mbusa wanga di, ndiribe kusowa, wandigonesa bwinodi mumsipu okoma x2
Kumadzi ake..........odikha.............ndimoyowanga!...............wofoka x2
Kumadzi ake odikha anditsogolera, ndimoyo wanga wofoka waulimbikitsa x2
Mwazodza mutu...........mafuta...............mwadzadza chikho!....................changadi x2
Mwazodza mutu wanga ndi mafuta okoma, mwadzadza chikho changadi ine chisefuka x2
Kumadzi ake...........odikha.............ndimoyo wanga!................wofoka x2
Kumadzi ake odikha anditsogolera, ndimoyo wanga wofoka waulimbikitsa x2
Zokoma ndiza...........zakuyanja........ndikhala nyumba!............ya Mlungu x2
Zokoma ndizakuyanja zizanditsatako ndikhala mnyumba ya Mlungu ku nthawi zonsezo x2
mm mm mmm.............mmm mm mmm..........mm mm mmm.........mmm mm mmm x2
mm mmm mm mmm mm mm mmm mm mm mm mm mmm mm mmm mm mmmm x2
Oyera oyera oyera Yehova Mlungu wathu tikuyamikani Yehova chifukwa cha zokoma zonse mumatichitila pa myoyo yathu, zoonadi tilibe kusowa, paliponse mumati tsogolera, ndipo sitikhala ndi mantha popeza inuyo mumatipelekeza kuli konse komwe tipita, ndipo Zikomo Yehova chifukwa cha moyo wathu, ukapooka mumatilimbikitsa ndipo tikulonjeza Yehova
tizakhala kunyumba yanu kunthawi zonse.... amen
Zokoma ndiza........zakuyanja..........................ndikhala nyumba!.........ya Mlungu x2
Zokoma ndizakuyanja zizanditsatako ndikhala mnyumba ya Mlungu ku nthawi zonsezo x2
Amen Amen azimayi kuyimba mwalutso.
Inali nyimbo yoyamba imene inaimbidwa pamene agogo anga amanyamuka rest well my lovely grand father
More than a blessing may the good Lord enlarge your territories
Amayi a Masintha amanditsitsi mula maimbidwe awo. Mulungu aptrize kukutsogolerani
A very beautiful song so spiritual and touching
Best song and instruments are well balanced with their voice.
Thanks you!
For ur I love the composure
Your music blesses me 🎉🎉
God bless you children of the living God love you All ❤
That's powerful song glory to be God
Ndikavera nyimbo iyi moyo wang umasinthik kwambr🙏
Praise the lord, i feel so blessed,hallelujah
Mukuimba bwino zedi azimayi, keep on❤
It's amazing song , praise God
Pitilizani kuyimbila mulungu nthawi zonse mwini moyo uno. Nyimbo imeneyi imanditsitsimutsa zedi.
May the name of the lord be glorified
Inde Yehova ndi Musa wanga
Amen
Andigonetsa😊
Well done Women of God Madintha uko ku Kaware2
This is very powerful..amen
Ambuye sataya wakeeee❤❤🎉
Azimai mumathaaa ambuye akudalitseni
This song remind me my rate mother she used to sing this song
Great, melodious, spiritual gospel music
Thank u our mother's for s good song am here in lundszi
Mulungu ndiye chikondi..Amen
A nice song God bless you mama
Always I blessed with these songs
Ndimakumbukila a Gogo anga mayi Napili Wateya mzimu wawo uziwusa muntendere ameni
Mzimu wanu uzipitilila kuwusabe muntendere mayi Naphili Wataya
Proudly be Presbyterian
Good song form masitnha !
Get well soon my Mother I love you sweet mother ❤❤
This is powerful song ❤
Nyimbo zanu zimanditsitsimutsa Ambuye akuze malire a choir yanu
My Favourite Choir
Powerful may God bless you
Comernt flom zambia ayam a james good songs 😅😅😅😅
Mumaimba bwino azimai pitilizani ❤❤❤❤
Touched song and beautiful instruments
I love the song n glory be to God
Amen, am really blessed
This is touching song big up women