Chisawawa | Maliro Achilima | Timva Zinthu | Tiyeni Tidekhe Kaye Amalawi.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ก.ย. 2024
  • #malawi #trending #viral

ความคิดเห็น • 74

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 3 หลายเดือนก่อน +6

    Koma chakwera 🙌🙌 mupaka kumpha muzanu ngati galu mulungu akukathe ndithu kulimba mtima ngati fiti yayikazi Koma wayaluka kulibe kuwina 2025 wukazawina ndiye Kuti wabera Koma sikuzakhara mtendere

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 3 หลายเดือนก่อน +7

    Sadiki mia ,chiwaya kasambala lero chilima amalawi tidzaputsa pakana liti chakwera ndipitanaye

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 3 หลายเดือนก่อน +1

    This should mark the begining of a great revolution in malawi. Panunkhe mphila basi sitidikiranso za 2025.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 หลายเดือนก่อน +7

    Udindowo saupeza Chakwera. Chakwera ndiwe otembereredwa.

  • @IsaacTsinde
    @IsaacTsinde 3 หลายเดือนก่อน +4

    Sichinakawinina chimenechi kupanda Chilima amuphayo

  • @LovenessGerald-n7f
    @LovenessGerald-n7f 3 หลายเดือนก่อน +1

    Palikundu pake ndipo galu ameneyo achite kuyipa khope ngat utsiku 4😭😭😭

  • @johnlameck8366
    @johnlameck8366 3 หลายเดือนก่อน +5

    Koma chilima yenkha anamulakwira bwanji

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 3 หลายเดือนก่อน +4

    Chalakwika kwambiri kupha anthu Ena chifukwa cha munthu mozi 😢😢😢

  • @MaureenMchenga
    @MaureenMchenga 3 หลายเดือนก่อน

    Zosakhala bwino kwambri😢😢😢😢

  • @jamesbanda1730
    @jamesbanda1730 3 หลายเดือนก่อน

    Mr president what happening in Malawi ha our home hear of Malawi our country is finishing with politicians Malawians are know going tru problems of end of Malawians financial Mr president must step don Malawi this movement of Kamuzu Banda know in Malawi Malawians the are back old movement with some people of Kamuzu Banda Gov.

  • @EsterJackson-v4g
    @EsterJackson-v4g 3 หลายเดือนก่อน

    😭😭😭😭

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike 3 หลายเดือนก่อน

    Chilima walakwanji abale😭😭😭

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o 3 หลายเดือนก่อน +3

    Zonse ndikulakwitsa nanga ndindan amafuna kufa pa onsewa

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 3 หลายเดือนก่อน

    Ngati a Malawi apapa sitipangapo kanthu palibenso tsogolo la dziko

  • @abdullalajabu5871
    @abdullalajabu5871 3 หลายเดือนก่อน

    timawonedwa kupusa amalawi chifukwa choti ndefe odeka komaso sitikuyiziwa nkhondo fuso ndikumati tizapange bwanji kuti nafeso tizakale osawopa😭😭😭😭

  • @pepichikako7122
    @pepichikako7122 3 หลายเดือนก่อน

    Koma Amalawi atopa. You know our people can be ruthless. Ine if I were him I would seek asylum. He looks like people want to take revenge on him and his family members.
    My prayers to the Chilima and all our fall Malawi government crew.

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ambuye atichitile chifundo ku Malawi ndikutukhululukila pazimwe sitinachite bwino pamaso pake😭😭😭

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 3 หลายเดือนก่อน +1

    Awuzeni ndithu mwina anva tikulira ife😢😢😢😢

  • @BlessingsFranklinWadson
    @BlessingsFranklinWadson 3 หลายเดือนก่อน +3

    Pwanya pake chakwera pamtumbo

  • @Guttagaard
    @Guttagaard 3 หลายเดือนก่อน

    Anthu akwiya kumene this is not the 1970s anymore

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 3 หลายเดือนก่อน

    Komatu Chilima mwamulakwira kwambiri. Anakumenyerani campaign kuti muwine in 2020, lero mwapha munthu amene adakumenyerani nkhondo, inuyo mmadziwa bwino kwambiri kuti ku north and Southern region without chilima simukadawina. Ndipo this tine around forget it

