Leftovers from the distant past the traditional Mfumukazi doesn't realise that her youthful radiance can't pluck the old flame into her Shoprite mess today. She runs her village without any councillors, it's a situational response to any matters Mama Mfumukazi ndi maulendo
Kkkkk its ndamunangatu awa kkkk mesa mmawakana koma nanyoni anakonza
Princess chitsulu mwayamba dzitsuzo Kodi mwasiya gospel?
Nkhani yatha osat ndinkhani yoti mutuluse nazo matumbo kkkkkk koma mfumukazi respect
Amfumukaxi congratulations for the decision made . Tatengerapo makamaka nagama kulandila zinthu thus mistake yolandila ija
Chabwino mfumu nkadzi mr amuchosa bwanji munyumba nankha padera zimuthera bwanji ine pheeee kudikira next moto buuuuuu
😂😂😂pamdera...akuti ziko linalengedwa bwanji..akazi sangakhale ndimakobili..akut sakupanga kanthu koma ana akubadwa
SINDIMATOLA ZOGWELA PANSI KKKKKKK. AHHH WELL DONE .FROM ZIM
😂😂😂😂😂😂😂 Iiiiiish km yap
Eeeee kukanana kwa bwanji uku abale
Akuti kungondiona ngt bashala nde nde kt basi
Mukakhale Amfumu akwathuu inuyo. Ndikupangana Hayalaa, 5 years contract mukasaine.
Kkkkk
Tikuziwana makona onse, mfumukazi anakoza🔥🔥🔥🔥
😅😅😅 more❤ 🔥🔥 Likiliki ladies you are the best for support
Girinánde kkkkkk is a character -liked from Hre
Hahahahahahaha koma maliro eish
Kkkkkkk km anfumu kazi
Congratulations mfumukazi mwandiweluzira bwino kwambiri ofunika kumagawanadi😂😂
Mmmmm😮
Kkkkkkkk eshiii koma zimandiwaza...gututu ndidolo.
Mfumukazi inu nkhani simaola akufunika apadera alangizidwe osati kungopita ntauni nthawi yomweyo ayambapo gwirogwiro... weruzani bwino mkhaniyi mfumukazi
Akuti azimayi ake anyadawonso?? Akazi akubadwa othilimana bwino akuti amuna azitigawana
Padera naye wakakamila pa banja akuti sakuchoka koma chikamwini nchovuta
Kkkkkk mfumukazi mumatha kuweruza
Gututu umandiwaza wamva kkkkkkk usazafe pano 😅😅😅
Fumukazi mukuwapasatu matama azimuna pakana mamuna sakhala ndikazi mozi zoona zimenezo mwationjeza kwambili 😢
Haha 😅zakupwetekani?
Good work times group
Maliro anabwera yu ndi Fredo kiss akubwera Yu NDi gamba tu Malo mwa gwuamba
Sou o primeiro directamente de moz 🇲🇿
shaaaa zafika pa fredokiss kkkkkkkkkk
Komatu guys mukubwera bho
🤣🤣🤣🤣mfumu kazi
Mfumu kazi tavomelano kt ndamunanu
Yomweyo mfumukazi
Nkazi padera ofunika mambama pang'ono , aziwe kulemekeza mamuna
Ilibwin kwambil
Kkkkkkk koma queen kungobwera ku mfumukazi kudzaika Virus kkkkkkk koma iweyo 😅😅😅😅😅😅
Afumukazi mwati imilila azibambo akazi mwachuluka😂
Mfumukazi ndi mbambande
Mfumukazi tangombiranani ndi giring'ande kkk
❤❤❤❤❤love u guys
Yoooo
Mfumukaz musatiputsise mukumufuna giling'ande😂😂
very true mfumukazi loves Giling''a nde - akumufuna
Akuti mundiuze chosuzumila kkkkkkkkkk koma mfumu kazi
Fredokiss akubwerayu ndi Gambaaatu kkkkkkkkkk
Padera wadyetsedwa makhwala 😂😂😂
Koma Agili😂
Fredokiss kkkkkkkk akubwera ndi gamba
Mfumukazi ndi ulendo 😂😂😂😂
Giling'ande eni ake azigogodo kkkkk
Koma mfumukazi ndi dirhu..mumatha
Mfumikazi🎉🎉🎉
But MFUMUKAZI COMEDY SERIES ni one 👌🔥🔥🔥🔥
Mai padela ingopangani chibwezi athawa ekha paberayo
Mfumukazi
😂😂😂😂 koma Giling'ande atamva ndi amuna anga haggi adah kkkk
.me chompret amenyo kkkkkkkkkkkkk
Giling'ande Machine
Koma nanyoni naye
Namoyo wasowatu 😂😂😂😂
Tizigawana iyaa! 😂🔥🔥🔥
Kkkkkk
Leftovers from the distant past the traditional Mfumukazi doesn't realise that her youthful radiance can't pluck the old flame into her Shoprite mess today. She runs her village without any councillors, it's a situational response to any matters Mama Mfumukazi ndi maulendo
fledokiss🤣🤣🤣🤣
Kalanka ....umaitha koma
koma ggiling'ande😂😂
😂😂😂😂koma mr shoprite
Mfumukazi akumufuna Ex 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Padera ndi nkhani zina 😂
😅 23:23
😅 23:23 😅
Princess Chitsuro ipa
Ipatse moto 🔥♥️🫂
Kkkk ndasangalala
Zilibwino
Koma iiiiiiiiiiii
Pitilizani kutisangalatsa timakunyadilani
Mumatha
PADERA UMAKWANA
Chosuzumila