  • @ChosenChirwa
    @ChosenChirwa 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ndipo angodikira tiyike maliro awonasotu chakwera

  • @AgnesChikonje
    @AgnesChikonje 3 หลายเดือนก่อน +3

    Komanso munthu modziyo amupheranji poti democracy ndiyawina aliyense

  • @benzobanda-ed8tp
    @benzobanda-ed8tp 3 หลายเดือนก่อน

    Good wayankhula bwino bola akanafa ndiyeyo chichakwelacho

  • @patriciagondwe2934
    @patriciagondwe2934 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mulungu dalisani malawi

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 3 หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo wanenelatu kuti ine ndidzafa ndi imfa yamulungu osati zanuzi simunditha ine ndi patali muononga ndalama zanu kumpatsa anthu anuwo kuti andisake koma sizitheka kkkkkkkk

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 3 หลายเดือนก่อน

    Mulungu akudziwa 😭😭😭😭

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike 3 หลายเดือนก่อน

    Sikusinja Gwenembe

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 3 หลายเดือนก่อน

    Chitsiru chinanso ndi army commander valentino, osanyengerera, asowe.

    • @gladyschisomo4324
      @gladyschisomo4324 3 หลายเดือนก่อน

      Ndipo nde ndimbuzi yamano kusi

  • @mostermostz5895
    @mostermostz5895 3 หลายเดือนก่อน +2

    Simikizilan ngat chakwera waphad chilima. Osamasokoneza maganizo azanu. Ngat pali umbon okwanira ufotokozen tikusaten

    • @FosterChilumba
      @FosterChilumba 3 หลายเดือนก่อน

      Kamanyi wakudambwe iwe ukuti chiyani

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน

      Ufuna unoni wanji cakwera ndi wakupha wasatanic mbusa wakumidima wapha chilima ndi anthu ena munthu oipitsitsa mdziko lamalawi osava chisoni ladzalo cakwera

    • @BFWCPHIRI1978
      @BFWCPHIRI1978 3 หลายเดือนก่อน

      Chakwela ndi okupha kumene ndipo aka sikoyamba ,wakhala akupha kuyambila ku church pofuna utsogoleri. Koma apa ndie walakwila dziko lonse pakupha chilima.

    • @ElliottBelon
      @ElliottBelon 3 หลายเดือนก่อน

      Mboli yako

    • @BenjaminKamanga-p8w
      @BenjaminKamanga-p8w 3 หลายเดือนก่อน

      Olo iweyo umboni oti chakwera ndiyemwe wapha ulinawo koma ukufunsa chinyezi mbafa galu iwe.

  • @benzobanda-ed8tp
    @benzobanda-ed8tp 3 หลายเดือนก่อน

    Good

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 3 หลายเดือนก่อน +3

    Chakwera Chakwera Chakwera wapha Chilima why

  • @fumbomumba5016
    @fumbomumba5016 3 หลายเดือนก่อน

    Chakweka ndi mbuzi kwabasi

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 3 หลายเดือนก่อน +1

    Malawi poison party mmmm chakwera imfa yomwe yagwika lero chilima mawa idzakupeza .

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi anthu amenewa akulira onsewa ntendere mukupeza komaaa???😢😢😢😢😢😢

  • @Short1212-ny4ng
    @Short1212-ny4ng 3 หลายเดือนก่อน +1

    Tikupeza tikupanga

  • @JacksonMoyo-tm8dv
    @JacksonMoyo-tm8dv 3 หลายเดือนก่อน

    Achakwera, zikhale ng'oma ndi kunkuyu atule pansi udindo atiphweteka kwabasi

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 หลายเดือนก่อน

    Koma ife amalawi tilibe nzelu ndithu tinamusankha tokha gulu uyu chakwela Kodi tingaskhe munthu woti alibe kalikonse ndikumusankha kuti akhale president zowoona zimenez andiso munthu woti akuthawa mulungu ndikusata satana ndiye ife nkumati ndiwabwino alongosola zinthu zoona tiyeni tiphuzilepo kanthu ife amalawi tiyeni tiseguke matso

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 3 หลายเดือนก่อน

    98% says a ........ ndi omwe apha a .......😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @EliasBanda-qj4bn
    @EliasBanda-qj4bn 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera nigalu kwambiri

  • @TressLuka
    @TressLuka 3 หลายเดือนก่อน

    Malòdzatuuu 😢😢😢😢

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 3 หลายเดือนก่อน +1

    Amalawi dzofuna tingoyamba khondo basi

  • @joaojoao1983
    @joaojoao1983 3 หลายเดือนก่อน +1

    Munamusanka ndinu.

  • @JosephChatama
    @JosephChatama 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mbudzi yamano kusi ikufuna umboni wina

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน

      Chisiru iwe kwabasi mbuzi anamno ako ndi amako iwenso ndi wamagazi mmmm munya muona asatanic inu

  • @DerickZiba
    @DerickZiba 3 หลายเดือนก่อน +1

    Devils kupha no good

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 3 หลายเดือนก่อน +3

    Akuwuze ndani? Pita kafufuze sinanga uli ndi nzeru kwambiri. Kuyankhula mopusa uku

  • @IsaacTsinde
    @IsaacTsinde 3 หลายเดือนก่อน +2

    Afiti opemphera a chakwera

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 3 หลายเดือนก่อน +1

    Tibweze bas

  • @KasimuMaulana-mu8we
    @KasimuMaulana-mu8we 3 หลายเดือนก่อน +1

    Kwamtele ndi chimadala

  • @EnelessLundu-sn8om
    @EnelessLundu-sn8om 3 หลายเดือนก่อน

    Kuntcheu kokhako osakamupatsa mpando kt akhale gwape ameneyo

  • @michaelamon9691
    @michaelamon9691 3 หลายเดือนก่อน +2

    Nkhani yolowetsa ndale pa maliro.

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 3 หลายเดือนก่อน +2

      Ngati mwapha Chilima ndiye mukalowanso mudzapha angati? Afiti otembereredwa inu.

    • @spargomw
      @spargomw 3 หลายเดือนก่อน +3

      Zitakhala zachitikira m'bale wako ungayankhule zopusazo? Misozi ya a Malawi ikhala ikumkumbutsa Mulungu dairy ndipo Mulungu aika chirichonse pa Mbalambanda

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน +1

      Ukati palowa ndale ukutathaudza chani iwe ndi opusa amalawi tikudziwa kuti cakwera wapha chilima mcp chipani ca magazi

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 3 หลายเดือนก่อน

      @@JoyceBanda-k8t Mkazi wanzeru kwambiri. Chauta akudalitse umaganiza mwanzeru.

  • @JohnMeleka-s1t
    @JohnMeleka-s1t 3 หลายเดือนก่อน

    Tikaonana kumaliloko ndiwathu ku ntcheu wina akatsala ine zachamba sifuna

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke 3 หลายเดือนก่อน

    Zowawatu koma

  • @ulemujumbe8501
    @ulemujumbe8501 3 หลายเดือนก่อน

    Komanso mfiti imeneyi isakapezekeko Ku maliroko

  • @georgeraphael8198
    @georgeraphael8198 3 หลายเดือนก่อน +1

    Ndi ngozi basi,a Malawi kupusa bwanji,muzachangamuka liti kodi? Kodi oyamba kufa pa ngozi ndi Chilima ekhayu?
    Musachuluse kulankhula zopusa, chifukwa anali munthu omveka za ziii 😂😂😂😂😂😂

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน

      Udzinena zimenezo ndi amako wamva cakwera wasatanic wapha chilima

    • @EnelessLundu-sn8om
      @EnelessLundu-sn8om 3 หลายเดือนก่อน

      Muuzeni chakwera kt akubanja akt usapezeke kumaliro kt adziwe kt anthu takwiya naye opusa ameneyu

    • @KestonNGUBO
      @KestonNGUBO 3 หลายเดือนก่อน

      Pa manyo Ako wav iwe

  • @jamesbanda1730
    @jamesbanda1730 3 หลายเดือนก่อน

    No no no as pastor

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala 3 หลายเดือนก่อน +2

    😢😢😢